Alendo nonse ndinu olandilidwa ๐.Tsatilani izi: 1๏ธโฃ. Ikani picture yanu, dzina lanu ndi komwe mumakhala. No audios โ 2๏ธโฃ. Macheza, ma video clips, nkhani, meme ndizololedwa. No stickers โ 3๏ธโฃ. Ma link ndi ma video olawura ๐ ndizosaloledwa โ ukapezeka remove ๐ญ 4๏ธโฃ. Ticheze bwino tisanyozane, ticheze ndi wina aliyense osasakhana kamba ka chipembezo, mtundu, khungu, sex or ulumali. 5๏ธโฃ. Ngati mwakondana kafusilaneni ku inbox kwanuko ife zisatikhuze. 6๏ธโฃ. Ngati mwakangana ku inbox ife zisatikhuze muthane nokha. Muli ndi ufulu kumupanga block chifukwa whatsapp ndi wanu. *NGATI SIMUTSATA ZIMENEZI MUZAPANGIDWA REMOVE. TIYENI TICHEZE MWAKATHITHI NDIFE AMODZI*!
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
๐ณ๐ณ๐ณ๐ณ Takulandilani kuno ku group la โ๏ธโ๏ธ KUCHIMAKE KWA MA LINKS ๐ช ๐ช ๐ซ๐ซ๐ฉโโค๏ธโ๐โ๐ฉ๐ด๐ด๐ด๐ด๐ด ๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐ ๐ซง๐ซง Malamulo anthu ali motere๐ฆ๐ฆ๐ง๐๐๐ ๐๐๐๐๐๐๐๐๐ 1๐ณ๐ณโ๏ธ Ngati mwalowa kumene mu group lino mukupemphedwa kuponya ๐ธ Pic ๐ธyanu ๐๐ฝโโ๏ธ dzina lanu๐๐ฝโโ๏ธkomaso komwe mumakhala๐๏ธkuti tikudziweniโ๏ธโ๏ธ 2๐ณ๐ณโ๏ธndi udindo wa aliyese kuponya ma link โ๏ธโ๏ธ 3๐ณ๐ณโ๏ธAno simalo opangila business kapena ndale โโ 4๐ณ๐ณmacheza ndi oloredwaโโ 4๐ณ๐ณโ๏ธOsaponya ma video ngakhaleso ma pic olaulaโโ 5๐ณ๐ณโ๏ธMa sticker siololedwaโโ 6๐ณ๐ณโ๏ธMa VN ayiโโ 7๐ณ๐ณโ๏ธ Zilankhulo zololedwa muno ndi English komanso Chichewa 8๐ณ๐ณโ๏ธ Ngati mwayambana kwinako zisafike muno โโ 9๐ณ๐ณโ๏ธ Ngati mwakondana Tengelanani ku imbox ๐๐ 10๐ณ๐ณโ๏ธOsalowa ku imbox kwa munthu popanda chilolezoโ๏ธ 11๐ณ๐ณโ๏ธ Sunday iriyonse timakhala ndi ๐ธ PIC DAY๐ธkuyambila nthawi ya 08:00hrsโmpakana kufikila nthawi ya 21:00hrsโโ๏ธ ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ ๐ฆ๐ฆMwakoma nonse nkhalani omasuka๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐
*WELCOME TO KUGAWANA NYIMBO MWAKATHITHI*. ๐ซ๐ง๐ง๐ผ๐ต๐ต๐ถ *MALAMULO ATHU ALIMOTELE๐๐ผ๐๐ผ*. *1.๐ukangojoina kumene group yambakaye waponya pic... Yako ndikuzilongotsola dzina lako ndikomwe ukuchokera*. *2.๐Tilemekedzane wina ndinzache posatengera mtundu kapena chipembedzo or kochokera*.โโโ๐๐ซ *3.๐No ma videos kapena zithunzi zolawula muno even ma voice notesโโโ๐๐ซukangopedzeka remove๐ฌ๐ฎ*. *4.๐No any foreigner groups/links, ma short videos or stickers muno ayiโโโ๐๐ซukangotumidza basi uwona nsana wanjira๐ฌ๐ฎ*. *5.๐ndiudindo wawina aliyense otumidza nyimbo muno osamangodikira ma admin okha kuti atumidze nyimboโโโ๐๐ซ*. *6. ๐Then usanapemphe nyimbo yamba kaye waponya nyimbo zomwe iwe ulinazo ndipo ife tizakuthandidza the same time*. *7.๐Kupempha mowirikidza koma iwe osatumidza zimenezo ayinsoโโโ๐๐ซma camera akakuwona ๐basi remove ndiyomweyo๐ฌ๐ฎ*. *8.๐Ndipo osatenga nawo gawo pa maprograms amenewa timasazikana naye mosayang'ana nkhope๐คฃโโโ๐๐ฌ๐ฎ*. *โ ๏ธ๐ธWARNING: ngati wapedza kt group lakiyidwa๐๐๐๐osafunsa kt why?โโโ๐ Udzalandira remove ๐ฌ๐ฎndekuti ma admin akukonza zina zake zosemphana ndi group*. *#. โ โ Tsatilani zimenezi kt matsiku anu okhala muno achuluke musanawone nsana wanjira ngati omwe adawona John chilembwe kumandala๐*. *#. โ โ Machedza wez koma nyimbo kathithi...*. *WROTE BY ALL ADMINISTRATOR OFFICCERS, MWAKOMA NONSE๐ฅณ๐ฅณ๐๐ป๐๐ป๐คผโโ๏ธ๐คธ๐ปโโ๏ธ๐คธ๐ป๐๐ปโโ๏ธ๐๐๐ป๐๐ป*.
TAKULANDIRANI KUNO KUCHIMAKE KWA NYIMBO KANTHITHI MARAMURO ALI MOTERE๐๐ (1). Osatumiza link ya group Linaย muno (2). Muno ma voice recording ayi aliyense akuyenera kulemba basi (3) kutumiza ma vedio kapena zithunzi zolawura muno ayi (4) Ukaponya nyimbo kapena vedio ukuyenera kulemba title ndamene anayimba (5)ย kulemba title zimathandiza munthu kut usatenge nyimbo yomwe uli nayo kale (6)ย Zosakhana mitundu muno ayi tonse ndife amodzi, nkhani za mipingo, ndaleย ndi mpira muno ayi BY ADMIN โ๏ธโ๏ธโ๏ธโ๏ธโ๏ธ. .......
TAKULANDILANI PA GROUP LA ZBS KHANI KATHITHI PA ZODIAC ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ TIYENI TITSATE MALAMULO AWA. 1๏ธโฃ Mukalowa mutumize pik yanu ndikutchura kumene mumachokera kupanda kutero remove โ 2๏ธโฃ Osatenga nawo mbali remove โ 3๏ธโฃ Record ndiyoloredwa Aliyese atha kumapeleka maganizo ake 4๏ธโฃ Kunyozana kapena kutukwanana muno ayi kupezeka remove โ 5๏ธโฃ Asing'anga muno ayi kupezeka remove โ 6๏ธโฃ Ndinu ololedwa Kutumiza khani zomwe mulinazo 7๏ธโฃ Osatumiza zolawula muno kupezeka remove โ 8๏ธโฃ Group ili ndi laulele ndiye khati mungamatumize khani ndiye kuti admin azakupatsani udindo wamuno 9๏ธโฃ Ma stika muno ayi amasokoneza group kupezeka remove โ TIYENI TITSATE MALAMULO KUTI MUSACHOSEDWE MUNO ZIKOMO ZBS NEWS UPDATE ๐ฒ๐ผ๐ปโจ๏ธ๐ฅ๏ธ๐ฑ๐ฌ๐ป๐บ๐๏ธ ALEX ONLINE TYPING.....: [link hidden โ subscribe to view]?mode=ems_wa_t
*TAKULANDILANI* *KUNO SITIPONYAKO MA FLIM MWAKATHITHI* *KUNO NIMANGOKUDZIWITSANI ZA MA FLIM OMWE ATULUKA KAPENA OMWE ATULUKE* *NGATI MUKUFUNA MUZIPEZA MA FLIM OSE MWADONGOSOLO MUKUYENELA KULIPILA KUTI NIKUPANGENI ADD PA GROUP MBAMBANDE YACHANGU NI YODALILIKA* 0994167642 or 088427789 kmso 0995580610
Guys muno aliyese akudziwa zomwe group ikufuna eti ndiyika malamulo komaso symbol. 1. No link โ 2. No VN 3. No picture. 4. No chilichose chomwe chilibe ma sticker.