CommunitiesMALUWA'MEMES AND MACHEZA 24HRS

MALUWA'MEMES AND MACHEZA 24HRS

100+ membersRecently addedRMN

About this community

📌𝗧𝗔𝗞𝗨𝗟𝗔𝗡𝗗𝗜𝗟𝗔𝗡𝗜 𝗣𝗔𝗡𝗢 𝗣𝗔 𝗠𝗔𝗟𝗨𝗪𝗔 𝗠𝗘𝗠𝗘𝗦 𝗔𝗡𝗗 𝗠𝗔𝗖𝗛𝗘𝗭𝗔 *CHOLINGA CHA GROUP INO NDIKUGAWANA MA MEMES KOMASO KUCHEZA* 𝗠𝗔𝗟𝗔𝗠𝗨𝗟𝗢 𝗔𝗧𝗛𝗨 𝗔𝗟𝗜 𝗠𝗢𝗧𝗘𝗟𝗘👇: ```1.MULENDO ALIYESE WANGOLOWA KUMENE AKUYENELA KUPONYA PICTURES YAKE NDIKUDZIFOTOKOZELA BWINO 2.MACHEZA OSAKHANA AY ❌ OSAPONYA MA MAMEMES OKAMBA ZOLAWULA AMA GROUP ENA.❌ 3.NO VOICE CHAT 🚫 NO AUDIO 🚫 AND OSALOWA KU INBOX OPANDA CHIFUKWA NGATI MWAGWILIZANA ZILI NDI INU KUMALOWANA INBOX KOMASO MUKAYAMBANA ZIZITHERA KOMWEKO.🛑 4.KUNYOZANA,KUTUKWANA KAPENA KUNYOZELANA ZIPEMBEDZO MUNO AY.❌❌ 6.ZANDALE KAPENA BUSNES MUNO AY.❌❌ 7.SUNDAY = PIC DAY 📸 8.MONDAY & WEDNESDAY = TOPIC DAY 🗣️ 9.TUESDAY = PROGRAM YA “ANAKULA BWANJI” 😂 10.THURSDAY = NKHANI ZA M’BANJA 🏠 11.FRIDAY = ZACHINYAMATA TIKULE BWANJI 🔥 12.SATURDAY = INTERVIEW DAY 🎤 13.MA VIDEO,MA STICKER.KOMASO MENTIONED GROUP SIZILOLEDWA.❌ 14.ALIYESE AKUYENELA KULEMEKEZA ADMIN KOMASO MAMEMBALA. ⚠️ NOTE:OPWANYA MALAMULO ADZAPANGIDWA REMOVE MONGA MWA MALAMULO 🚫 TSATILAN MALAMULO KUTI MUKHALITSE ZIKOMO 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥```

RMN
Unlock / View Community

Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.

Related communities

MEMES🎶🎬🥰 AND TRENDING CONTENT😇❤️

*😏 💔MEMES AND TRENDING CONTENT GROUP RULES😂. 🤥* 1. *No Spam* – Avoid repeated or irrelevant messages. 2. *No Bots, Bugs, or Tricks* – No bots, glitches, or tech tricks allowed. 3. *No Unrelated Tagging* – Only tag the group when you are participating in discussions. 4. *BANT* – If you can’t match the energy, don’t engage. 5. *Respect Admins & Mods* – Follow instructions. Repeated disrespect may lead to removal. 6. *No Frequent Exits/Rejoins* – Constantly leaving and rejoining may block you from coming back. 7. *No Promo Links* – Only share Memes and have fun. 8. *Admins Can Delete Messages* – Only if it’s spam, links or not memes related. DON'T TAG/MENTIONED THE GROUP *⚠️Violation = 2-day removal or permanent ban.* *😒MEMES AND TRENDING CONTENT😂 is all about Entertainment, Reels, music, group calls and fun. Let’s keep the vibe right!* 🎶🔥❤️ *SMART!*😌

1K+ membersEnglish

KHANI🔥🔥 ZAKUCHIPINDA🔥🔥 AND🔥🔥 MACHEZA🔥🔥 GULUPU

*TAKULANDILANI KUGULUPU LATHU LA KHANI ZAKUCHIPINDA MOTSOGOZEBWA NDINE F KHOZA KAPENA KUTI FRANK KHOZA NYAMATA WAPA MWAZA NDIPO KHALANI OMASUKA CHOLINGA CHA GULUPU LATHU NDIKUFUNA KUPHUZITSANA NDI KUDZIWANA* 1️⃣ *NDIPO MALAMULO ATHU ALI MOTELE NGATI MWALOWA KUMENE MUKUYENELA KUPONYA PIK KOMASO DZINA NDI KOMWE MUKUKHLA* 2️⃣ *KUPONYA MA VIDEO NDIKWAWIMA ALIYESE OSADIKILA ADAMN OKHA* 3️⃣ *KULOWA KU IN BOX KWAMUTHU OPANDA CHILOLEZO* ❌❌❌❌❌❌❌❌ 4️⃣ *KUNYOZANA KAPENA KUTUKWANIZANA SITIMALOLA MUKAPEZEKA PANJA*❌❌❌❌❌❌ 5️⃣ *MA Link AMA GULUPU ENA SITIMALOLA MUKAPEZEKA PANJA* ❌❌❌❌❌❌ 6️⃣ *MA VN SITIMALOLA MUKAPEZEKA PANJA* ❌❌❌❌❌❌❌❌ 7️⃣ *MA STICKER SITIMALOLA MUKAPEZEKA* ❌❌❌❌❌❌❌ 8️⃣ *NGATI SIMUKUTENGA MBALI PAMA PROGRAM ATHU MUDZATULUTSIBW 9️⃣ *KUTUMIZA MA VIDEO NDIKWAWIMA ALIYESE OSADIKILA ADAMN OKHA* 🔟 🎄🎄🎄🎄🎄 *Dzina la hule muno sitimalola ukapezeka panja*

1K+ membersNYA

NYIMBO NDI MACHEZA ALL WELCOME 💃🏽🕺🏽💃🏽🕺🏽

*WELCOME TO NYIMBO NDI MACHEZA*🎶🎵💃🏼🕺🏻💃🏼🕺🏻❤️❤️ *MALAMULO⤵️* *(1)Mukalowa ponyani chithuzi/photo yanu ndikumene mukukhalira. Komanso kumatengapo mbari muzochitika zathu osangokhara chete🧎🏻* *(2)Kunyozerana zipembedzo/kunyozana wina ndi mzake sizoloredwa ukapezeka remove.*❌❌❌ *(3)Sitimalora kulankhula, nkhani, zithuzi or ma videos olawura/porno, ukapezeka remove*❌❌❌ *(4)Kutumiza ma audio/VN, stickers AYI ukapezeka remove.*❌❌❌ *(5)Ndi udindo wa aliyense kutumiza nyimbo, mukamatumiza onetsetsani kuti ndi document. Za ma video kumalemba woyimba ndi tittle kupanda kutero remove🎶*❌❌❌ *(6)Sizololedwa kulowerana ku inbox koma ngati mwagwirizana kuti muzicheza ku inbox ndi ufulu wanu komanso ngati mukuwona Kuti mukuvutitsidwa kwambiri muli ndi ufulu kuwuza admin zankhaniyi.* *(7) Ngati munthu wakulowerani ku inbox popanda chilorezo chanu and sizinaku sangalatseni osabweretsa nkhani pa group, mudzatulutsidwa chifukwa zima bweretsa chisokonezo pa group, pitani ku inbox kwa admins adzakuthandizanj.* *(8) Sunday tidzikhara tikuponya chithuzi/pic day kupanda kuponyanawo remove*❌❌❌ *(9)Ndikoletsedwa kuponya ma links amagroups ena komanso a facebook ndi YouTube ukapezeka remove.* *(10) Musana pemphe zondani kaye wanthu pa group pano chikhalidwe or MUSADABWE NYIMBO yanu ikapanda kupatsidwa. Chikhalidwe ndichofunika.* *(11) Zandale muno, mpira kapena kunyoza chipembedzo komanso za malonda kapena a sing’anga sizoloredwa or remove*❌❌ *(12) Nyimbo zonse zizi pemphedwa pano osati ku inbox or mudzatulutsidwa* *(13) Chilankhulo muno ndi Chichewa ndi Chizungu basi.* *(14) Ngati member wa kulowerani ku inbox popanda chilorezo chanu and simuna sangalare nanzo wunzani admin straight osadikira kuti pathe week/ma week chifukwa zimabvuta kupanga sort out nkhaniyo komanso muzibweretsa ndi umboni kwa admins kuti admins athe kuyendetsa nkhani yo bwino.* *(15)Tiyeni titsatire malamuro tonse Kuti nthawi ndimatsiku okhala muno achuluke* *KHALANI OMASUKA KOMANSO KUTENGAPO MBALI MU ZOCHITIKA ZATHU* *By admin* 💃🏽🕺🏽❤️

900+ membersNYA

← ميـمز // Memes↻ 😂♥️

* _الـࢪوم دۍ مسـاحتۍ الـخاصه أوزع فيهـا طاقـه سلبيـه أوزع_ _طاقـه إيجـابيه أوزع فشـار أنا حـر_💀". ⤹. * _مبعـرفش اتمسـڪك بالعـلاقات ايـدۍ فيهـا زيـت_💀".⤹. * _لينڪك الزفت المخروب اهو هاتي صحابڪك وتعالى ولَا اقولڪك تعالى لوحدڪك_💀🫵🏻". ⤹. 𝐋𝐢𝐧𝐤 [link hidden — subscribe to view]?mode=ems_copy_t

900+ membersArabic

MALUWA'S MEMES24HRS

*WELCOME TO MALUWA'S MEMES24HRS* *WWW.MALUWA'SMEMES24HRS.COM* *MALAMULO AGROUP* ```1. MULENDO WONGOLOWA KUMENE AKUYINERA KUPONYA PIC NDIKUNENA KOMWE AKUCHOKERA. 2. CHOLINGA CHA GROUP NDI KUCHEDZA NDI KUGAWANA MA MEMES 3. WOSAPONYA MA MEMES AMA GROUP ENA❌❌ 4. NO VOICE CHAT AYI NO AUDIO ❌❌ 5. ZONYOZANA AYI KUTUKWANANA AYI❌❌ 6. OSANYOZANA ZIPEMBEZO❌ 7. ZANDALE AYI NO❌❌ 8. SUNDAY PIC DAY 9. MONDAY AND WEDNESDAY TOPIC DAY 10. TUESDAY PROGRAM YA ANAKULA BWANJI 11. THURSDAY PROGRAM YA NKHANI ZA M'BANJA 12. FRIDAY PROGRAM YA ZACHINYAMATA TIKULE BWANJI 13. SUTADAY INTERVIEW DAY 14. SUNDAY PIC DAY 15. MUNO SIMOPANGILA BUSINESS 16.VIDEO -&- MA STICKER MUNO AYI KOMASO MENTIONED GROUP ❌ NOTE: OPWANYA MALAMULO AZAPEDZEKA PANJA REMOVE MONGA MWA MALAMULO ZIKOMO SATILANI MALAMULO KUTI MUKHALITSE``` 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

800+ membersNYA

MACHEZA AND LOVE GROUP 😂😂😂🙋💃💃💞💞💞🤸🤸🏃

🌹🌹🌹 WELCOME TO MACHEZA AND LOVE GROUP 🌹🌹🌹 😏😏 CHOLINGA CHA GROUP LA THULI NDI KUPHUZINSANA KOMASO KUTHANDIZANA MAGANIZO PAZOMWE ACHINYAMATA IFE TIKUKUMANA NAZO PAMOYO WATHU WA TSIKU NDI 😏😏😏 (1) MULENDO ALIYENSE AKUYENERA KUPONYA PIC KUTI ATHU AKUZIWENI OSAPONYAYO 🚮🚮🚮🚮 🥰 🥰🥰🥰 (2) MUTHU ALIYENSE AKUYENERA KULEMEKEZA MAGANIZO AZANU KOMASO MA ADMIN KUKUYENERA KUSATA MA LAMULO OSASATIRA MALAMULO 🚮🚮🚮🚮🚮 (3) ALIYENSE AKUYENERA KUTENGAPO GAWO PAZOCHITIKA ZAPA GROUP PANO OSATENGA NAWO GAWO 🚮🚮🚮 (4) KUTUMIZA MA VIDEO, MA PHOTO KOMASO MA STICKER OLAULA MUNO AI OPEZEKA 🚮🚮🚮🚮🚮 (5) ZONYOZANA MUNO AI OPEZEKA 🚮🚮🚮🚮 (6) 🥰🥰🥰🥰SUNDAY LILILONSE TIMAKHARA NDI PIC DAY ALIYENSE AKUYENERA KUPONYA OSAPONYAYO 🚮🚮🚮🚮 (7)🌹🌹🌹🌹🥰🥰 MUTHU AKAKULOWERANI KU INBOX ZIZITHERA KOMWEKO SIMUKUYENERA KUBWERA NAZO PA GROUP PANO KAPENA NGAT MWAPEZA VUTO MUPEZENI ADMIN ALIYENSE AZAKUTHANDIZA 👍👍👍👍 (8) 🌹🌹🌹🌹TIMAKHARA NDI MA PROGRAM PA GROUP PANO ALIYENSE AKUYENERA KUTENGAPO GAWO PAZOCHITIKA ZAPA GROUP PANO OSATENGA NAWO GAWO 🚮🚮🚮🚮 NOTICE: ALIYENSE OSASATIRA MALAMULO PA GROUP PANO ADZACHOTSEDWA THAWI YOMWEYO🤪🤪🤪🤪 🥰🥰🥰🥰🥰🌹🌹🌹🌹🌹❤️❤️❤️❤️❤️ THANK YOU 💕💕💕💕💕🌹🌹🌹🌹💥💥💥💥💥💥

800+ membersRMN