ابحث في فهرس WhatsAd لمجموعات واتساب للعثور على الأفضل.
نتيجة واحدة في فهرس مجموعات WhatsAd
TAKULANDILANI PANO PA KUPEZA WACHIKONDI MOSAVUTA AND MOSALIPILITSA Malamulo ali motere 1️⃣ kupeza wachikondi ndi ulere 2️⃣ ngt mukufuna mkazi /mamuna pezani admin aliyese ndipo muzifotokoze like 1 zaka 2 ana ngt mulinao 3 mukukhala kt nanga wachikondiyo akhale wakt 4 akhale wazaka zingt mkazi/mamuna mukumufunayo mukatelo muzidikila admin mwamutumizila zithuyo kubwereselani wachikoniyo 3️⃣ ngt mkazi or mamuna mwapatsidwao sadakusangalaseni muliso ndi mwai obwera kwa admin ndikuwauza kt akupaseniso wina 4️⃣ sitimalora zinthu izi 1 kuzipanga post wekha 2 ndi admin ekhayo amapanga post muthu ngt mwini wakewe ukuvomera kt akupange post pa grp 5️⃣ ngt mwalowa ku inbox kwa mkazi ky mamuna without admin zomwe mukazione uko ife sizimatikhudza 6️⃣ timakhala ndi call pa grp pano aliyese ndioloredwe kukapanga join 7️⃣ pano sitimalora zinthu izi 1 Zolaula 2 ma sticker 3 kunyozana 4 link ya grp ina muno ai 5 za ku inbox ky maudani akomwetimakhalako asabwere pano Ngt zina zakusowetsa mtendereukufuna ma ganizo anthu pezani admin tizapnga topic ndipo muzapeza choonadi kuchokera ku maganizo anthu omwe amapeleka pa toic Akapezeka onyozela malamulowa timapanga remove posatengera mtundu By admin
رابط دعوة موثّق وتفاصيل الأعضاء وخيارات الإعلان على WhatsAd.
*TAKULANDIRANI KU TIPEZE WACHIKONDI 💓💓* *MALAMURO NDI AWA* 👇 *1️⃣ALIYENSE AKUYENERA KUTENGA NAWO MBALI KUTI MACHEZA AKOME KOMASO KUTI TIPEZE WACHIKONDI MOSAVUTA👩❤️💋👨👨❤️👨* *2️⃣MULENDO UKAFIKA AKUYENERA KUPONYA PIC NDI KUNENA KOMWE UMAKHALA💃🕺* 🤳 *3️⃣MA LINK AMA GROUP ENA MUNO AI 👺👺* 4️⃣ *MA PROGRAM ATHU ALI MOTERE:* *MONDAY, WEDNESDAY NDI FRIDAY TIMAKHALA NDI* *TOPIC. NDIPO SUNDAY NDI PIC DAY* 💃🕺🤳 *5️⃣NKHANI ZA KU INBOX ZIZITHERO KUMWEKO* 🫐🫐🫐🫐🫐 *6️⃣KUCHEZERANA KUZIWANA KUMAONONGA GROUP KUMACHEZA NDI ALIYENSE* 🤺 *7️⃣VOICE NOTE MUNO AI & WEEK ILIYONSE TIMACHOSA ANTHU OSATENGA NAWO MBALI* 🤺🏹 *🌹🌹🌹TIPEZE WACHIKONDI*
Timapereka ngongole za business komanso Ulimi