HEALTHY HERBAL CARE 3 ☘️
*MALAMULO A HEALTHY HERBS CARE☘️*
*MWALANDILIDWA PANO PA HEALTHY CARE☘️*
Timalisiya group lotsekula ndicholinga choti mudziperekaka Nkhawa/madandaulo anu.
Ngati mukufuna macheza, loweranani ku inbox kuti mudzicheza modekha.
Ufulu otseka kapena kutsekula group ndiwa admin aliyense ngati waona kufunikira kwake
*❤️❤️❤️ Group lino ndilaulere/Losalipiritsa*
Chiyankhulo chamuno ndi *Chichewa* kapena *English*
1️⃣Kutukwanizana,kapena kunyozelana chipembedzo or ntundu wamunthu ndikolesedwa muno. Ukapezeka, *remove*
*2️⃣Ma link amagroup ena*, ma video / ma pic olaura,zandale,zampira tingoti chilichonse chosemphana ndi group lino ndizolesedwa. Ukapezeka *remove*
3️⃣Chonde musabwele ndi vuto loti mukufuna mutaye mimba simuzathandizidwa ife sitipha munthu
4️⃣Ngati mukuona kuti vuto lanu ndilovuta kufotokoza pa group muli ololedwa kubwera kuma inbox athu
5️⃣Pakapezeka oseka kapena onyoza matenda anzache azachosedwa
6️⃣Ngati akufuna thandizo wina akuziwa kapena anasungilako remedy yomwe akufunayo aliyense ali ololedwa kuthandiza nthawi zina ma Doc athu amakhala busy
7️⃣ Ngati mwakonda kutumiza chithuzi/video Clips, fotokozerani (caption) za chomwe mwaponyacho. Izi zimathandiza kuti munthu asankhe kuonera kapena ayi. If not, *remove*
8️⃣ Ngati mwazindikira/mwadzuwitsidwa kuti mwaponya/mwachita zosemphana ndi malamulo, mudzipatsidwa mpata wa 5 minutes kuti muchotse (delete for everyone) apo ayi *remove*
*9️⃣🌹Timakhala busy nthawi zambiri tikamalowa pa group pano timapeza ma massages ambiri oti sitingakwanise kuwapanga follow malingana ndi busy yathu ndiye ngati mwapempha thandidzo koma sunayankhidwe bwelani inbox.*
*🔟🩲👙Kufunsilana muno timaletsa, koma ngati mwakonda kutero,zidzithera kuma inbox komweko ife muno zisatikhudze*
Mukhozanso kudandaula kwa ma admin athu muno for *removal*
1️⃣1️⃣. *No Voice Chat*. Ukapezeka *remove*
*Tiyeni tilemekeze malamulo a group lino chikolopa chisanayende!!!*
Zikomo
*Healthy Herbs Care ☘️*