CommunitiesFOREVER GOOD FRIENDS๐Ÿป๐Ÿคธโ€โ™€๏ธ๐Ÿฅณ๐ŸŽฏ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ

FOREVER GOOD FRIENDS๐Ÿป๐Ÿคธโ€โ™€๏ธ๐Ÿฅณ๐ŸŽฏ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ

58 membersNYA

About this community

Takulandilani pano pa forever good friends group Mukhale omasuka Ngati muli alendo choyenera kupanga ndi ichi kutumiza picture kapena kuti chinthuzi chani ndikuzitchula dzina kuti ndinu ndani. Muno timaphuzitsa kulemekezani wina ndi mzake posatengela kuti uyu ndi mwana kapena wamkulu Sitilola zinthuzi zolaula kapena makanema olaula ukapezeka utatumiza zimenezi uzapezeka panjaโŒ Timakhala ndima interview muno sizitengela kuti ndi anthu awudindo kapena ayi aliyese wasakhidwa kupangidwa interview amayenera apezekepo ndithu Cholinga cha interview ndikudziwana kuti ndinu yani ndipo mumapanga chani komaso ngati pali anthu ena ofuna kukufikilani pa business yanu kapena pa ntchito yanu akupezeni ndikukupasani ntchito Lamulungu lirilonse kumakhala kutumiza pic ndikuzitchulanso kuti ndinu yani chifukwa chopangila zimenezi ndichakuti tizikumbukilana ndithu Ma link ama group ena muno samaloledwa pokha pokha ngati group yo ili yokhuza ma vacancy muntha kutumiza koma ngati asali okhuza zimenezi muzapangidwa remove Pano pamakhala ma topic osiyana siyana ofuna inu ndine kuthandizana sima admin okha amene amaloledwa kubwelesa topic inuso muli ndi ufulu otelo ndithu ndipo mukukakamizidwa kutenga nawo gawo pa topic komaso pasapezeke nkhani ina yomwe ikukambidwa pakati panthu pamene tili ndi topic Cholinga cha group sopano nachi achinyamata ambiri masiku ano akumakhala ndimatenga omumtima kapena kuti kusausika ndimavuto osiyana siyana so ife pano tonse pamodzi ngati wina ali ndimavuto ake osavutika kapena kupanika pezeni modzi mwa anthu amene ali pa group pa ndipo iye azichibwelesa pamudzipa ngati topic cholinga chake ndichakuti kufuna kumuthandiza mzathu amene ali mumavuto yo zikomo mukhale ndi tsiku lopambana

BusinessNYA
Unlock / View Community

Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.

Related communities

Friends of MDY Sheets (02)

Welcome to the Friends of MDY (Mercaz Daf Yomi) group In this group you will receive: MDY Updates R' Eli's sheets Daily link to the edited YouTube shiur Link to this group:- FoMDY.8MinDaf.com Full Daf on WhatsApp FullWA.8MinDaf.com 8 Minute Daf on WhatsApp Subscribe.8MinDaf.com To sponsor a Shiur Sponsor.8MinDaf.com For the Shabbos News letter Ohr HaMercaz JoinOHM.8MinDaf.com Zoom:- zoom.8MinDaf.com Email R' Eli [email protected]

1.4K+ membersActive this monthEnglish

FRIENDS OF THE REALMS CHORALE NAIROBI (T.R.C)

๐—ง๐—›๐—˜ ๐—ฅ๐—˜๐—”๐—Ÿ๐— ๐—ฆ ๐—–๐—›๐—ข๐—ฅ๐—”๐—Ÿ๐—˜- ๐—ก๐—”๐—œ๐—ฅ๐—ข๐—•๐—œ ๐˜๐Ž๐”๐“๐”๐๐„; https://youtube.com/@therealmschoralenairobi?si=zW0n_hSSrlw01PZ1 ๐“๐ˆ๐Š๐“๐Ž๐Š; tiktok.com/@the.realms.chorale ๐…๐€๐‚๐„๐๐Ž๐Ž๐Š; https://www.facebook.com/share/1Cv6nZ2rDY/ ๐‘ฎ๐’“๐’๐’–๐’‘:https://www.facebook.com/groups/[contact hidden]/?ref=share&mibextid=NSMWBT ๐‘ท๐’‚๐’ˆ๐’†:https://www.facebook.com/share/1JVmh3zLoL/

1K+ membersActive this monthSCO

๐Ÿ’™๐ŸŒนโœจ๐Ÿ’ŽFRIENDS ๐Ÿ’™ ๐Ÿ’Ž๐Ÿ’Šโœจ๐ŸŒˆANDโœจ๐Ÿ’Ž๐Ÿ’™ LOVERS โœจ๐Ÿ’™๐Ÿ’Ž

We respect each other Plz introduce yourself with a pic , age , location . Use view once ๐Ÿ˜๐Ÿ’Ž๐Ÿ’™๐Ÿ’Š๐Ÿ’ƒ๐Ÿ’ƒ No porn videos ๐Ÿ˜๐Ÿ’Ž๐Ÿ’™๐Ÿ’Š No instulting ๐Ÿ˜๐Ÿ’Ž๐Ÿ’™๐Ÿ’Š๐Ÿ’ƒ ๐Ÿ’Ž๐Ÿ’Š๐Ÿ’Š๐Ÿ’ƒ We share jokes๐Ÿ˜ ๐Ÿ’Ž๐Ÿ’™๐Ÿ’Š๐Ÿ’ƒ We use view once when sharing pics ๐Ÿ˜๐Ÿ’Ž๐Ÿ’™๐Ÿ’Š๐Ÿ’ƒ U can find your friend here ๐Ÿ˜๐Ÿ’Ž๐Ÿ’™๐Ÿ’Š๐Ÿ’ƒ Plz dont mantion your group U can find your soulmate ๐Ÿ˜๐Ÿ’Ž๐Ÿ’™๐Ÿ’Š๐Ÿ’ƒ If you break the Rules u will be Removed with immediate effect ๐Ÿ˜ ๐Ÿ˜ ๐Ÿ˜ ๐Ÿ˜ ๐Ÿ˜  Lets have some fun ๐Ÿ˜‚๐Ÿ’ƒ๐Ÿ’Š๐Ÿ’™๐Ÿ˜๐Ÿ˜๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

1K+ membersActive this monthDAN

FRIENDSHIP ZONE๐Ÿค๐Ÿ—ฃ๏ธ๐Ÿ—ฃ๏ธ๐–๐€๐๐Ž ๐Š๐” ๐“๐‘๐”๐’๐“ ๐–๐Ž๐‘๐“๐‡๐˜ ๐“๐„๐€๐ŒโœŒ๏ธ๐Ÿคช๐Ÿ˜Ž๐Ÿคฅ

Welcome to fun vibes Where death takes place โ—โ—BUT NOTE THE FOLLOWINGโš ๏ธ 1. Mentioning the group isn't allowed 2. Disrespect of few members is a straight red card 3. No porn here 4. No links allowed 5. Enjoy to the fullest before u are removed๐Ÿ˜๐Ÿ˜

1K+ membersEnglish

Yossiยฒ Green ๐Ÿ’š Friends!!!! ืžืื—ื•ืจื™ ื”ืคืจื’ื•ื“

Welcome to the official *Yossi Green Friends* group! Please join R' Yossi on an incredible musical journey filled with Torah, music & inspiration! Feel free to send old and unique clips, recordings, pictures, or posters of Yossi Green! Group Link: [link hidden โ€” subscribe to view] The conversation is about Yossi Green! If u would like to post videos of someone singing a Yossi Green song please message an admin Please recite birchas haTorah before viewing this group. Please no random links, videos Enjoy! Please stay on topic. Thanks! *The ยฎ Mediaโ„ข Team Platform* For an extensive list of ยฎ Media groups and affiliate groups click the links! Groups for Yiddishkeit, Chessed, Entertainment, Music, Simchas and more: ๐ŸŒ THE ETC NETWORK Groups https://www.Linktr.ee/theetcnetwork ๐Ÿ’™ Tachlis Daily https://www.Linktr.ee/etcgrouplinks ๐ŸŽท Music Chats https://www.Linktr.ee/musicfansnetwork ๐Ÿฅ‚ Simchas http://Simchas.net

1K+ membersActive this monthEnglish

Tashaโ€™s Preorder Goods๐Ÿ‘— 1

The Goods are all pre-order goods ( wholesale and retail ). PV when interested ๐Ÿ˜Š Thank You. The process to order is very simple: 1. Identify the goods you want ๐Ÿ‘—. 2. PV the admin. 3. Pay 50% of what you desire . 4. Wait patiently for your goods to arrive after two to three weeks weeks of placing order๐Ÿ˜Š 5. After receiving your goods, pay the balance. SIMPLE RIGHT๐Ÿ˜Š Please my group is not for you to text up girls. *It is only for business purposes* Thanks ๐Ÿ™

1K+ membersEnglish

Related searches

Business WhatsApp communitiesBrowse all communities