Uchingopinda Kanda pick ,age n location tozivana. No politics❎️No other links✖️Jokes Kanda✅️music kanda n introduce urself
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
We have clearance sale of over 300 Electronics items at throw away prices. Grab yours now. All brand new two years warranty. Whatapp/ call 0754230314 BREAKING NEWS 24 hours open Our New business just started for loans and Asset financing Get your loan now stress free.
Nonse amene mwalowa kumene ndakulandirani Muno ndimaponya katundu wa south africa, Tanzania,zambia, Mozambique komanso Tanzania..katundu wina sakhara kuti alipo kale Zimatengera inuyo mundiuze chomwe mukufuna kenako mulipire potsimikiza order yanu Katundu osalipira sinditenga Katundu amafikira ku Dedza,Zomba komanso KU bt ndi lilongwe ndipo kwa akutali ndimatumiza pogwiritsa ntchito njira yomwe inuyo mwasankha Mukhale omasuka ndithu.... nthawi zina katundu amatha kuchedwa izi sizikutanthauza kuti taba koma nthawi zina timatha kukumana ndi zovuta zina zomwe zimapangitsa katundu kuchedwa but all in all katundu amafikabe ndithu.ngati mukufuna kudziwa zambiri hit my inbox. Mbendera yomwe ndaika imasonyeza kochokera item yomwe nfaponyayo
[link hidden — subscribe to view]