ابحث في فهرس WhatsAd لمجموعات واتساب للعثور على الأفضل.
حوالي 1 نتيجة (0.42 ثانية)
PLEASE ATETION 🙏🙏🚦🧏♂️🧏♂️🧏♂️🧏♂️🧏♂️ *MWALANDILIDWA MU GROUP LA ZOCHITIKA PA MALAWI [link hidden — subscribe to view] *CHOLINGA CHA GROUP LINO*💪💪 *Cholinga cha group lino ndicho kuphuzisana nd kuziwisana zomwe zachitika madera mwathu kose komwe tili* *Ndpo group lino nd la open member aliyese alindi ufulu otumiza nkhani, ndakatulo, nyimbo,ma vedio ndi zina zambili zokhazo zosaresedwa mu group muno*🙏🙏 *ZOLESEDWA MUNO NDIPO TIVAN APA CHIFUKWA UKANYOZERA UPEZEKA KUNJA*👇👇👇👇👇👇👇👇👇👇 1- *Choyambilila ukalowa kumene muno tumiza picture nd kuzifotokoza komwe umakhara ngati sutelo remove* ❌❌❌ 2- *Osaponya zolaula muno ukapezeka nd remove*❌❌❌❌ 3- *Osaponya malink muno ukapezeka nd remove* ❌❌❌ 4- *Muno simosasila malonda ukapezeka nd remove* ❌❌ 5- *Osanyozerana zipembezo muno ukapezeka nd remove*❌❌❌ *8- *Ma recorder muno ayi kupezeka nd remove* 🚫🚫 6- *Kulowelana ku inbox no permission report kubwera kwa admin nd remove*❌❌❌❌ 7- *Two weeks osatenga mbali or comment nd remove*❌❌❌w3 NDPO KUSWA LAMULO LIMOZ IWE ND WAKUNJA BASI Chonde tiyen titengen mbali kut egroup lanthu likhare lokoma Sunday nd picture day tiziponya ma pic athu tiziziwana kuyenda mkuvina bas Maro mwa admin DESK ndngot mwagona nose💪💪💪 ZOCHITIKA PA MALAWI WOYEEEEEEEE💪💪💪💪💪🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼