ابحث في فهرس WhatsAd لمجموعات واتساب للعثور على الأفضل.
حوالي 1 نتيجة (0.42 ثانية)
*WELCOME TO PHWETE LOSATHA GROUP* 💎💎💎💎💎💎💎💎💎💎💎 *_MALAMULO ALI MOTELE MUNO_* (1️⃣) *Aliyese mulendo akalowa muno akuyenela kuponya picture yake komaso dzina ndikumudzi kwanu* (2️⃣) *Sitilola kuponya links ya group ina muno ukapezeka remove🚮❌* (3️⃣) *Sitilola zinthuzi zolawuula kapena ma video olawula ukapezeka remove❌🚮* (4️⃣) *Sitilola kuponya sticker muno ukapezeka remove ❌🚮* (5️⃣) *Ma voice muno sitilola komas muno simopangila business ukapezeka remove*❌🚮 (6️⃣) *Aliyese osatengapo mbali muno after week mudzienda chikolopa kuyambila (25 message in 22 message out)* (7️⃣) *Osalowa ku inbox popanda chilolezo cha mwini wakeyo, akakupatsa chilolezocho za kuinbox zinthele konko zisafike pa group* (8️⃣) *Kupeza wachikondi nkololedwa ngati mwakondana pitilizani pokwanilitsa maloto Anu* (9️⃣) *Ngati muli ndi wachikondi wanu pa group chezani ndi wina aliyense koma mosapyola malire kupewa phokoso ndi okondedwa anuwo* (🔟) *ngt ndiwe wa nsanje modzi pa uwu wiri wanu akuyanera kutuluka or ayi nonse limodzi* *_Chenjezo_*: _ngati Zachikondi zanu zikubweletsa chisokonezo pa group pano nonse mudzachotsedwa posayang'anira kuti ndindani eve admin_ *Ma program anthu ali motele muno* 👇👇👇👇👇👇👇👇👇👇👇👇👇👇👇👇👇 (1️⃣) *Monday timakhala ndi topic 8:00pm* (2️⃣) *Tuesday timakhala ndi topic 8:00pm* (3️⃣) *Wednesday program ya Miyambi yomwe aliyense amayenera kutenga po gawo 8:00pm* (4️⃣) *Thursday timakhala ndi topic 8:00pm* (5️⃣) *Friday timakhala ndi topic 8:00pm* (6️⃣) *Saturday program ya tikudziweni yomwe tidzikhala tikucheza ndi mulendo 8:00pm* (7️⃣) *Sunday lililonse program ya tidziwane amai ndi abambo yomwe idzikhala pic day (ndiwe okwatila kapena uli single) kwa tsiku lonse* *_tiyeni tilemekezane wina ndi zake tisanyozane🙏🙏🙏_* *Tisanyozelane zipembezo muno* *_Tiyeni malamulo tiwagwilitse tchito kuti Masiku onkhala nafe muno achuluke zikomo_* *Ndiudindo waliyese kutenga nao gawo muno* *_Done_by_administration_panel.com_*......📝📝🤳