ابحث في فهرس WhatsAd لمجموعات واتساب للعثور على الأفضل.
نتيجة واحدة في فهرس مجموعات WhatsAd
MUKANGOPANGA JOIN ISANATHE 10 MINUTES PELEKANI MONI KUPANDA KUTERO MUDZATCHOTSEDWA NDIPO SIMUDZAPANGIDWASO ADD. @CHICHEWA MOVIES@ *CHOLINGA CHA GROUP LINO NDIKUGAWANA MA FILIM A CHICHEWA* a English mutha kuponya ngati muli nawo. Zoyenera kutsatira 👉 *👉 Osatumiza link ya group ina* 👉 _Osatumiza zolaula_ _👉 Osatumiza stickers_ _👉 Osatumiza vn voice recorder_ _👉 Osalowa ku inbox popanda chifukwa chomveka_ *_👉 Machedza ndiololedwa
رابط دعوة موثّق وتفاصيل الأعضاء وخيارات الإعلان على WhatsAd.
*PLEASE ATTETION* 🙏🙏 *Muli bwanj kose Muli mwalandridwa group lino nkhan Nd kugawana malink bas nyimbo,nkhan,chilichose Muno Nd choloredwa kupatula kutukwana Nd zo laula bas* *Nd ma recorder* *Machezaso Muno Nd ororedwa km Chichewa Nd chingerez KT tizane bas* *TIVELANE KM CHINTHU ICH PLZ OSAPONYA KAMBILIMBLI LINK IMOZMOZ KUPONYA KAMOZ ANTHU NGAT AIKONDA ALOWA BAS UKAPEZEKA ROMOVE ZBWANA TIMAKANA MUMUNO*💪 *Mmalo mwa madmn ose Nd ngot MWAKOMA nose*🙏🙏🙏🙏🙏👇👇👇👇🤸🤸
Tigawane ma link""";;; udindo otumiza link muno ndi wa wina aliyense, pemphani ndipo muzapasidwa, ndipo nkhani yathu muno ndi ma link bas zinazo osaponya muno usanafunse uzachitidwa remove, macheza abwino zikomo.
TAKULANDILANI KHALANI OMASUKA CHONDE TSATANI IZI KUTI. MUKHALITSE PAMALO PANO👇👇👇 1. Link ya group Lina ayi🚫 2. Zolaula kuno ayi🚫 3. Zoyambana kutukwana ayi kunyozana ayi🚫 5. Ma voice recorder ayi 🚫 6. Ndiudindo waliyese kuponya filim TIPEZEN ADMIN KUTI TIKUTHANDIZENI ZAMAFILIM OMWE MUKUFUNA👇👇 099130220 Mukafunaso VIP ILIPO MTENGO K2000 AKU JON OR MAYUNITS🙏🏽