AVAILABLE N TAKING ORDERS🥳🥳 (NAPHY ONLINE SHOPPING GROUP 1)TZ N ZAMBIA ONLY 🩷🩷🩷🥳🥳🥳🥳🔥🔥🔥🔥
Takulandirani ma customer nonse🤗🤗feel free
Muno timakhala ndi katundu wa available komanso taking orders
monga wa ku kitchen, clothes, shoes, handbags, n many more
Admin amakhala ku Karonga kutali timatumiza through post office, ampex courier, speed n bus at customer's cost
Pa chinthu chomwe mwasankha mumalipiliratu
Ngati mukufuna chinthu chomwe sinapange post ndipezeni ku inbox ndi pic ya chinthu chomwe mukufunacho
Order price imayambira zinthu zitatu 💞💕
Enjoy shopping with us 😊
NB:No refund allowed exchange only
Mode of payment
1004108 airtel money code
442825 mpamba code
1007613209 nb account
[contact hidden] fdh acc
Alinafe sikelo Osaiwala screenshot please