Vinn Vann ak HT nan vil Okap ak nan GranNó a📢📢📢📱⌚💻👟👠🎒🛍️🛒.
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
👉🏾VIN VANN KOMÈS OU 👉🏾VIN PROMOTE BIZNIS OU 👉🏾VIN ACHTE TOUT SAW PA JWENN LÓT KOTE YO 🆘PA TAG GWOUP LA NAN STATIW SVP PASKE WAP DEYÒ OTOMATIK🆘
*TAKULANDILANI KUGULUPU LATHU LA KHANI ZAKUCHIPINDA MOTSOGOZEBWA NDINE F KHOZA KAPENA KUTI FRANK KHOZA NYAMATA WAPA MWAZA NDIPO KHALANI OMASUKA CHOLINGA CHA GULUPU LATHU NDIKUFUNA KUPHUZITSANA NDI KUDZIWANA* 1️⃣ *NDIPO MALAMULO ATHU ALI MOTELE NGATI MWALOWA KUMENE MUKUYENELA KUPONYA PIK KOMASO DZINA NDI KOMWE MUKUKHLA* 2️⃣ *KUPONYA MA VIDEO NDIKWAWIMA ALIYESE OSADIKILA ADAMN OKHA* 3️⃣ *KULOWA KU IN BOX KWAMUTHU OPANDA CHILOLEZO* ❌❌❌❌❌❌❌❌ 4️⃣ *KUNYOZANA KAPENA KUTUKWANIZANA SITIMALOLA MUKAPEZEKA PANJA*❌❌❌❌❌❌ 5️⃣ *MA Link AMA GULUPU ENA SITIMALOLA MUKAPEZEKA PANJA* ❌❌❌❌❌❌ 6️⃣ *MA VN SITIMALOLA MUKAPEZEKA PANJA* ❌❌❌❌❌❌❌❌ 7️⃣ *MA STICKER SITIMALOLA MUKAPEZEKA* ❌❌❌❌❌❌❌ 8️⃣ *NGATI SIMUKUTENGA MBALI PAMA PROGRAM ATHU MUDZATULUTSIBW 9️⃣ *KUTUMIZA MA VIDEO NDIKWAWIMA ALIYESE OSADIKILA ADAMN OKHA* 🔟 🎄🎄🎄🎄🎄 *Dzina la hule muno sitimalola ukapezeka panja*
*WELCOME TO NYIMBO NDI MACHEZA*🎶🎵💃🏼🕺🏻💃🏼🕺🏻❤️❤️ *MALAMULO⤵️* *(1)Mukalowa ponyani chithuzi/photo yanu ndikumene mukukhalira. Komanso kumatengapo mbari muzochitika zathu osangokhara chete🧎🏻* *(2)Kunyozerana zipembedzo/kunyozana wina ndi mzake sizoloredwa ukapezeka remove.*❌❌❌ *(3)Sitimalora kulankhula, nkhani, zithuzi or ma videos olawura/porno, ukapezeka remove*❌❌❌ *(4)Kutumiza ma audio/VN, stickers AYI ukapezeka remove.*❌❌❌ *(5)Ndi udindo wa aliyense kutumiza nyimbo, mukamatumiza onetsetsani kuti ndi document. Za ma video kumalemba woyimba ndi tittle kupanda kutero remove🎶*❌❌❌ *(6)Sizololedwa kulowerana ku inbox koma ngati mwagwirizana kuti muzicheza ku inbox ndi ufulu wanu komanso ngati mukuwona Kuti mukuvutitsidwa kwambiri muli ndi ufulu kuwuza admin zankhaniyi.* *(7) Ngati munthu wakulowerani ku inbox popanda chilorezo chanu and sizinaku sangalatseni osabweretsa nkhani pa group, mudzatulutsidwa chifukwa zima bweretsa chisokonezo pa group, pitani ku inbox kwa admins adzakuthandizanj.* *(8) Sunday tidzikhara tikuponya chithuzi/pic day kupanda kuponyanawo remove*❌❌❌ *(9)Ndikoletsedwa kuponya ma links amagroups ena komanso a facebook ndi YouTube ukapezeka remove.* *(10) Musana pemphe zondani kaye wanthu pa group pano chikhalidwe or MUSADABWE NYIMBO yanu ikapanda kupatsidwa. Chikhalidwe ndichofunika.* *(11) Zandale muno, mpira kapena kunyoza chipembedzo komanso za malonda kapena a sing’anga sizoloredwa or remove*❌❌ *(12) Nyimbo zonse zizi pemphedwa pano osati ku inbox or mudzatulutsidwa* *(13) Chilankhulo muno ndi Chichewa ndi Chizungu basi.* *(14) Ngati member wa kulowerani ku inbox popanda chilorezo chanu and simuna sangalare nanzo wunzani admin straight osadikira kuti pathe week/ma week chifukwa zimabvuta kupanga sort out nkhaniyo komanso muzibweretsa ndi umboni kwa admins kuti admins athe kuyendetsa nkhani yo bwino.* *(15)Tiyeni titsatire malamuro tonse Kuti nthawi ndimatsiku okhala muno achuluke* *KHALANI OMASUKA KOMANSO KUTENGAPO MBALI MU ZOCHITIKA ZATHU* *By admin* 💃🏽🕺🏽❤️
TAKULANDILAN TO SAKUCHIPINDA KALANI OMASUKA. MALAMULO ATHU ALI MOTERE. : 1:OSAMANYOZANA. SIPHEMBESO. 2. OSATUMIZA LIKE YA GROUP INA UKHAPESEKA REMOVAL ❌. 3. SAUSING'ANGA MUNO AYI UKAPESEKA REMOVAL ❌ 4. OSATUMIZA SITIKI UKAPESEKA REMOVAL ❌ 5. NDIFULU WINA ALIYESE KUTUMIZA MAPONO ☑️☑️🌷🌷🌹🌹🥀🥀 6. NGATI MWALOWA KUMENE MU GROUP LI MUYENELA KUPONYA PIC NDIKOMWE MUKUCHOKHELA☑️☑️🍌🍌💃🌹🌹 7 SUNDAY ILILIYOSE TIMAPONYA PIC DAY OSAPONYAWO REMOVAL 💃💃💃💃💃 8. OSALOWA. KU INBOX KWA KANSI KAPENA MAMUNA POPANDA CHILOLESO UKUKAPESEKA REMOVAL ❌ 9. NGAT PALI VUTO MUPESENI DIMINI WINA ALIYESE AKUTANDISE ✅✅✅ NDIKUKULUPILIRA KUTI AMVEKA MALAMULO TIYENI TISATILE MALAMULO KUT TIKALISE PAMUZI PANO ZIKOM KWAMBIRI MAMEMBARA NOSE ♥️🧚🤸🤸🤸🤸🥀🥀🥀🥀🌹🌹
*Announcement* Good day brethren, a Reminder of our group rules Once Again: 1. *No forwards, chain messages of whatever nature that is, video/ gospel message here/ recording of audio clips. We encourage people to share their own revelation that you get when you read the word of God.* 2. *Dreams & prayer requests should be shared to Pastor Jehu's inbox only[contact hidden].* 3. *The group is strictly a prayer group, personal chats do them kuinbox.* 4. *All testimonies should be shared through our Father Pastor Jehu first. We are all encouraged to send them to his inbox.* 5. *when we correct each other lets do it in love not using harsh words* 6. *No advertising on the group of any products or services. Or sending group links that are not PMM related. Group is strictly a prayer group lets respect that.* 7. *All funeral announcements should go through the group admin. Lets avoid posting any announcements which are not group related on the group.* 8. *Report to the group Admins if you get any messages in your inbox requesting for money or any strange friendship requests from any group members/ any abusive message.* 9. *No use of stickers is allowed on the group.* 10. *If you want to talk to Pastor Jehu Do not call use WhatsApp messages ONLY* *Any questions you might have inbox any admin* *NB: if you break any of the rules group Admins will not hesitate to remove you from the group.* Be blessed as we fellowship together..
🌹🌹🌹 WELCOME TO MACHEZA AND LOVE GROUP 🌹🌹🌹 😏😏 CHOLINGA CHA GROUP LA THULI NDI KUPHUZINSANA KOMASO KUTHANDIZANA MAGANIZO PAZOMWE ACHINYAMATA IFE TIKUKUMANA NAZO PAMOYO WATHU WA TSIKU NDI 😏😏😏 (1) MULENDO ALIYENSE AKUYENERA KUPONYA PIC KUTI ATHU AKUZIWENI OSAPONYAYO 🚮🚮🚮🚮 🥰 🥰🥰🥰 (2) MUTHU ALIYENSE AKUYENERA KULEMEKEZA MAGANIZO AZANU KOMASO MA ADMIN KUKUYENERA KUSATA MA LAMULO OSASATIRA MALAMULO 🚮🚮🚮🚮🚮 (3) ALIYENSE AKUYENERA KUTENGAPO GAWO PAZOCHITIKA ZAPA GROUP PANO OSATENGA NAWO GAWO 🚮🚮🚮 (4) KUTUMIZA MA VIDEO, MA PHOTO KOMASO MA STICKER OLAULA MUNO AI OPEZEKA 🚮🚮🚮🚮🚮 (5) ZONYOZANA MUNO AI OPEZEKA 🚮🚮🚮🚮 (6) 🥰🥰🥰🥰SUNDAY LILILONSE TIMAKHARA NDI PIC DAY ALIYENSE AKUYENERA KUPONYA OSAPONYAYO 🚮🚮🚮🚮 (7)🌹🌹🌹🌹🥰🥰 MUTHU AKAKULOWERANI KU INBOX ZIZITHERA KOMWEKO SIMUKUYENERA KUBWERA NAZO PA GROUP PANO KAPENA NGAT MWAPEZA VUTO MUPEZENI ADMIN ALIYENSE AZAKUTHANDIZA 👍👍👍👍 (8) 🌹🌹🌹🌹TIMAKHARA NDI MA PROGRAM PA GROUP PANO ALIYENSE AKUYENERA KUTENGAPO GAWO PAZOCHITIKA ZAPA GROUP PANO OSATENGA NAWO GAWO 🚮🚮🚮🚮 NOTICE: ALIYENSE OSASATIRA MALAMULO PA GROUP PANO ADZACHOTSEDWA THAWI YOMWEYO🤪🤪🤪🤪 🥰🥰🥰🥰🥰🌹🌹🌹🌹🌹❤️❤️❤️❤️❤️ THANK YOU 💕💕💕💕💕🌹🌹🌹🌹💥💥💥💥💥💥