BAKILI MULUZI TV 2 πΊπ‘
*BAKILI MULUZI TV 2 πΊπ‘* GROUP
πΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊ
MALAMULO ALI MOTELE
*(1) OSAPONYA LINKββββ YA GROUP INA MUNO UKAPEZEKA UTULUSIDWA TIFUTASO LINK WAPONYAYO POMWEPO*
πΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊ
*BAKILI MULUZI TV*
*(2) OSANYOZANA MUNO MITUNDU KOMASO ZIPEMBEZO*
πΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊ
*BAKILI MULUZI TV*
*(3) OSAPONYA ZOLAULAβββββββ MUNO*
πΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊ
*BAKILI MULUZI TV*
*(4) MUNO KHAN TIKUFUNA ZOKOZA MALAWI OSATI KUMAYAMIKILA BOMA POMWE LIKUPANGA ZOSAUKISA MALAWI IFE A BAKILI MULUZI TV SITIKHALA CHETE MPAKA MALAWI AZAPEZE UFULO ZIKO LATHU LINO*
πΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊ
*BAKILI MULUZI TV*
*(5) NDI UDINDO WA ALIYESE KUPONYA KHAN MUNO POSADIKI MA DIMIN*
πΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊ
*BAKILI MULUZI TV*
*(6) TIKHAKE AMALAWI OKONDANA NDI OLEMEKEZANA WINA NDIMZAKE KUTI ZIKO LATHU LIKHALE LOSOGOLA CHIFUKWA CHIKONDI NDICHOMano liga me aqui AndrΓ© CHUMA*.
πΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊ
BAKILI MULUZI TVCHIYAMBI KOMASO MATHERO A ULAMULIRO WA CHISLAM ( Islamic State) part 2
Kumwalira kwa Umar kudali mathero a ulamuliro wake mu 644CE
Council kapena kuti akuluakulu adakhalirana pansi ndikusankha dzina la Uthman Ibn Affaan kukhala mulowa M'malo mwa Umar mu Chaka Cha 644CE
Ngakhale kuti Uthman adakhala mtsogoleri wa wa asilaam , anthu ena chapasipasi sizidawasangalase kuti Uthman akhale mtsogoleri wa asilaam , koma Iwo amafuna Ali ibn Abu Talib .
Uthman adakhala pa udindo kuyambira mchaka Cha 644 mpaka mu 656 , mwachidule adakhala mtsogoleri Kwa zaka 12
Uthman Ali pa utsogoleri adapanga zitunukuko izi ;
Adasonkhanisa Quran kukhala Buku limodzi , poyamba Quran asilaam amayisunga Mutu ( amayiloweza ) ndiye Uthman pokhala mtsogoleri wa asilaam zidayamba kumupasa mantha kuti tsiku lina anthu amene adaloweza Quran azatha ndikufa ndiye Quran izasowa , kenako adabwera ndi maganizo osonkhanisa Quran yonse mu buku kuti isungike mpaka kalekale kumibado .
Uthman ndi amene adakulisa dziko la chislam ( Islamic State) kukafika mpaka ku mpoto Kwa Africa ( north Africa) komaso chagawo chotchedwa Armenia
Uthman adakhazikisa ch GROUPπΊπΊπΊπΊπΊπΊπ‘π‘π‘π‘π‘π‘π‘π‘π‘π‘π‘π‘π‘π‘π‘π‘πΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊπΊ