Search the WhatsAd Community Intelligence index of WhatsApp groups to find the best ones.
1 result in the WhatsAd group index
_*MALAMULO ATHU NDI AWA*_ _Takulandilani mu group muno la zakuchipinda Choyamba mukalowa muno mukuyenera kuponya Pic yanu komaso kufotokoza komwe mumakhala. Cholinga cha group ino ndichakuti tiziphunzitsana zinthu zosiyanasiyana zakuchipinda, komaso kuponya ndi kuonera ma video tiliso ndi ma program osiyanasiyana, timaletsa ana muno, yekhayo anakwanisa Zaka 18 ndamene ali oloredwa, Komaso ngati muli ndi dandaulo pitani Ku inbox Kwa admin ndikupereka dandaulo lanulo musaponye dandaulo lanu direct pa gulu ayi chifukwa si udindo kutero_ _*TIMALETSERATU ZINTHU IZI*_ππ» _*Section 1* Kuponya ma links komaso ma stickers osemphana ndi group iyi_ _*Section 2* Kunyozana_ _*Section 3* Kutukwanizana_ _*Section 4* Kusankhana mitundu Komaso kusankhana machezedwe_ _*Section 5* Osalowa ku in-box kwa munthu without permission_ _*Section 6* Kuponya nkhani za ndale_ _*Section 7* Kuponya nyimbo_ _*Section 8* Kuponya nkhani za chipembezo_ _*Section 9* Ma voice recorder osamalankhula chisawawa tsikub lake ndi Saturday._ _*Section 10* osatenga mbali timamuchotsa_ _*Section 11* Kulemba mayina osadziwika bwino ovuta kuwatchula removed_ _*Section 12* Nkhani za ku in-box osazibweretsa pa gulu ngati wina wakulakwirani awuzeni adindo omwe ndi ma admin kuti akuthandizeni_ _*Section 13:* Timaletseratu kunyozana muno mawu okuti ndiwe galu kapena ndiwe Hule asatuluke pa kamwa panu chifukwa kutero muzayankha mulandu._ _*Section 14:* Pa group pano tikalandila uthenga WA maliro group limatsekedwa 6 koloko mamawa kutsekula 6 koloko Madzulo. Munthawiyi timakhala tikukhuza maliro_ _Tsatirani malamulo athuwa kuti achuluke masiku anu okhala muno._ *By Administration office*βπ»
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
MALAMULO:::::::::::::::::::::::::::::::::: (1) WOSAPONYA LINK YA GROUP LINA (2) ZANDALE KAPENA ZACHIPEMPHEZO NDI KUNYOZANA MUNO AYI ZIMENEZO AWA NDIMACHEZA TIYENI TIKONDANE WINA NDIZAKE (3) WOSATUMIZA CHINTHU CHOKHUZA ZOLAULA MUNO (4) WOSAYIMBA VOICE CALL PA GROUP (5) NGATI MUKUCHEZA NDI ZANU PANKHANI ZA MPIRA CHEZANI BWINOBWINO POSADUMPHA MALILE A ULEMU (6) SUNDAY TIMAKHALA NDI PIC DAY NDICHOLINGA CHOTI TIZIWANE (7) ZIWANI KUTI NDIUDINDO WAWINA ALIYESE KUTUMIZA ZINTHU ZOKHUZA MASEWELO A MPIRA KUTI GROUPLI LIBHEBHE ZIKOMO MAKOMA NONSE MASAPOTA A MA TEAM WOSIYANASIYANAβοΈ
βΌοΈGROUP NUMBER 2β π [link hidden β subscribe to view]?mode=gi_t TIYENI TISATIRE MALAMULO APA GROUP PANO KUTI MUPITILIZE KUKHALA MEMBER WA PA GROUP PANO OSATUMIZA ZITHU ZOLAWURA PA GROUP PANO OSATUMIZA VOICE CHAT KAPENA OSAYIMBA VOICE CALL OSATUMIZA LINK YA GROUP LINA OSATUKWANIZANA NDI MUTHU AKALAKWITSA OSAMANGOTUMIZA ZITHU ZILIZOSE PA GROUP PANO TUMIZANI ZITHU ZOGWIRIZANA NDI GROUP LINO OSATI ZILIZOSE``` NKHANGA ZAONA PA LIMPOPO FM NDI COMRADE NTANYIWA π²πΌπΏπ²π²πΏπΏπ¦ πΏπΌπΊπΈπ«°π€βπ₯±π₯π₯π₯```