TAKURANDILANI KUCHIMAKE KWA NYIMBO MALAMULO ALI MOTERE 1.OSATUMIZA ZOLAWULA PA GROUP IRI KAPENA STICKER UKAPEZEKA REMOVE 2.MUNO MA VOICE RECORDING AKURETSEDWA ALIYESE AKUENERA KUREMBA 3.UKATUMIZA VIDEO OR AUDIO UKUYENERA KUREMBA TITLE YANYIMBOYO 4.KUTUKWANANIZANA MUNO AYI ALIYESE AZIREMBA DZINA LA NYIMBO YOMWE AKUFUNA 5.ZOSANKHANA MITUNDU MUNO AYI GYZ 6.KUREMBA TITLE ZIMATHANDIZA MUNTHU KUTI USATENGE NYIMBO YOTI ULINAYO KARE 7.UKAFUNA KUCHEDZA NDI MDZAKO KU INBOX UMUUZA AKALORA UPITA ☑️🤝🥰 8.KU INBOX KO MUKAYAMBANA NKHAN IMENEYO OSABWERETSA PA GROUP MUKAPEZEKA 🪓❌❌ ZIKOMO ANTHU NOSE MUGULUPU LIMENERI TIYENI TIPEZE NYIMBO ZA PAMTIMA PANTHU PANO 🙏
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
*WELCOME TO NYIMBO NDI MACHEZA*🎶🎵💃🏼🕺🏻💃🏼🕺🏻❤️❤️ *MALAMULO⤵️* *(1)Mukalowa ponyani chithuzi/photo yanu ndikumene mukukhalira. Komanso kumatengapo mbari muzochitika zathu osangokhara chete🧎🏻* *(2)Kunyozerana zipembedzo/kunyozana wina ndi mzake sizoloredwa ukapezeka remove.*❌❌❌ *(3)Sitimalora kulankhula, nkhani, zithuzi or ma videos olawura/porno, ukapezeka remove*❌❌❌ *(4)Kutumiza ma audio/VN, stickers AYI ukapezeka remove.*❌❌❌ *(5)Ndi udindo wa aliyense kutumiza nyimbo, mukamatumiza onetsetsani kuti ndi document. Za ma video kumalemba woyimba ndi tittle kupanda kutero remove🎶*❌❌❌ *(6)Sizololedwa kulowerana ku inbox koma ngati mwagwirizana kuti muzicheza ku inbox ndi ufulu wanu komanso ngati mukuwona Kuti mukuvutitsidwa kwambiri muli ndi ufulu kuwuza admin zankhaniyi.* *(7) Ngati munthu wakulowerani ku inbox popanda chilorezo chanu and sizinaku sangalatseni osabweretsa nkhani pa group, mudzatulutsidwa chifukwa zima bweretsa chisokonezo pa group, pitani ku inbox kwa admins adzakuthandizanj.* *(8) Sunday tidzikhara tikuponya chithuzi/pic day kupanda kuponyanawo remove*❌❌❌ *(9)Ndikoletsedwa kuponya ma links amagroups ena komanso a facebook ndi YouTube ukapezeka remove.* *(10) Musana pemphe zondani kaye wanthu pa group pano chikhalidwe or MUSADABWE NYIMBO yanu ikapanda kupatsidwa. Chikhalidwe ndichofunika.* *(11) Zandale muno, mpira kapena kunyoza chipembedzo komanso za malonda kapena a sing’anga sizoloredwa or remove*❌❌ *(12) Nyimbo zonse zizi pemphedwa pano osati ku inbox or mudzatulutsidwa* *(13) Chilankhulo muno ndi Chichewa ndi Chizungu basi.* *(14) Ngati member wa kulowerani ku inbox popanda chilorezo chanu and simuna sangalare nanzo wunzani admin straight osadikira kuti pathe week/ma week chifukwa zimabvuta kupanga sort out nkhaniyo komanso muzibweretsa ndi umboni kwa admins kuti admins athe kuyendetsa nkhani yo bwino.* *(15)Tiyeni titsatire malamuro tonse Kuti nthawi ndimatsiku okhala muno achuluke* *KHALANI OMASUKA KOMANSO KUTENGAPO MBALI MU ZOCHITIKA ZATHU* *By admin* 💃🏽🕺🏽❤️
*NYIMBO ZOTAMANDA KOMANSO KUKWEZA YEHOVA*
We sell bed linen and blankets of different types from South Africa 🇿🇦. Admin amakhala kubalaka and South Africa
Malamulo a Muno ------------------------------ (1)Kupempha ndikutumiza nyimbo. (2)Nyimbo zake ziyambire 2010 kumatsika kumusi. (3)Osatukwanana wina ndimzake timalimbikitsa ubale muno. (4) Osatumiza link or ma Photo olaura kapenanso zosemphana ndi group lino muzachotsedwa. (5)Osanyozerana mtundu kapena chipembedzo tonse ndi amodzi. Komaso osaponya ma sticker muno ayi (6)Ndi udindo wa aliyense kutumiza ndikupempha nyimbo zakale koma ngati mwafuna zatsopano pemphani ku inbox ena azakupatsani komweko. (7) Ma voice note siololedwa muno koma zikavutitsitsa kuti mufuna nyimbo nde mutu wake simukuudziwa funsani admin aliyense kuti mumumvetseletse Voice note ndipo akusakireni . (8)Osatukwana muno tili ndi anthu akulu akulu azaka zapakanthawi omwe amafunika kuwalemekeza. Tiyeni titsate malamuro kuti tipitilize kusangalara ndinyimbo komanso zochitika zotikumbutsa kale lathu .
💝💞💝💞💝 MALAMULO ATHU ALI MOTERE 💓💓💓💓💓💓 1 MVELANI MALAMULO A GROUP INO 2 KUCHEZA MOSASANKHANA MUTUNDU KOMASO KOCHOKERA POTI TOSE NDIFEANA ABANJA LIMODZI 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 3 NDIUDINDO WA ALIYESE KUTUMIDZA MA VIDEOS AKUCHIPINDA KOMASO MAPIC MWAKATHITHI 💐💐 AMENE SAKUTENGA GAWO KWA 3 DAYS REMOVE 🚯🚯 4 MALINK AMAGULU ENA MUNO OSAPONYAMO CHONDE UKANGOPEZEKA OTERO REMOVE 🕺🕺🕺🕺🕺🕺🕺🕺 5 MA V N TISAGWILITSE NTCHITO KUOPAKUTI TINGAWATHERE BUNDLE ANTHU ENA COZ TIMAPEZA MO SIYANA NDALAMA YA BUNDLE NO STICKERS NO VOICE CHAT 💋💋💋💋💋💋💋💋💋💋💋 6 TIZIKHALA NDI TOPIC LACHITATU LILILOSE NTHAWIYA 7 30 MAZULO🌿🌿🌿🌿🌿🌿🌿🌿🎄🎄🎄🎄🎄🎄🎄 7 SUNDY LILILOSE NDI PIC DAY ALIYESE AKUPEMPHEDWA KUPONYA PIC YAKE NDIKUFOTOKOZA NDI DZINA LAKE KOMASO KOMWEAKUKHALA ! KUPONYA PIC YAMWINIWAKE KULAKWA UKAPEZEKA REMOVE⚠️⚠️⚠️ 8 MUKAFUNA KUFUSILANA PA GROUP POPANO KUPANGIRA ENA ALIPABANJA TINGAWATHESERE BANJA MUKAFUNA KULOWA KU IN BOX AUZENI PA GROUP POPANO KUTI NDIKHOZA KUFIKA KUSELIKO💝💞💝💞💝 MALAMULO ATHU ALI MOTERE 💓💓💓💓💓💓 1 MVELANI MALAMULO A GROUP INO 2 KUCHEZA MOSASANKHANA MUTUNDU KOMASO KOCHOKERA POTI TOSE NDIFEANA ABANJA LIMODZI 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 3 NDIUDINDO WA ALIYESE KUTUMIDZA MA VIDEOS AKUCHIPINDA KOMASO MAPIC MWAKATHITHI 💐💐 AMENE SAKUTENGA GAWO KWA 3 DAYS REMOVE 🚯🚯 4 MALINK AMAGULU ENA MUNO OSAPONYAMO CHONDE UKANGOPEZEKA OTERO REMOVE 🕺🕺🕺🕺🕺🕺🕺🕺 5 MA V N TISAGWILITSE NTCHITO KUOPAKUTI TINGAWATHERE BUNDLE ANTHU ENA COZ TIMAPEZA MO SIYANA NDALAMA YA BUNDLE NO STICKERS NO VOICE CHAT 💋💋💋💋💋💋💋💋💋💋💋 6 TIZIKHALA NDI TOPIC LACHITATU LILILOSE NTHAWIYA 7 30 MAZULO🌿🌿🌿🌿🌿🌿🌿🌿🎄🎄🎄🎄🎄🎄🎄 7 SUNDY LILILOSE NDI PIC DAY ALIYESE AKUPEMPHEDWA KUPONYA PIC YAKE NDIKUFOTOKOZA NDI DZINA LAKE KOMASO KOMWEAKUKHALA ! KUPONYA PIC YAMWINIWAKE KULAKWA UKAPEZEKA REMOVE⚠️⚠️⚠️ 8 MUKAFUNA KUFUSILANA PA GROUP POPANO KUPANGIRA ENA ALIPABANJA TINGAWATHESERE BANJA MUKAFUNA KULOWA KU IN BOX AUZENI PA GROUP POPANO KUTI NDIKHOZA KUFIKA KUSELIKO
*WELCOME TO KUGAWANA NYIMBO MWAKATHITHI*. 🫂🎧🎧🎼🎵🎵🎶 *MALAMULO ATHU ALIMOTELE👇🏼👇🏼*. *1.🛑ukangojoina kumene group yambakaye waponya pic... Yako ndikuzilongotsola dzina lako ndikomwe ukuchokera*. *2.🛑Tilemekedzane wina ndinzache posatengera mtundu kapena chipembedzo or kochokera*.❌❌⛔📛🚫 *3.🛑No ma videos kapena zithunzi zolawula muno even ma voice notes❌❌⛔📛🚫ukangopedzeka remove🎬🚮*. *4.🛑No any foreigner groups/links, ma short videos or stickers muno ayi❌❌⛔📛🚫ukangotumidza basi uwona nsana wanjira🎬🚮*. *5.🛑ndiudindo wawina aliyense otumidza nyimbo muno osamangodikira ma admin okha kuti atumidze nyimbo❌❌⛔📛🚫*. *6. 🛑Then usanapemphe nyimbo yamba kaye waponya nyimbo zomwe iwe ulinazo ndipo ife tizakuthandidza the same time*. *7.🛑Kupempha mowirikidza koma iwe osatumidza zimenezo ayinso❌❌⛔📛🚫ma camera akakuwona 👀basi remove ndiyomweyo🎬🚮*. *8.🛑Ndipo osatenga nawo gawo pa maprograms amenewa timasazikana naye mosayang'ana nkhope🤣❌❌⛔📛🎬🚮*. *⚠️🚸WARNING: ngati wapedza kt group lakiyidwa🔐🔐🔒🔒osafunsa kt why?❌❌⛔📛 Udzalandira remove 🎬🚮ndekuti ma admin akukonza zina zake zosemphana ndi group*. *#. ✅✅Tsatilani zimenezi kt matsiku anu okhala muno achuluke musanawone nsana wanjira ngati omwe adawona John chilembwe kumandala😉*. *#. ✅✅Machedza wez koma nyimbo kathithi...*. *WROTE BY ALL ADMINISTRATOR OFFICCERS, MWAKOMA NONSE🥳🥳💃🏻💃🏻🤼♀️🤸🏻♀️🤸🏻🏋🏻♀️🙊🙌🏻🙌🏻*.