*MALAMULO ATHU MUNO MU BULLETS MANOMA SILVER ๐ฅ ZAMASEWERO* โฝโฝโฝ (1) alendo khalani omasuka potenga nawo mbali mu zochitika za group lino (2) *timakamba nkhani zokhuza mpira 95% zakunja kwa mpira 5%* (3) 99% zilankhulo zovomerezeka chichewa English 1% zilankhulo zina (4) *sitimalola kupanga recode kuponya ma link ama group ena ndi ma sticks ena ali onse muno* (5) matsiku ena timakhala ndi ma program monga Monday timakhala ndi mulendo wathu Friday top 20 munthawiyi sitimalola munthu kuponyapo nkhani zakunja kwa program yo mukagotero remove pompo pompo (6) *kusalana kapena kusankhana pa group chifukwa chosiyana zipembezo kapenanso mitundu nkolesedwa* (7) member yemwe sanalowe nawo mu top 20 kwa 2weeks kapena osakwanisako 30 messages adzachotsedwa (8) *tiyeni tipasane ndi kusungilana ulemu polankhula komanso pano sipopezera mkazi / mamuna chonde guys anthufe ndife akulu akulu komanso ndife pachibale za pa group zizithera pa group pompano* (9) group lino sitimalola kubweresa ma update onama pano ukangopezeka pompo pompo remove (10) *ma dmin athu nawonso ndi anthu ali ndi kufooka kwawo ngati alankhula china chake chosakhala bwino ndi ufulu wa member wina aliyense kuzuzura mwaulemu osati monyoza ayi* (11) ma dmin athu samatulutsa munthu mopanda chifukwa ziwani kuti mukangotulutsidwa simuzapangidwanso add ndiye chonde osamabwera ku in box kwa admin *mukangosunga zomwe mwauzidwa panozi ziwani kuti mukhalitsa muno mpaka kale* mphavu nyerere ๐๐๐๐๐ญ๐ณ๐ญ๐ณ๐ญ๐ณ๐ญ๐ณ mphavu bullets ๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฆ๐น mphave silver ๐ฆ๐ท๐ฆ๐ท๐ฆ๐ท๐ฆ๐ท *umodzi pa machedza* ๐คธโโ๐คธโโ๐คธโโ๐คธโโ๐คธโโ
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
MALAMULO ATHU ALI MOTERE PA GROUP PANO๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ๐ฅณ๐ฅณ๐ฅณ๐ฅณ๐ฅณ๐ฅณ๐ซ ๐ซ ๐ฅณ (1)Sitilora kutumiza ma links ena Muno ukapezeka remove ๐ก๐ก (2)Muno kutumiza nkhani za spots 90% macheza 10% (3)Ndi udindo WA aliyense kutumiza sports osadikira adimin okha okha komanso wa (0 )comment azapangidwa remove (4)Muno ma vn, ma porno,zandale ,zachipembedzo ,ma stickers,timaletsa only sports bas (5)Za ku inbox zithere komko zisafike pa group pano yemwe azapezeke remove (6)
WELCOME TO FCB NYASA BIG 2๏ธโฃ0๏ธโฃ2๏ธโฃ5๏ธโฃ SUPPORTERS GROUP NDIPO MALAMULO ATHU ALI MOTEREโฌ๏ธโฌ๏ธโฌ๏ธ 1๏ธโฃ TIKONDANE WINA NDI MZAKE TOSE NDIFE BANJA LIMODZI MONGA MAPALE 2๏ธโฃOSAMASANKHANA MITINDU KAPENA CHIPEMBEZO 3๏ธโฃ NDI UDINDO WA WINA ALIYETSE KUTUMIDZA UPDATE PA GROUP PANO 4๏ธโฃ NO PORNO VIDEO OR PHOTO( ZITHUZ KAPENA MA VIDEO OLAURA MUNO AYI NDI ZOLETSEDWA 5๏ธโฃ OSAMAPONYA LINK YA GROUP LINA MUNO 6๏ธโฃ OSAMAPONYA MA STICKER MUNO 7๏ธโฃ NO VN MUNO POKHA POKHA ITAKHALA SPORTS 8๏ธโฃ WINA ALIYETSE AZITENGA MBALI MKAKHALA 1 WEEEK OSATENGA MBALI MZATULUSIDWA 9๏ธโฃ OSAMANYOZANA ๐ NKHAN ZA PA GROUP PANO ZIZIKHALA 90% ZA MPIRA MBALI INAYO TIKHOZA KUMACHEZALO DZINA 1๏ธโฃ1๏ธโฃ ZA NDALE MUNO AYI UKAPEZEKA REMOVE 1๏ธโฃ2๏ธโฃ NKHAN ZA GROUP PANO ZIZITHERA POMPANO NOT KU INBOX 1๏ธโฃ3๏ธโฃ MKAPEZA VUTO PITANI KU INBOX KWA ADMIN NDIPO TSATILAN MALAMULO ZIKOMO *BY ADMIN MUNSA ENTERTAINMENT ๐๐๐๐
To join our newsgroup go to the below link and be fully informed of what is really happening in Israel and the World. [link hidden โ subscribe to view]?mode=ac_t
NBB๐ฆ๐น๐ฆ๐นNOMA๐ช๐บ๐ช๐บSILVER STRIKERS๐ง๐ผ๐ง๐ผ Takulandilan ku group la masapota ampira okonda ma team awo mwamtendere. Muno timalimbikisa kukondana wina ndi mzake osat mikangano koma macheza okhuza mpira bas. Ochilimika kuponya nkhan pazikhakala mwayi wa mphoto ya ma bundle a internet *Malamulo agroup lino* Zolesedwa 1.osaponya link la group Lina โโโโukatero remove 2.osaponya chilichonse choonesa kulaulaโโโโukatero remove 3.osachula maina oyambisa mikangano muno monga:kapado/nkhumba fc,chingambwe fc,nyau fcโโโโ ukapezeka remove. 4.osaponya ma sticker,voice note,kutukwanaโโโโUkapezeka remove 5.siku la mpira(match day)ndi siku longoponya ma updade osasakaniza nkhan kupereka mpata kwa mamembala kusatira mpira. 6.kupereka update yabodzaโโโโ Ukapezeka remove 7.kusakhala active kwa 2weeksโโโโremove 8.Ili ndi group la za mpira only osatumiza zosemphana ndi mpira monga za ndale,nkhan osat zampiraโโโโukapezeka remove 9.ukalowa pa chat kukakhala game tiziyesesa kusatila mamessage omwe atizidwa kale kut tione mmene ma results mmene akuyendera kupewa mafunso ot game ikuyenda bwanji,wagolesa ndan,zikutha bwanji,izi zimapwetekesa omwe amuluza. 11.oyambisa chisokonezo munoโโโโremove *Kutumiza nkhan ndi kwa aliyense osadikilira ma admin okha* Ngat mwawona vuto pa malamulowa pezanani ndi admin ndipo tulani nkhawa zanu. Masiku ena tizikhala ndi mway ocheza ndi alendo koma a mpira okhaokha. *Maule,manoma ndi ma bankers ๐ฉ๐ฉ๐ฉ๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฌ๐ท๐ฌ๐ท๐ฌ๐ท๐ช๐บ๐ช๐บ๐ช๐บ๐ง๐ผ๐ง๐ผ๐ง๐ผ๐ง๐ผpamodz imapanga flames๐ฒ๐ผ* Zikomo khalan omasuka *By adminstration*
*WELCOME TO ๐ ฑ๏ธ๐ ฑ๏ธ๐ฟ๐ฆ๐น FCB NYASA BIG BULLETS* *MALAMULO ATHU ALI MOTELE*๐๐๐ 1๏ธโฃ๐ฟ๐ฆ๐น *Tiyeni tikondane ngat banja limodzi* 2๏ธโฃ๐ฟ๐ฆ๐น *Muno kunyozana ayi ๐คชngat wina wapezeka akunyonza anzake remove ๐ฎโ๐๏ธ* 3๏ธโฃ๐ฟ๐ฆ๐น *Kuponya nkhani za masewelo si ntchito ya admin okha ayi ๐คkma aliyese* 4๏ธโฃ๐ฟ๐ฆ๐น *Za masewelo za kunja ngakhalenso kuno kwathu ndye zofunika koma zikhale zoona* 5๏ธโฃ๐ฟ๐ฆ๐น *Ngati mwalowelana ku inbox zithere komweko muno ayi* (koma osalowelana opanda chilorenzo ayi) 6๏ธโฃ๐ฟ๐ฆ๐น *Muno osaponya ma links agroup ina,Ukapezeka remove ๐ฎโ๐๏ธ* (sitilola maliki agrp ina) 7๏ธโฃ๐ฟ๐ฆ๐น *Muno aliyese osatenga mbali timamutulusa cox muno simongokhala chete ayi* (plus group ili sila asing'anga ai koma la mpira) 8๏ธโฃ๐ฟ๐ฆ๐น *No VN, Porn videos, Stickers and ma photo alaula!* *Muno zonse tantchulazi sitilola Ukapezeka remove ๐ฎโ*๐ญ 9๏ธโฃ๐ฟ๐ฆ๐น *Zandale muno ayi, za chipembezo munso ayi, kutukwana ayinso๐ค ukapeza remove ๐ฎโ๐๏ธ* ๐๐ฟ๐ฆ๐น *Muno 95% ndi nkhani za bullets bas 5% osalayo ya ma team ena* 1๏ธโฃ1๏ธโฃ๐ฟ๐ฆ๐น *Kupanga left muno ndye kuti zampira simbali yako* 1๏ธโฃ2๏ธโฃ๐ฟ๐ฆ๐น *KUTSOGONZA MULUNGU NDYE CHINTHU CHOPAMBANA KWABASI* 1๏ธโฃ3๏ธโฃ๐ฟ๐ฆ๐น *GULU LIZINKHALA LOSEKA KUYAMBIRA 10:30pm FOR SECURITY REASONS MALINGA NDI ANZATHU OFUNA KUTUMIZA ZOSAYENERA* *๐ฐ๐By your Administration* *Ngati mwalikonda group ili, tsatilan malamulo onsewa kuti tikhale limodzi bye bye for now* Don't forget (We are here for the football) *FOREVER MAULE ๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฟ๐ฟ๐ฆ๐น๐ฆ๐น๐ฅ๐ฅ*
Malamulo aa group ali mothelo 1 Vn yoletsedwa โโ 2 macheza katiti โ โ 3 Voice chat yoletsedwa โโ 4 kutukwanana muno ay โโ 5 Nkhani za mpira โ โ โ 6 ma stick No โโ 7 mautenga okuza team ina ay โโ 8 ma link aa group lina ay โ โ 9 Lamulo lomaliza chonde mokumbepa all members monga masapoter aa team yathu ya NBB NYASA BIG BULLETS chonde osanyosa ma admin tikale okondana kulakwisa admin timausana kut tikotse mvuto limenelo zikomo maule notse ๐๐๐๐๐