ابحث في فهرس WhatsAd لمجموعات واتساب للعثور على الأفضل.
نتيجة واحدة في فهرس مجموعات WhatsAd
TAKURANDILANI KUCHIMAKE KWA NYIMBO MALAMULO ALI MOTERE 1.OSATUMIZA ZOLAWULA PA GROUP IRI KAPENA STICKER UKAPEZEKA REMOVE 2.MUNO MA VOICE RECORDING AKURETSEDWA ALIYESE AKUENERA KUREMBA 3.UKATUMIZA VIDEO OR AUDIO UKUYENERA KUREMBA TITLE YANYIMBOYO 4.KUTUKWANANIZANA MUNO AYI ALIYESE AZIREMBA DZINA LA NYIMBO YOMWE AKUFUNA 5.ZOSANKHANA MITUNDU MUNO AYI GYZ 6.KUREMBA TITLE ZIMATHANDIZA MUNTHU KUTI USATENGE NYIMBO YOTI ULINAYO KARE 7.UKAFUNA KUCHEDZA NDI MDZAKO KU INBOX UMUUZA AKALORA UPITA ☑️🤝🥰 8.KU INBOX KO MUKAYAMBANA NKHAN IMENEYO OSABWERETSA PA GROUP MUKAPEZEKA 🪓❌❌ ZIKOMO ANTHU NOSE MUGULUPU LIMENERI TIYENI TIPEZE NYIMBO ZA PAMTIMA PANTHU PANO 🙏
رابط دعوة موثّق وتفاصيل الأعضاء وخيارات الإعلان على WhatsAd.
*NYIMBO ZOTAMANDA KOMANSO KUKWEZA YEHOVA*
We sell bed linen and blankets of different types from South Africa 🇿🇦. Admin amakhala kubalaka and South Africa
Malamulo a Muno ------------------------------ (1)Kupempha ndikutumiza nyimbo. (2)Nyimbo zake ziyambire 2010 kumatsika kumusi. (3)Osatukwanana wina ndimzake timalimbikitsa ubale muno. (4) Osatumiza link or ma Photo olaura kapenanso zosemphana ndi group lino muzachotsedwa. (5)Osanyozerana mtundu kapena chipembedzo tonse ndi amodzi. Komaso osaponya ma sticker muno ayi (6)Ndi udindo wa aliyense kutumiza ndikupempha nyimbo zakale koma ngati mwafuna zatsopano pemphani ku inbox ena azakupatsani komweko. (7) Ma voice note siololedwa muno koma zikavutitsitsa kuti mufuna nyimbo nde mutu wake simukuudziwa funsani admin aliyense kuti mumumvetseletse Voice note ndipo akusakireni . (8)Osatukwana muno tili ndi anthu akulu akulu azaka zapakanthawi omwe amafunika kuwalemekeza. Tiyeni titsate malamuro kuti tipitilize kusangalara ndinyimbo komanso zochitika zotikumbutsa kale lathu .