OCHEWA NDI CHIKHALIDWE CHAWO 2
TAKULANDILANI
1~onetsetsani kuti ndinu mchewa.
2~Ponyani MA video aliwose a mchichewa, komaso agule wakulu, kapena aliwose a chikhalidwe. ✅
3~Zolaula, zovula muno ayi°❌
4~osakangana muno, ticheze koma zothandizana, zodziwitsana. ✅
5~zilombo zoyaluka, zikhala ngat munthu muno ayi, 🏹
6~Tisanyozerane chipembedzo,
7~zandale mudziwa kale paja kt akulamula ndi mchewa, ndiye achewa sitinyozana Kuma kulangizana❤🔥
8~tiye nazo I nkhani kathithi kunoooo🎴🎴🎴
9~<>Aliyese akuyenera kutengao mbali muno Osama gowonera chizangala cha anzako..
Wosavera,wosatengapo mbali,, chikolopa