*Takulandilan pano pa group ya chiuzila macheza & sounds*๐ฅ Malamulo athu ali motele: 1 *ndiudindo wawina aliyese kuponya nkhan komaso nyimbo osadikila admin* 2 *osaponya video or zithuz zolaula* 3 *tisasankhane mtundu tosefe ndife ana abanja limodz* 4 *nkhan za ku inbox zisafike pa group* 5 *tisanyozane pa group kapena kuponya Link ya group ina udzapangidwa remove nthaw yomweyo* 6 *ku join group ino kulibe join fee ndiulele* 7 *Sunday ndi tsiku loponya zithuz ndikufotokoza komwe umakhala* *Pomaliza landilan ulemu nose ma members ya group ino ndipo ndinu olandilidwa ndi manja awiri. Komaso pempho kwa admin akukupemphan ma members nose kut mukhale osamala malamulowa kut masiku okhala nafe achuluke ambuye azikudalisa nthaw zose*๐๐๐ปzikomo
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
*TAKULANDILANI KUGULUPU LATHU LA KHANI ZAKUCHIPINDA MOTSOGOZEBWA NDINE F KHOZA KAPENA KUTI FRANK KHOZA NYAMATA WAPA MWAZA NDIPO KHALANI OMASUKA CHOLINGA CHA GULUPU LATHU NDIKUFUNA KUPHUZITSANA NDI KUDZIWANA* 1๏ธโฃ *NDIPO MALAMULO ATHU ALI MOTELE NGATI MWALOWA KUMENE MUKUYENELA KUPONYA PIK KOMASO DZINA NDI KOMWE MUKUKHLA* 2๏ธโฃ *KUPONYA MA VIDEO NDIKWAWIMA ALIYESE OSADIKILA ADAMN OKHA* 3๏ธโฃ *KULOWA KU IN BOX KWAMUTHU OPANDA CHILOLEZO* โโโโโโโโ 4๏ธโฃ *KUNYOZANA KAPENA KUTUKWANIZANA SITIMALOLA MUKAPEZEKA PANJA*โโโโโโ 5๏ธโฃ *MA Link AMA GULUPU ENA SITIMALOLA MUKAPEZEKA PANJA* โโโโโโ 6๏ธโฃ *MA VN SITIMALOLA MUKAPEZEKA PANJA* โโโโโโโโ 7๏ธโฃ *MA STICKER SITIMALOLA MUKAPEZEKA* โโโโโโโ 8๏ธโฃ *NGATI SIMUKUTENGA MBALI PAMA PROGRAM ATHU MUDZATULUTSIBW 9๏ธโฃ *KUTUMIZA MA VIDEO NDIKWAWIMA ALIYESE OSADIKILA ADAMN OKHA* ๐ ๐๐๐๐๐ *Dzina la hule muno sitimalola ukapezeka panja*
*WELCOME TO NYIMBO NDI MACHEZA*๐ถ๐ต๐๐ผ๐บ๐ป๐๐ผ๐บ๐ปโค๏ธโค๏ธ *MALAMULOโคต๏ธ* *(1)Mukalowa ponyani chithuzi/photo yanu ndikumene mukukhalira. Komanso kumatengapo mbari muzochitika zathu osangokhara chete๐ง๐ป* *(2)Kunyozerana zipembedzo/kunyozana wina ndi mzake sizoloredwa ukapezeka remove.*โโโ *(3)Sitimalora kulankhula, nkhani, zithuzi or ma videos olawura/porno, ukapezeka remove*โโโ *(4)Kutumiza ma audio/VN, stickers AYI ukapezeka remove.*โโโ *(5)Ndi udindo wa aliyense kutumiza nyimbo, mukamatumiza onetsetsani kuti ndi document. Za ma video kumalemba woyimba ndi tittle kupanda kutero remove๐ถ*โโโ *(6)Sizololedwa kulowerana ku inbox koma ngati mwagwirizana kuti muzicheza ku inbox ndi ufulu wanu komanso ngati mukuwona Kuti mukuvutitsidwa kwambiri muli ndi ufulu kuwuza admin zankhaniyi.* *(7) Ngati munthu wakulowerani ku inbox popanda chilorezo chanu and sizinaku sangalatseni osabweretsa nkhani pa group, mudzatulutsidwa chifukwa zima bweretsa chisokonezo pa group, pitani ku inbox kwa admins adzakuthandizanj.* *(8) Sunday tidzikhara tikuponya chithuzi/pic day kupanda kuponyanawo remove*โโโ *(9)Ndikoletsedwa kuponya ma links amagroups ena komanso a facebook ndi YouTube ukapezeka remove.* *(10) Musana pemphe zondani kaye wanthu pa group pano chikhalidwe or MUSADABWE NYIMBO yanu ikapanda kupatsidwa. Chikhalidwe ndichofunika.* *(11) Zandale muno, mpira kapena kunyoza chipembedzo komanso za malonda kapena a singโanga sizoloredwa or remove*โโ *(12) Nyimbo zonse zizi pemphedwa pano osati ku inbox or mudzatulutsidwa* *(13) Chilankhulo muno ndi Chichewa ndi Chizungu basi.* *(14) Ngati member wa kulowerani ku inbox popanda chilorezo chanu and simuna sangalare nanzo wunzani admin straight osadikira kuti pathe week/ma week chifukwa zimabvuta kupanga sort out nkhaniyo komanso muzibweretsa ndi umboni kwa admins kuti admins athe kuyendetsa nkhani yo bwino.* *(15)Tiyeni titsatire malamuro tonse Kuti nthawi ndimatsiku okhala muno achuluke* *KHALANI OMASUKA KOMANSO KUTENGAPO MBALI MU ZOCHITIKA ZATHU* *By admin* ๐๐ฝ๐บ๐ฝโค๏ธ
This group is for only flayers & promoting show's __โก____Rules_____ ( 1 ) No...voice โ ( 3 ) only texing an sharing pictures & advance videos for upcoming show'sโ ( 4 ) no bad stickers๐ซ ( 5) Don't take someone's number in group without permission ๐ซ
๐น๐น๐น WELCOME TO MACHEZA AND LOVE GROUP ๐น๐น๐น ๐๐ CHOLINGA CHA GROUP LA THULI NDI KUPHUZINSANA KOMASO KUTHANDIZANA MAGANIZO PAZOMWE ACHINYAMATA IFE TIKUKUMANA NAZO PAMOYO WATHU WA TSIKU NDI ๐๐๐ (1) MULENDO ALIYENSE AKUYENERA KUPONYA PIC KUTI ATHU AKUZIWENI OSAPONYAYO ๐ฎ๐ฎ๐ฎ๐ฎ ๐ฅฐ ๐ฅฐ๐ฅฐ๐ฅฐ (2) MUTHU ALIYENSE AKUYENERA KULEMEKEZA MAGANIZO AZANU KOMASO MA ADMIN KUKUYENERA KUSATA MA LAMULO OSASATIRA MALAMULO ๐ฎ๐ฎ๐ฎ๐ฎ๐ฎ (3) ALIYENSE AKUYENERA KUTENGAPO GAWO PAZOCHITIKA ZAPA GROUP PANO OSATENGA NAWO GAWO ๐ฎ๐ฎ๐ฎ (4) KUTUMIZA MA VIDEO, MA PHOTO KOMASO MA STICKER OLAULA MUNO AI OPEZEKA ๐ฎ๐ฎ๐ฎ๐ฎ๐ฎ (5) ZONYOZANA MUNO AI OPEZEKA ๐ฎ๐ฎ๐ฎ๐ฎ (6) ๐ฅฐ๐ฅฐ๐ฅฐ๐ฅฐSUNDAY LILILONSE TIMAKHARA NDI PIC DAY ALIYENSE AKUYENERA KUPONYA OSAPONYAYO ๐ฎ๐ฎ๐ฎ๐ฎ (7)๐น๐น๐น๐น๐ฅฐ๐ฅฐ MUTHU AKAKULOWERANI KU INBOX ZIZITHERA KOMWEKO SIMUKUYENERA KUBWERA NAZO PA GROUP PANO KAPENA NGAT MWAPEZA VUTO MUPEZENI ADMIN ALIYENSE AZAKUTHANDIZA ๐๐๐๐ (8) ๐น๐น๐น๐นTIMAKHARA NDI MA PROGRAM PA GROUP PANO ALIYENSE AKUYENERA KUTENGAPO GAWO PAZOCHITIKA ZAPA GROUP PANO OSATENGA NAWO GAWO ๐ฎ๐ฎ๐ฎ๐ฎ NOTICE: ALIYENSE OSASATIRA MALAMULO PA GROUP PANO ADZACHOTSEDWA THAWI YOMWEYO๐คช๐คช๐คช๐คช ๐ฅฐ๐ฅฐ๐ฅฐ๐ฅฐ๐ฅฐ๐น๐น๐น๐น๐นโค๏ธโค๏ธโค๏ธโค๏ธโค๏ธ THANK YOU ๐๐๐๐๐๐น๐น๐น๐น๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ
MWANACHE SUMAILA GROUP group yi ndiya business zili ndinu kukhala kapena kupanga left, mwalandilidwa muno sitiponya ma bm kwamene akufuna inbox km akhale kut ali ndi OTT kapena 1vocha tikutumizilen ku inbox kwanu pogwilitsa ntchito bundle yanuyo zikom kwamene muli ku malaw tumizani ndalam pa number iy 0997756879 NDIPO mupangidwa add ku group ya VIP kut muzilandila mapono aulele komanso group yo SIMATSEKEDWA 24HRS mukadikira zaulele nde muzingoona ma short omweo sinanga zinthuzi timagwirisa ntchito bundle potumiza nde kwamene ali LEDE ATHA kundipeza inbox mukadikira zaulele nde muzingoona ma short omweo sinanga zinthuzi timagwirisa ntchito bundle potumiza nde gulani vocha ndipo mupangidwa add ku group ya VIP kut muzilandila mapono aulele komanso. ndondomeko ili motele ku malaw kukutumiziran ku inbox kwanu ndi K1500 malile data yanu ithe kukupangan add ku VIP ndk2000 ku South African kukutumiziran ku inbox kwanu ndi R10 kukupangan add ku VIP ndi R20 zikom
One sound movement, yhuts empowerment, Giving awareness, helping one another and also global business forum ,politics entertainment, please read the description before taking action let us respect to one another๐ฌ๐ฒ๐ท๐บ๐ฌ๐ณ๐ฌ๐ผ๐ง๐ท๐ฒ๐ฑ๐ง๐ซ๐จ๐ฒ๐ช๐น๐ฏ๐ฒ๐ฌ๐ง๐บ๐ธ๐ณ๐ฌ๐ธ๐ณ๐ฑ๐ท๐ซ๐ท๐ฉ๐ฟ๐ฒ๐ด๐ธ๐ฆ