No refund only exchange tikuoda sizili available ngat mukukayika musaode ... kusankha kulipila kuyikidwa pa list...
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
*No refund only exchange* *Osaiwala screen shot mukatumiza ndalama* *Zomwe mukufuna titumeni tizakuodelani* *Muno sitiba* Timaodesa komaso ma retail price Inbox mukafuna kukambilana zambiri *Admin amakhala ku Lilongwe* *Kulikonse timatumiza*
No refund only exchange ...ngat mukukayika musaode
*WELCOME TO KUGAWANA NYIMBO MWAKATHITHI*. 🫂🎧🎧🎼🎵🎵🎶 *MALAMULO ATHU ALIMOTELE👇🏼👇🏼*. *1.🛑ukangojoina kumene group yambakaye waponya pic... Yako ndikuzilongotsola dzina lako ndikomwe ukuchokera*. *2.🛑Tilemekedzane wina ndinzache posatengera mtundu kapena chipembedzo or kochokera*.❌❌⛔📛🚫 *3.🛑No ma videos kapena zithunzi zolawula muno even ma voice notes❌❌⛔📛🚫ukangopedzeka remove🎬🚮*. *4.🛑No any foreigner groups/links, ma short videos or stickers muno ayi❌❌⛔📛🚫ukangotumidza basi uwona nsana wanjira🎬🚮*. *5.🛑ndiudindo wawina aliyense otumidza nyimbo muno osamangodikira ma admin okha kuti atumidze nyimbo❌❌⛔📛🚫*. *6. 🛑Then usanapemphe nyimbo yamba kaye waponya nyimbo zomwe iwe ulinazo ndipo ife tizakuthandidza the same time*. *7.🛑Kupempha mowirikidza koma iwe osatumidza zimenezo ayinso❌❌⛔📛🚫ma camera akakuwona 👀basi remove ndiyomweyo🎬🚮*. *8.🛑Ndipo osatenga nawo gawo pa maprograms amenewa timasazikana naye mosayang'ana nkhope🤣❌❌⛔📛🎬🚮*. *⚠️🚸WARNING: ngati wapedza kt group lakiyidwa🔐🔐🔒🔒osafunsa kt why?❌❌⛔📛 Udzalandira remove 🎬🚮ndekuti ma admin akukonza zina zake zosemphana ndi group*. *#. ✅✅Tsatilani zimenezi kt matsiku anu okhala muno achuluke musanawone nsana wanjira ngati omwe adawona John chilembwe kumandala😉*. *#. ✅✅Machedza wez koma nyimbo kathithi...*. *WROTE BY ALL ADMINISTRATOR OFFICCERS, MWAKOMA NONSE🥳🥳💃🏻💃🏻🤼♀️🤸🏻♀️🤸🏻🏋🏻♀️🙊🙌🏻🙌🏻*.
admin amakhala LL area 23 kutali timatumiza
*No refund only exchange* *Osaiwala screen shot mukatumiza ndalama* *Zomwe mukufuna titumeni tizakuodelani* *Muno sitiba*
Tikuoda ngat mukukayika musaode....no refund only exchange