CommunitiesAKAKONDANA ALEKENI MIX MACHEZA๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿซต๐Ÿซต๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐ŸŒณ๐ŸŒณ

AKAKONDANA ALEKENI MIX MACHEZA๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿซต๐Ÿซต๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐ŸŒณ๐ŸŒณ

100+ membersYAO

About this community

๐Ÿ’ซ๐Ÿ’ซ๐Ÿ’ซ๐Ÿ’ซ๐Ÿ’ซ๐Ÿ’ซ๐Ÿ’ซ๐Ÿ’ซ๐Ÿ’ซ ๐Ÿ„๐ŸŒณ๐ŸŒณ๐ŸŒณ๐Ÿชต๐Ÿชต๐Ÿชต๐Ÿชต๐ŸŒฒ *WELCOME to AKAKONDANA* *ALEKENI GROUP* *MALAMURO ATHU ALI MOTERE .* 1. *MULENDO CHOYAMBA PONYANI PIC .๐Ÿ‘๐Ÿ‘๐Ÿซ‚๐Ÿซ‚NDI KUNENA KOMWE MUMAKHALA.*๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ 2. *IZI MUNO AI๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡* *( zolawura ayi ,kunyozana zipembezo ayi ma VN ayi ,za asing'anga ayi )๐Ÿ‘* 4. *TIZIKHARA ndi TOPIC MASIKU AWA๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿซ’๐Ÿซ’๐Ÿซ’๐Ÿซ’* *LOREMBA ndi LACHITATU* *:TOPIC DAY* *LACHIWIRI ndi LACINAYI*: *:MCHEZO* ๐Ÿ€๐Ÿ€๐Ÿ€๐Ÿ€ *LACHISANU:MULENDO* ๐ŸŒฟ๐ŸŒฟ๐ŸŒฟ๐ŸŒฟ๐ŸŒฟ *LOWERUKA :TSUTSO(debate)* ๐ŸŒพ๐ŸŒพ๐ŸŒพ๐ŸŒพ๐ŸŒพ *SUNDAY:PIC DAY* ๐Ÿ’ซ๐Ÿชต๐ŸŒณ๐ŸŒณ๐ŸŒณ๐Ÿชด๐Ÿชด๐Ÿ‚๐Ÿ‚๐Ÿ‚ *๐ŸŒณ๐ŸŒณ๐ŸŒณ๐ŸŒณ๐ŸŒณkwa osatenga mbali kwa one week lamuro lidzagwira ntchito remove basiโŒโŒโŒโŒโš ๏ธโš ๏ธโš ๏ธ* . *MAU OTI HULE TIMALETSA MUNO CHONDE UKAPEZEKA REMOVE BASI BCZ AMAYAMBISA PHOKOSO* โ˜„๏ธ๐Ÿชน๐Ÿƒ๐Ÿƒ๐Ÿƒ๐Ÿƒ๐Ÿƒ *OSASAKHANA PA MACEZA PEPHO ZKOMO KWAMBILI ATHU NONSE๐Ÿงจ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ*

YAO
Unlock / View Community

Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.

Related communities

KHANI๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ ZAKUCHIPINDA๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ AND๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ MACHEZA๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ GULUPU

*TAKULANDILANI KUGULUPU LATHU LA KHANI ZAKUCHIPINDA MOTSOGOZEBWA NDINE F KHOZA KAPENA KUTI FRANK KHOZA NYAMATA WAPA MWAZA NDIPO KHALANI OMASUKA CHOLINGA CHA GULUPU LATHU NDIKUFUNA KUPHUZITSANA NDI KUDZIWANA* 1๏ธโƒฃ *NDIPO MALAMULO ATHU ALI MOTELE NGATI MWALOWA KUMENE MUKUYENELA KUPONYA PIK KOMASO DZINA NDI KOMWE MUKUKHLA* 2๏ธโƒฃ *KUPONYA MA VIDEO NDIKWAWIMA ALIYESE OSADIKILA ADAMN OKHA* 3๏ธโƒฃ *KULOWA KU IN BOX KWAMUTHU OPANDA CHILOLEZO* โŒโŒโŒโŒโŒโŒโŒโŒ 4๏ธโƒฃ *KUNYOZANA KAPENA KUTUKWANIZANA SITIMALOLA MUKAPEZEKA PANJA*โŒโŒโŒโŒโŒโŒ 5๏ธโƒฃ *MA Link AMA GULUPU ENA SITIMALOLA MUKAPEZEKA PANJA* โŒโŒโŒโŒโŒโŒ 6๏ธโƒฃ *MA VN SITIMALOLA MUKAPEZEKA PANJA* โŒโŒโŒโŒโŒโŒโŒโŒ 7๏ธโƒฃ *MA STICKER SITIMALOLA MUKAPEZEKA* โŒโŒโŒโŒโŒโŒโŒ 8๏ธโƒฃ *NGATI SIMUKUTENGA MBALI PAMA PROGRAM ATHU MUDZATULUTSIBW 9๏ธโƒฃ *KUTUMIZA MA VIDEO NDIKWAWIMA ALIYESE OSADIKILA ADAMN OKHA* ๐Ÿ”Ÿ ๐ŸŽ„๐ŸŽ„๐ŸŽ„๐ŸŽ„๐ŸŽ„ *Dzina la hule muno sitimalola ukapezeka panja*

1K+ membersNYA

NYIMBO NDI MACHEZA ALL WELCOME ๐Ÿ’ƒ๐Ÿฝ๐Ÿ•บ๐Ÿฝ๐Ÿ’ƒ๐Ÿฝ๐Ÿ•บ๐Ÿฝ

*WELCOME TO NYIMBO NDI MACHEZA*๐ŸŽถ๐ŸŽต๐Ÿ’ƒ๐Ÿผ๐Ÿ•บ๐Ÿป๐Ÿ’ƒ๐Ÿผ๐Ÿ•บ๐Ÿปโค๏ธโค๏ธ *MALAMULOโคต๏ธ* *(1)Mukalowa ponyani chithuzi/photo yanu ndikumene mukukhalira. Komanso kumatengapo mbari muzochitika zathu osangokhara chete๐ŸงŽ๐Ÿป* *(2)Kunyozerana zipembedzo/kunyozana wina ndi mzake sizoloredwa ukapezeka remove.*โŒโŒโŒ *(3)Sitimalora kulankhula, nkhani, zithuzi or ma videos olawura/porno, ukapezeka remove*โŒโŒโŒ *(4)Kutumiza ma audio/VN, stickers AYI ukapezeka remove.*โŒโŒโŒ *(5)Ndi udindo wa aliyense kutumiza nyimbo, mukamatumiza onetsetsani kuti ndi document. Za ma video kumalemba woyimba ndi tittle kupanda kutero remove๐ŸŽถ*โŒโŒโŒ *(6)Sizololedwa kulowerana ku inbox koma ngati mwagwirizana kuti muzicheza ku inbox ndi ufulu wanu komanso ngati mukuwona Kuti mukuvutitsidwa kwambiri muli ndi ufulu kuwuza admin zankhaniyi.* *(7) Ngati munthu wakulowerani ku inbox popanda chilorezo chanu and sizinaku sangalatseni osabweretsa nkhani pa group, mudzatulutsidwa chifukwa zima bweretsa chisokonezo pa group, pitani ku inbox kwa admins adzakuthandizanj.* *(8) Sunday tidzikhara tikuponya chithuzi/pic day kupanda kuponyanawo remove*โŒโŒโŒ *(9)Ndikoletsedwa kuponya ma links amagroups ena komanso a facebook ndi YouTube ukapezeka remove.* *(10) Musana pemphe zondani kaye wanthu pa group pano chikhalidwe or MUSADABWE NYIMBO yanu ikapanda kupatsidwa. Chikhalidwe ndichofunika.* *(11) Zandale muno, mpira kapena kunyoza chipembedzo komanso za malonda kapena a singโ€™anga sizoloredwa or remove*โŒโŒ *(12) Nyimbo zonse zizi pemphedwa pano osati ku inbox or mudzatulutsidwa* *(13) Chilankhulo muno ndi Chichewa ndi Chizungu basi.* *(14) Ngati member wa kulowerani ku inbox popanda chilorezo chanu and simuna sangalare nanzo wunzani admin straight osadikira kuti pathe week/ma week chifukwa zimabvuta kupanga sort out nkhaniyo komanso muzibweretsa ndi umboni kwa admins kuti admins athe kuyendetsa nkhani yo bwino.* *(15)Tiyeni titsatire malamuro tonse Kuti nthawi ndimatsiku okhala muno achuluke* *KHALANI OMASUKA KOMANSO KUTENGAPO MBALI MU ZOCHITIKA ZATHU* *By admin* ๐Ÿ’ƒ๐Ÿฝ๐Ÿ•บ๐Ÿฝโค๏ธ

900+ membersNYA

MACHEZA AND LOVE GROUP ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ™‹๐Ÿ’ƒ๐Ÿ’ƒ๐Ÿ’ž๐Ÿ’ž๐Ÿ’ž๐Ÿคธ๐Ÿคธ๐Ÿƒ

๐ŸŒน๐ŸŒน๐ŸŒน WELCOME TO MACHEZA AND LOVE GROUP ๐ŸŒน๐ŸŒน๐ŸŒน ๐Ÿ˜๐Ÿ˜ CHOLINGA CHA GROUP LA THULI NDI KUPHUZINSANA KOMASO KUTHANDIZANA MAGANIZO PAZOMWE ACHINYAMATA IFE TIKUKUMANA NAZO PAMOYO WATHU WA TSIKU NDI ๐Ÿ˜๐Ÿ˜๐Ÿ˜ (1) MULENDO ALIYENSE AKUYENERA KUPONYA PIC KUTI ATHU AKUZIWENI OSAPONYAYO ๐Ÿšฎ๐Ÿšฎ๐Ÿšฎ๐Ÿšฎ ๐Ÿฅฐ ๐Ÿฅฐ๐Ÿฅฐ๐Ÿฅฐ (2) MUTHU ALIYENSE AKUYENERA KULEMEKEZA MAGANIZO AZANU KOMASO MA ADMIN KUKUYENERA KUSATA MA LAMULO OSASATIRA MALAMULO ๐Ÿšฎ๐Ÿšฎ๐Ÿšฎ๐Ÿšฎ๐Ÿšฎ (3) ALIYENSE AKUYENERA KUTENGAPO GAWO PAZOCHITIKA ZAPA GROUP PANO OSATENGA NAWO GAWO ๐Ÿšฎ๐Ÿšฎ๐Ÿšฎ (4) KUTUMIZA MA VIDEO, MA PHOTO KOMASO MA STICKER OLAULA MUNO AI OPEZEKA ๐Ÿšฎ๐Ÿšฎ๐Ÿšฎ๐Ÿšฎ๐Ÿšฎ (5) ZONYOZANA MUNO AI OPEZEKA ๐Ÿšฎ๐Ÿšฎ๐Ÿšฎ๐Ÿšฎ (6) ๐Ÿฅฐ๐Ÿฅฐ๐Ÿฅฐ๐ŸฅฐSUNDAY LILILONSE TIMAKHARA NDI PIC DAY ALIYENSE AKUYENERA KUPONYA OSAPONYAYO ๐Ÿšฎ๐Ÿšฎ๐Ÿšฎ๐Ÿšฎ (7)๐ŸŒน๐ŸŒน๐ŸŒน๐ŸŒน๐Ÿฅฐ๐Ÿฅฐ MUTHU AKAKULOWERANI KU INBOX ZIZITHERA KOMWEKO SIMUKUYENERA KUBWERA NAZO PA GROUP PANO KAPENA NGAT MWAPEZA VUTO MUPEZENI ADMIN ALIYENSE AZAKUTHANDIZA ๐Ÿ‘๐Ÿ‘๐Ÿ‘๐Ÿ‘ (8) ๐ŸŒน๐ŸŒน๐ŸŒน๐ŸŒนTIMAKHARA NDI MA PROGRAM PA GROUP PANO ALIYENSE AKUYENERA KUTENGAPO GAWO PAZOCHITIKA ZAPA GROUP PANO OSATENGA NAWO GAWO ๐Ÿšฎ๐Ÿšฎ๐Ÿšฎ๐Ÿšฎ NOTICE: ALIYENSE OSASATIRA MALAMULO PA GROUP PANO ADZACHOTSEDWA THAWI YOMWEYO๐Ÿคช๐Ÿคช๐Ÿคช๐Ÿคช ๐Ÿฅฐ๐Ÿฅฐ๐Ÿฅฐ๐Ÿฅฐ๐Ÿฅฐ๐ŸŒน๐ŸŒน๐ŸŒน๐ŸŒน๐ŸŒนโค๏ธโค๏ธโค๏ธโค๏ธโค๏ธ THANK YOU ๐Ÿ’•๐Ÿ’•๐Ÿ’•๐Ÿ’•๐Ÿ’•๐ŸŒน๐ŸŒน๐ŸŒน๐ŸŒน๐Ÿ’ฅ๐Ÿ’ฅ๐Ÿ’ฅ๐Ÿ’ฅ๐Ÿ’ฅ๐Ÿ’ฅ

800+ membersRMN

MACHEZA ALIONSE GROUP MWANACHE

MWANACHE SUMAILA GROUP group yi ndiya business zili ndinu kukhala kapena kupanga left, mwalandilidwa muno sitiponya ma bm kwamene akufuna inbox km akhale kut ali ndi OTT kapena 1vocha tikutumizilen ku inbox kwanu pogwilitsa ntchito bundle yanuyo zikom kwamene muli ku malaw tumizani ndalam pa number iy 0997756879 NDIPO mupangidwa add ku group ya VIP kut muzilandila mapono aulele komanso group yo SIMATSEKEDWA 24HRS mukadikira zaulele nde muzingoona ma short omweo sinanga zinthuzi timagwirisa ntchito bundle potumiza nde kwamene ali LEDE ATHA kundipeza inbox mukadikira zaulele nde muzingoona ma short omweo sinanga zinthuzi timagwirisa ntchito bundle potumiza nde gulani vocha ndipo mupangidwa add ku group ya VIP kut muzilandila mapono aulele komanso. ndondomeko ili motele ku malaw kukutumiziran ku inbox kwanu ndi K1500 malile data yanu ithe kukupangan add ku VIP ndk2000 ku South African kukutumiziran ku inbox kwanu ndi R10 kukupangan add ku VIP ndi R20 zikom

800+ membersActive this monthNYA

Macheza aku chipinda๐Ÿ‘๐ŸŒ

๐“๐š๐ค๐ฎ๐ฅ๐š๐ง๐๐ข๐ฅ๐š๐ง๐ข ๐ง๐จ๐ง๐ฌ๐ž ๐Œ๐€๐‚๐‡๐„๐™๐€ ๐€๐Š๐”๐‚๐‡๐ˆ๐๐ˆ๐๐ƒ๐€ ๐Ÿ‘๐ŸŒ ๐Ÿค๐Ÿค๐Ÿค Ngati ndiwe mlendo tumiza picture anthu akuziwe komaso komwe umakhala. ๐”ธ๐•๐•š๐•ช๐•–๐•ค๐•– ๐•’๐•๐•š ๐•Ÿ๐••๐•š ๐•ฆ๐•—๐•ฆ๐•๐•ฆ ๐• ๐•œ๐•™๐•’๐•๐•’ ๐•ž๐•ฆ๐•Ÿ๐•  ๐•œ๐•’๐•ก๐•–๐•Ÿ๐•’ ๐•œ๐•ฆ๐•ก๐•’๐•Ÿ๐•˜๐•’ ๐•๐•–๐•—๐•ฅ ๐•ค๐•š๐•ฅ๐•š๐•œ๐•’๐•œ๐•’๐•ž๐•š๐•ซ๐•’ ๐•ž๐•ฆ๐•Ÿ๐•ฅ๐•™๐•ฆ 1. Voice note โœ… 2. Sticker's โœ… 3. Kucheza โœ… 4. Zaku *INBOX* ๐Ÿ“ฅ *ZIZITHERA KONKO* Ngati zavuta pezani admin akuthandizeni ๐Ÿšฎ *Azimai.* ๐Ÿƒ๐ŸŒน.. Ngati mwamuna akukuvutitsani Ku inbox pangani screenshot Ku group anthu timuziwe ayaluke. _Mulibe Mwana muno aliyese chomwe akupanga akuchiziwa_ . 5. Ma Link ๐Ÿ–‡๏ธ ena Muno ayi ukapezeka remove akusata.๐Ÿšฎ 6. *Sunday ndi pic day* = Kuzikhalaso voice Chart = Aliyese akhoza Kuyambisa *NTHAWI*: *_6Am_ to* *_10Pm_* โ›ฝALIYESE OSATENGA MBALI MU GROUP remove amayenda.. mothamangila nthawi๐Ÿ’Š ๐•‹๐• ๐•Ÿ๐•ค๐•– ๐•‹๐•š๐•๐•š ๐•Ÿ๐••๐•š ๐•ฆ๐••๐•š๐•Ÿ๐••๐•  ๐•จ๐• ๐•ฅ๐•™๐•’๐•Ÿ๐••๐•š๐•ซ๐•’ ๐•œ๐•ฆ๐•ฅ ๐•˜๐•ฃ๐• ๐•ฆ๐•ก ๐•๐•š๐•ซ๐•š๐•œ๐• ๐•ž๐•’ ๐•ก๐• ๐•ฅ๐•–๐•Ÿ๐•˜๐•’ ๐•ž๐•“๐•’๐•๐•š ๐•Ÿ๐•ฅ๐•™๐•’๐•จ๐•š ๐•ซ๐• ๐•Ÿ๐•ค๐•–. *NOTE* MALAMULO AGROUP AMASITHIDWA PAKADUTSA NTHAWI FROM: _ADMIN DESK_๐Ÿ™

700+ membersActive this monthNYA

ZAKUCHIPINDA AND MACHEZA GROUP ๐Ÿ’•โฃ๏ธ๐Ÿ’–๐Ÿ’

*WELCOME TO =* *ZAKUCHIPINDA ZENIZENI GROUP๐Ÿ“๐Ÿ“๐Ÿ“๐Ÿ“๐Ÿ“๐Ÿ“๐Ÿ“๐Ÿ“๐Ÿ“๐Ÿ“๐Ÿ“๐Ÿ“* *TAKULANDILANI MALAMULO NDI AWA๐Ÿ‘‡๐Ÿป๐Ÿ‘‡๐Ÿป๐Ÿ‘‡๐Ÿป๐Ÿ‘‡๐Ÿป* *1.....MUKALOWA KUMENE MUKUYENELA KUPONYA PIC YANU NDI KUZIFOTOKOZA KOMWE MUMAKHALA ANTHU AKUDZIWENI๐ŸŒพ๐ŸŒพ๐ŸŒพ๐ŸŒพ๐ŸŒพ๐ŸŒพ๐ŸŒพ๐ŸŒพ* *2..... SITILOLA VN ZASING'ANGA AYI KOMASO MA STICKER AI MUNO ๐Ÿ‘‰ UKAPEZEKA REMOVE๐ŸŒบ๐ŸŒบ๐ŸŒบ๐ŸŒบ๐ŸŒบ๐ŸŒบ๐ŸŒบ๐ŸŒบ๐ŸŒบ๐ŸŒบ๐ŸŒบ๐ŸŒบ* *3..... SUNDAY LILILONSE TIMAKHALA NDI PIC DAY๐Ÿฅ€๐Ÿฅ€๐Ÿฅ€๐Ÿฅ€๐Ÿฅ€๐Ÿฅ€๐Ÿฅ€๐Ÿฅ€๐Ÿฅ€๐Ÿฅ€๐Ÿฅ€๐Ÿฅ€* *4..... WOSATENGA NAWO GAWO MUZOCHITIKA REMOVE๐Ÿชป๐Ÿชป๐Ÿชป๐Ÿชป๐Ÿชป๐Ÿชป๐Ÿชป๐Ÿชป๐Ÿชป๐Ÿชป๐Ÿชป๐Ÿชป* *5..... TIMALOLA KUPONYA VIDEO OR PIC YOKHUDZANA NDIZOMWE ZIMACHITIKA KUCHIPINDA KOMA MA VIDEO ACHISAWAWA SITILOLA AYIโ›บโ›บโ›บโ›บโ›บโ›บโ›บโ›บโ›บโ›บ* *6..... ALIYENSE ALI NDI UFULU OPONYA MA VIDEO OKHUDZANA NZAKUCHIPINDA KUPONYA MA VIDEO MKWALIYENSE๐Ÿ“ฟ๐Ÿ“ฟ๐Ÿ“ฟ๐Ÿ“ฟ๐Ÿ“ฟ๐Ÿ“ฟ๐Ÿ“ฟ๐Ÿ“ฟ๐Ÿ“ฟ๐Ÿ“ฟ* *7.....ZAKU INBOX KONKO ZISAFIKE PA GROUP PANO๐Ÿฅˆ๐Ÿฅˆ๐Ÿฅˆ๐Ÿฅˆ๐Ÿฅˆ๐Ÿฅˆ๐Ÿฅˆ๐Ÿฅˆ๐Ÿฅˆ๐Ÿฅˆ* *8..... SITILOLA KUNYOZELANA MTUNDU TONSE NDIFE AMODZI KUCHENZA MOSANKHANA AYI KUNYOZELANA ZIPEMBEDZO AYI SITILOLA๐Ÿ’“๐Ÿ’“๐Ÿ’“๐Ÿ’“๐Ÿ’“๐Ÿ’“๐Ÿ’“๐Ÿ’“* *KUKHALA BEST ACTIVE MEMBER NDIKUMATENGA MBALI MUMA PROGRAM ATHU KOMANSO KUMACHENZA NDALIYENSE๐Ÿ’š๐Ÿ’š๐Ÿ’š๐Ÿ’š๐Ÿ’š๐Ÿ’š๐Ÿ’š๐Ÿ’š๐Ÿ’š๐Ÿ’š๐Ÿ’š๐Ÿ’š* *MUKAFUNA KUKHALITSA MUNO TSATILANI MALAMULOWA ZIKOMO TIMAKUNYADILANI NONSE๐Ÿค๐Ÿค๐Ÿค๐Ÿค๐Ÿค๐Ÿค๐Ÿ™๐Ÿ™๐Ÿ™๐Ÿ™๐Ÿ™๐Ÿ™๐Ÿคธโ€โ™€๏ธ๐Ÿคธโ€โ™€๏ธ๐Ÿคธโ€โ™€๏ธ๐Ÿคธโ€โ™€๏ธ๐Ÿคธโ€โ™€๏ธ๐Ÿคธโ€โ™€๏ธ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ*

700+ membersSNA