ابحث في فهرس WhatsAd لمجموعات واتساب للعثور على الأفضل.
نتيجة واحدة في فهرس مجموعات WhatsAd
Ponyani group link
رابط دعوة موثّق وتفاصيل الأعضاء وخيارات الإعلان على WhatsAd.
TAKULNDILANU MUNON NDIPO KHALANI OMASUKA🇲🇼🇲🇼🌽🌽
WELLCOME TO KUPHWETSA MKUTO PA PHWETTE LA MACHEZA GROUP✌✌🏓🗣🤝💪* *~_NGATI ULI SING'ANGA ZIPASILETU ULEMU SOCIAL MEDIA SIMAOPA MAULA_~* *🏓Cholinga cha group lino ndikundikulimbikitsa ubale komaso macheza pajaamati kuyendamkumvina🤝🤝💪* *MALAMULO ATHU ALIMOTELE👇👇👇👇👇* *1🏓Osatumiza link ya group ina muno opezeka remv🚫* *2🏓Mulendo akalowa ayenera kuponya pic komaso kunena komwe amakhala ✅* *3🏓ma VN ( RECORD ⏺️) muno ayi* *4🏓Tiyenela kulemekezana wina ndizake osati kusalana* *5🏓sunday llililose tixikhala ndi pic day ✅* *6🏓Ngat mwalowelana ku inbox zizithera komweko zisafike kuno* *7🏓osaponya zithuz zolaula komaso ma vidios olaula* *8🏓Ma mumbers nose ndinu ololedwa kubwela ndi topic ngat admin sana bweletse* *9🏓onse omangokhala ndwiiiii muno osama commenta zanzake zakolopedwa* *10🏓Muno zandale sitilola komaso kutumiza khani za sing'anga muno ayi🚫🚫🚫* *🗣🗣ndakusokosela mkulinga utamva tsatiran mallamulo kuti tiyendele limozi* *`🤝🤝 MUMODZI MULI PHAMVU BY PANGOLINI` 🦔🦔🦔💥💥💥*