BIG BRAINS 2025☂️☂️

100+ membersTPI

About this community

MALAMULO AGULU Poyamba BIG BRAINS 2025 ndi gulu landale lomwe limabweretsa pamodzi anthu onse okonda zipani zosiyanasiyana kuti akambirane nkhani zandale molemekezana. Ndikugwira ntchito za zipani zawo potsata malamulo achipani. Malamulo oyendetsera gulu: 1. Titumize nkhani zokhuzana ndi ndale basi mu chiyankhulo cha chingerezi kapena chichewa basi 2. Kunyozana kapena kunyozerana mitundu, chikhalidwe ndi zipembedzo nkosaloledwa 3. Kutumiza ma link amagulu ena nkosaloledwa 4. Osasintha chithunzi choyimilira gulu kapena dzina lagulu popanda chilolezo kuchoka ku ma admin 5. Admin wina aliyense Ali ndi mphanvu zochotsa kapena kuika membera pa gulu lino. 6. Tsankho kuchoka kwa ma admin kapena membala aliyense nkosaloledwa 7.Zikadziwika kuti nkhani yomwe membala waponya ndiyabodza membara ayenera kuyichotsa kapena kupepesa 8. Membala adzabwezeretsedwa ndi admin yemwe anamuchotsa. 9. Mamembala onse ndi olimbikitsidwa kutenga nawo gawo pa zokambirana za gulu lino. Zilango Zilango kwaolakwira malamulo zizapelekedwa ndi ma admin potengera kukula kwa nkhani komanso kupalamulapalamula kwa olakwayo Zikomo

TPI
Unlock / View Community

Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.

Related communities

GRACE EXQUISITE TUTORIAL 2026 BRAINSTORMING GROUP 1⃣

*WELCOME TO GRACE EXQUISITE TUTORIAL'S 2026 BRAINSTORMING GROUP 1! 🚀* *Grace Exquisite Tutorials – Group Rules 📌* Please read and follow these to keep the group focused and respectful: 1. *Respect* everyone - admins and students. 2. *No bullying, insults, or bad language.* 3. *No distractions* during class. Keep chats on topic. 4. *No external links, forwards, or voice calls* without admin permission. 5. *Be active in class.* No ghost learning. 6. *No slandering* Grace Exquisite Tutorials. 7. *No religious, tribal, or social arguments.* We’re here to learn. 8. *Don’t share personal details* of yourself or others. 9. *No cheating or plagiarism* in assignments and tests. 10. *Inform an admin* if you’ll be absent or late. 11. *Submit assignments* only in the specified format/channel and before the deadline. Late work may not be accepted. 12. *Use English* in the main group unless told otherwise. 13. *Only share class-related files, images, and voice notes.* No memes, forwards, or unrelated media. 14. *Admin decisions are final* in the group. For complaints, DM an admin privately. 15. *This group is for academics only.* Keep social chats out. *Consequences:* Breaking any rule = warning, mute, or removal. Serious or repeated violations will disqualify you from rewards. *JOIN GROUP NOW 🇬🇧* [link hidden — subscribe to view]

500+ membersAFR

💡BRAINSTORMERS💡

Қатыып қалған правила жокшщс❗️ Нам абсолютно Поох^й❗️🏳️ Админ адам коссандаа берылмейды❗️ Кірген соң шығасыңдарма үндемей шығыңдар кім қосты деп зерттемей нах❗️ КЫРЫЛГАНДАР сразу ушады❗️ Шыгатын болсандар кырмендер❗️

100+ membersKAZ

JAMB brainstorm 🧘

*Monday:* Chemistry *Tuesday:* Biology *Wednesday:* Physics *Thursday:* English *Friday:* JAMB chosen novel *Saturday:* Prep JAMB exam on all 4 subject. *Sunday:* Mindset building,Chillax, try a hobby, rest body, mind, heart and soul. Any difficulties from the week can brought forte.

51 membersEnglish