ابحث في فهرس WhatsAd لمجموعات واتساب للعثور على الأفضل.
نتيجة واحدة في فهرس مجموعات WhatsAd
KUGAWANA NYIMBO KANTHINTHI MUNO MULIBWANJI MABWANA NDIMADONA NOTSE MUNO 🎥🎶🎙️🎶 NKHALAN OMASUKA NOSE PA GROUP PANO MOSATAYA NTHAWI MALAMULO ANTHU NDI AWA (1)MUSAPEZEKE KU IN BOX YAMZANU OPANDA CHILOLEZO MUKATERO REMOVE (2) TOSE TIKUYENERA KUMATENGA MBALI POTUMIZA NYIMBO NGATI TILINAZO. (3) MUNO SITIROLA KUTUMIDZA MA LINK ACHIKUNJA (4)GROUP LIZISEKEDWA NTHAWI IKAKWANA 10:30 PM SIKULILIROSE (5) PAKANKHALA CHOLAKWIKA NDI GROUP LINO PITANI KWA DIMIN WINAALIYESE KUTI AKUNTHANDIZEN (6)MUNO SITIROLA KULANKHURA VOICE UKAPEZEKA REMOVE❌ (7) NDIZOKAKAMIZA MWAWINA ALIYESE KUPANGA COMMIT PA GROUP PANO PASAMADUSE MASIKA 10 UKAPEZEKA ❌REMOVE 🎧🎤 POMALIDZA TINGOT NKHALANI OMASUKA NDIKULANDILA NYIMBO KANTHINTHI THANKS MY MEMBERS🎤🎧📹🔥🖱️🤳KUGAWANA NYIMBO KANTHINTHI MUNO MULIBWANJI MABWANA NDIMADONA NOTSE MUNO 🎥🎶🎙️🎶 NKHALAN OMASUKA NOSE PA GROUP PANO MOSATAYA NTHAWI MALAMULO ANTHU NDI AWA (1)MUSAPEZEKE KU IN BOX YAMZANU OPANDA CHILOLEZO MUKATERO REMOVE (2) TOSE TIKUYENERA KUMATENGA MBALI POTUMIZA NYIMBO NGATI TILINAZO. (3) MUNO SITIROLA KUTUMIDZA MA LINK ACHIKUNJA (4)GROUP LIZISEKEDWA NTHAWI IKAKWANA 10:30 PM SIKULILIROSE (5) PAKANKHALA CHOLAKWIKA NDI GROUP LINO PITANI KWA DIMIN WINAALIYESE KUTI AKUNTHANDIZEN (6)MUNO SITIROLA KULANKHURA VOICE UKAPEZEKA REMOVE❌ (7) NDIZOKAKAMIZA MWAWINA ALIYESE KUPANGA COMMIT PA GROUP PANO PASAMADUSE MASIKA 10 UKAPEZEKA ❌REMOVE 🎧🎤 POMALIDZA TINGOT NKHALANI OMASUKA NDIKULANDILA NYIMBO KANTHINTHI THANKS MY MEMBERS🎤🎧📹🔥🖱️🤳
رابط دعوة موثّق وتفاصيل الأعضاء وخيارات الإعلان على WhatsAd.
No refund only exchange tikuoda sizili available ngat mukukayika musaode ... kusankha kulipila kuyikidwa pa list...
*NYIMBO ZOTAMANDA KOMANSO KUKWEZA YEHOVA*
Malamulo a Muno ------------------------------ (1)Kupempha ndikutumiza nyimbo. (2)Nyimbo zake ziyambire 2010 kumatsika kumusi. (3)Osatukwanana wina ndimzake timalimbikitsa ubale muno. (4) Osatumiza link or ma Photo olaura kapenanso zosemphana ndi group lino muzachotsedwa. (5)Osanyozerana mtundu kapena chipembedzo tonse ndi amodzi. Komaso osaponya ma sticker muno ayi (6)Ndi udindo wa aliyense kutumiza ndikupempha nyimbo zakale koma ngati mwafuna zatsopano pemphani ku inbox ena azakupatsani komweko. (7) Ma voice note siololedwa muno koma zikavutitsitsa kuti mufuna nyimbo nde mutu wake simukuudziwa funsani admin aliyense kuti mumumvetseletse Voice note ndipo akusakireni . (8)Osatukwana muno tili ndi anthu akulu akulu azaka zapakanthawi omwe amafunika kuwalemekeza. Tiyeni titsate malamuro kuti tipitilize kusangalara ndinyimbo komanso zochitika zotikumbutsa kale lathu .