ابحث في فهرس WhatsAd لمجموعات واتساب للعثور على الأفضل.
نتيجة واحدة في فهرس مجموعات WhatsAd
MALAMULO 👇🏼👇🏼 1. Mukalowa tchulani dzina ndi komwe mumakhala kuti anthu akudziweni. 2. Zolaula muno ayi. 3. Nkhani za ku inbox zizithela komweko. 4. Osanyozelana Zipembedzo. 5. Tikuyenela kulemekezana wina ndi mzake. 6. Tiziponya nkhani zoona zokhazokha. 7. Mukafuna kulowa gulu la zachifundo fikilani admin kuti akulongosoleleni bwinobwino. 8. Ngati mwalakwilidwa afikileni adindo kuti akuthandizeni. 9. Aliyense akupemphedwa kutenga gawo muzochitika. 10. Nthawi yophunzitsana chinthu tikupemphedwa kutsatila mwachidwi ndi ndemanga komanso ngati sitikumvetsa tizifunsa pamapeto pa phunziro. 11. Ma stickers komanso ma vn ndi oletsedwa. 12. Za asing'anga komanso ma link ena ndi oletsedwa.
رابط دعوة موثّق وتفاصيل الأعضاء وخيارات الإعلان على WhatsAd.
1 Osasitha chithunzi kapena mutu wa gulu ❌❌❌❌ 2 Ma videos olaula or pic muno ayiii..🚫🚫🚫🚫❌❌❌❌ 3 Osatumiza link ya group lina muno ❌❌❌❌❌ 4 No voice messages/ stickers.❌❌❌❌ 5 Muno simosewela komo kugawana NKhani ndi Sports.✅ 6 Kumatengapo mbali osamangoti duu muzatulusidwa.✅ 7 Ulemu kwa aliyese ndiofunika✅ 8 Nkhani zaku inbox zithere Komweko Osazibweretsa Pano✅ 9 Ngati member wa group waona polakwika alowe ku inbox kwa admin Kuti Amthandize✅ 10 Kusarana ziyankhulo muno ai or zipembezo tose ndife amodzi amalawi.🚫🚫🚫❌❌❌❌❌❌ 11 Aziwitseni anthu zomwe mwatumiza kupanda kutero mupedzeka panja.✅ 🔚 by Admin