CommunitiesAKILA AND DAT V DENMARK MBAMBANDE MOVES

AKILA AND DAT V DENMARK MBAMBANDE MOVES

600+ membersBUM

About this community

MULI OLANDILIDWA NDIPO KHALANI OMASUKA KOMA IFE MA ADMINI TIMAKHALA NDIMA CONDITIONS AMENE MUKUYENELA KUWASATA MONGA NGATI MA MEMBERS A GROUP LINO 1 osapanga send link ina iliyonse pa group kupatula la group lino 2 tikakhala ndizochita pano pa group ngati pic day komaso ndi zina zambili ngati simukutenga nawo gawo asala yake ndi remove 3 osapanga send zithuz zolawula kapena video 📹 yolawula 4 ma recording saloledwa pano 5 voice chat kapena kuti call sizoloredwa 6 osapanga send sticker iliyonse 7 member aliyese akuyenera kukhala ndima message opitilira 10 patsiku 8 anthu omwe simukufuna kukhala pano khomo ndilotsekula mukhoza kutuluka 9 zako ngati akuyambisa mapokoso kapena akukutukwana musabweze chifukwa mukatelo mukhala limodzi pa ulendo 10 khalani anthu okondana ngati ndife amalawi tokhatokha 11 matumizidwe amafilm ngati film yatumizidwa osayibwelezaso 12 ngati muli ndi number yomwe ikufunika kupanga add tumizani ndipo ipangidwa add GROUPULI LIMALAMULIDWA NDI ANTHU AWA OYAMBA DESMOND WACHIWIRI MR PEACE WACHITATU SHONGA WACHINAYI ASIFA WACHI NUMBER 5 LAMIN YAMAL. NGATI PALI VUTO APEZENI ATHU AMENEWO AKUTHANDIZANI NDINE WANUWANU DESMOND DMINI 🙏🙏🙏

BUM
Unlock / View Community

Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.

Related communities

CHICHEWA MOVIE MBAMBANDE 2

WELCOME TO G2💥MOVlES lNTlME🙏🔥🔥 1. NO CRiP. ❌ 2 .NO VN/AUD. ❌ 3 .NO STlCK. ❌ 4 .NO PORN. ❌ 5 .NO MlKANGANO. ❌ 6 .NO BUSlNESS. ❌ 7 .NO PlCTURES. ❌ 8 .NO OTHERLlNK❌ 9 .OSALOWELANA INBOX KOPANDA CHlLOLEZO UKUPEZEKA REMOVE❌ Cholinga chagrou plinondikugawana ma fIlim, mulindi ufulu opepha fIlim kapenakutumiza fIlim , aliyese akuyenelakutenga Mbali kuti apeze fIlimmosavuta, satani malamulo kutimukhalise muno I THlNK NDALlZA. by SlMPLE MAN📝✍️✍️ 100%

900+ membersActive this monthYAO

INTERNATIONAL 🅨︎🅐︎ AKILA MOVIES 🔥🔥

NGATI MUFUNA KULANDILA MA FILM MWACHANGU TIYAKHULENI INBOX CHIFUKWA MUNO TINASIYA KUPONYA MA FILM KOMA TILI NDI GROUP LOMWE TIKUPONYA MA FILM TIPEZENI KUTI MULIPIRE NDIKULOWETSENI KU GROUP #MY NUMBER [contact hidden] NGATI MUKUFUNA MA FILM TIPEZENI 🔥🔥🔥

900+ membersSCO

AKILA ENTERTAINMENT YA MA MOVIE'S 🎬 🎞

NGATI MUKUFUNA KULANDILA MA FILM MWACHANGU TIYAKHULENI INBOX CHIFUKWA MUNO TINASIYA KUPONYA MA FILM KOMA TILI NDI GROUP LOMWE TIKUPONYA MA FILM TIPEZENI KUTI MULIPIRE NDIKULOWETSENI KU GROUP #MY NUMBER [contact hidden] NGATI MUKUFUNA MA FILM TIPEZENI 🔥🔥🔥🦅

800+ membersBUM

AKILA ENTERTAINMENT'

*WELCOME EVERYONE* ↪️ Pano ma movie ndi nyanja muchita kutopa nawo chofunika ndikukhara permanent member koma ngati mungafune palinso option yopeleka nsonkho per fortnite nde ngati mwavomeleza zokhara permanent member musavutike na ngati muli ku Malawi ponyani K15,000 ku ma number awa 0996239430 kapena 0886050940 onsewo amalemba kuti Kelvin Moffat nsonkho umenewu mutha kuponya half inayo nkumaliza mwenzi winawo nzothekanso and; ↪️ Don't forget mukaponya nsonkho wanu kubwera inbox kuti ndikulembeni pa list koma ngati muli ku South Africa musavutikenso gulani R100 airtime telkom nde mujambure nkutumiza inbox yanga and apanso mutha kuponya kaye half inayo nkumaliza the following month mukatero ndekuti mwakhara member okhazikika ndipo simudzachotsedwanso pa group pano mpaka kare and ngati mukufuna kupeleka per fortnite ndi K2000 ngati muli ku Malawi koma ngati muli ku South Africa ndi R20 Telkom Airtime after every two weeks ngati simunagwilizane ndi malamulowa the door is open sure.

800+ membersNYA

AKILA ENTERTAINMENT 🖥️💻

TAKULANDILANI NONSE MA MEMBERS TIYENI TIGAWANE MA MOVIES A CHICHEWA

700+ membersYAO

LETEST INDIA YA MA COVER MBAMBANDE

INDIA YA MA COVER MBAMBANDE ALENDO NONSE NDINU OLANDILIDWA NDIPO KHALANI OMASUKA PA MUNZI PANO MALAMULO ALI MOTE 1NO MIKANGANO ❌❌ 2 NO OTHER LINKS ❌❌ 3 NO PORN ❌❌❌❌❌ 4 NO STICKS ❌❌ 5 NO VN/AUD❌❌ 6 NO BUSINESS ❌❌ 7 NO PICTURES ❌❌ 8 NO CRIP❌❌❌ ZOYENERA KUCHITA 9 NDI UDINDO WA ALIYESE KUPONYA MA FILIMU OMWE ALINAWO OSAYEMBEKEZA ADMIN OKHA AYI 10 MUNOMO SIMONGOKHALIRA KUPEMPHA AYI NAWENSO UZIPONYA MA FILIMU 11 NGATI MUNZATHU WAPEMPHA FILIMU NDI UDINDO WA ALIYESE KUMUPONYERA DZIKOMO POKHARA M'MONZI MWA IFE MWAKOMA NONSEINDIA YA MA COVER MBAMBANDE ALENDO NONSE NDINU OLANDILIDWA NDIPO KHALANI OMASUKA PA MUNZI PANO MALAMULO ALI MOTE 1NO MIKANGANO ❌❌ 2 NO OTHER LINKS ❌❌ 3 NO PORN ❌❌❌❌❌ 4 NO STICKS ❌❌ 5 NO VN/AUD❌❌ 6 NO BUSINESS ❌❌ 7 NO PICTURES ❌❌ 8 NO CRIP❌❌❌ ZOYENERA KUCHITA 9 NDI UDINDO WA ALIYESE KUPONYA MA FILIMU OMWE ALINAWO OSAYEMBEKEZA ADMIN OKHA AYI 10 MUNOMO SIMONGOKHALIRA KUPEMPHA AYI NAWENSO UZIPONYA MA FILIMU 11 NGATI MUNZATHU WAPEMPHA FILIMU NDI UDINDO WA ALIYESE KUMUPONYERA DZIKOMO POKHARA M'MONZI MWA IFE MWAKOMA NONSE

600+ membersKNG