FAST MOVIES(SEASONS & FULL MOVIE)
MWALANDIRIDWA KUNO KU FAST MOVIES🙏
CHONDE KHALANI OMASUKA MALAMURO ANTHU ALI MOTERE👇👇
(1)Osaponya link ya group lina ukapezeka❌❌
(2) Osaponya zinthuzi zolaura kapena video ina iliyonse yolaura ukapezeka ❌❌
(3)Osanyozerana zipembezo mukapezeka nonse ❌❌
(4)Kutumiza nyimbo group lino sikololedwa ngakhale ndi pang'ono ukapezeka ❌❌
(5)Kuponya film ndi udindo wa member wina aliyense osasiyira admin yekha,muno timaponyamo ma
_India
_Nigeria
_Action
_catoon
Ukapezeka utaponya zinthu zosiyana ndi zimenezi ❌❌
(6)Khani zaku inbox 📥 osazibweretsa pa group pano ukapezeka ❌❌
(7)Osalowerana ku inbox opezekayo ❌❌
(8)Ngati member satenga nawo gawo kwa ma week awiri remove
(9)Osatumiza voice note ina iliyonse kapena kuyimba call ukapezeka ❌❌
(10) LAMURO LOFUNIKIRA NDI LAKUTI👉Satilani malamuro onse kuti mukhalitse mu group lino.
PRINTED BY ADMINS
ZIKOMO🙏🙏🙏