1 Osasitha chithunzi kapena mutu wa gulu ❌❌❌❌ 2 Ma videos olaula or pic muno ayiii..🚫🚫🚫🚫❌❌❌❌ 3 Osatumiza link ya group lina muno ❌❌❌❌❌ 4 No voice messages/ stickers.❌❌❌❌ 5 Muno simosewela komo kugawana NKhani ndi Sports.✅ 6 Kumatengapo mbali osamangoti duu muzatulusidwa.✅ 7 Ulemu kwa aliyese ndiofunika✅ 8 Nkhani zaku inbox zithere Komweko Osazibweretsa Pano✅ 9 Ngati member wa group waona polakwika alowe ku inbox kwa admin Kuti Amthandize✅ 10 Kusarana ziyankhulo muno ai or zipembezo tose ndife amodzi amalawi.🚫🚫🚫❌❌❌❌❌❌ 11 Aziwitseni anthu zomwe mwatumiza kupanda kutero mupedzeka panja.✅ 🔚 by Admin
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
1️⃣Osasitha chithuzi kapena mutu wa gulu 2⃣Ma videos olaula muno ayi or pic. 3️⃣Osatumiza link ya group lina muno ayinso 4️⃣No voice messages /stickers 🚯. 5️⃣Muno simosewela koma kugawana Sports ndi Tinkhani patali patali 6️⃣kumatengapo mbali osamangoti duu muzatulusidwa. 7️⃣Ulemu kwa aliyese. 8️⃣Nkhan zaku inbox zithere Komweko. 9️⃣Ngati member wa group waona povuta pena pake pita kwa admin aliyese muuze kuti akuthandize 🔟 Kusarana ziyankhulo muno ai or zipembezo tose ndife amodzi amalawi. 11. Aziwitseni anthu zomwe mwatumiza kupanda kutero mupedzeka panja 🔚 *By Admin*
WELCOME TO FCB NYASA BIG 2️⃣0️⃣2️⃣5️⃣ SUPPORTERS GROUP NDIPO MALAMULO ATHU ALI MOTERE⬇️⬇️⬇️ 1️⃣ TIKONDANE WINA NDI MZAKE TOSE NDIFE BANJA LIMODZI MONGA MAPALE 2️⃣OSAMASANKHANA MITINDU KAPENA CHIPEMBEZO 3️⃣ NDI UDINDO WA WINA ALIYETSE KUTUMIDZA UPDATE PA GROUP PANO 4️⃣ NO PORNO VIDEO OR PHOTO( ZITHUZ KAPENA MA VIDEO OLAURA MUNO AYI NDI ZOLETSEDWA 5️⃣ OSAMAPONYA LINK YA GROUP LINA MUNO 6️⃣ OSAMAPONYA MA STICKER MUNO 7️⃣ NO VN MUNO POKHA POKHA ITAKHALA SPORTS 8️⃣ WINA ALIYETSE AZITENGA MBALI MKAKHALA 1 WEEEK OSATENGA MBALI MZATULUSIDWA 9️⃣ OSAMANYOZANA 🔟 NKHAN ZA PA GROUP PANO ZIZIKHALA 90% ZA MPIRA MBALI INAYO TIKHOZA KUMACHEZALO DZINA 1️⃣1️⃣ ZA NDALE MUNO AYI UKAPEZEKA REMOVE 1️⃣2️⃣ NKHAN ZA GROUP PANO ZIZITHERA POMPANO NOT KU INBOX 1️⃣3️⃣ MKAPEZA VUTO PITANI KU INBOX KWA ADMIN NDIPO TSATILAN MALAMULO ZIKOMO *BY ADMIN MUNSA ENTERTAINMENT 🙏🙏🙏🙏
A COLLECTION OF SEVENTH DAY ADVENTIST CHURCH HYMNS
*WELCOME TO 🅱️🅱️🍿🇦🇹 FCB NYASA BIG BULLETS* *MALAMULO ATHU ALI MOTELE*👇👇👇 1️⃣🍿🇦🇹 *Tiyeni tikondane ngat banja limodzi* 2️⃣🍿🇦🇹 *Muno kunyozana ayi 🤪ngat wina wapezeka akunyonza anzake remove 🚮❌🏌️* 3️⃣🍿🇦🇹 *Kuponya nkhani za masewelo si ntchito ya admin okha ayi 🤓kma aliyese* 4️⃣🍿🇦🇹 *Za masewelo za kunja ngakhalenso kuno kwathu ndye zofunika koma zikhale zoona* 5️⃣🍿🇦🇹 *Ngati mwalowelana ku inbox zithere komweko muno ayi* (koma osalowelana opanda chilorenzo ayi) 6️⃣🍿🇦🇹 *Muno osaponya ma links agroup ina,Ukapezeka remove 🚮❌🏌️* (sitilola maliki agrp ina) 7️⃣🍿🇦🇹 *Muno aliyese osatenga mbali timamutulusa cox muno simongokhala chete ayi* (plus group ili sila asing'anga ai koma la mpira) 8️⃣🍿🇦🇹 *No VN, Porn videos, Stickers and ma photo alaula!* *Muno zonse tantchulazi sitilola Ukapezeka remove 🚮❌*🚭 9️⃣🍿🇦🇹 *Zandale muno ayi, za chipembezo munso ayi, kutukwana ayinso🤓 ukapeza remove 🚮❌🏌️* 🔟🍿🇦🇹 *Muno 95% ndi nkhani za bullets bas 5% osalayo ya ma team ena* 1️⃣1️⃣🍿🇦🇹 *Kupanga left muno ndye kuti zampira simbali yako* 1️⃣2️⃣🍿🇦🇹 *KUTSOGONZA MULUNGU NDYE CHINTHU CHOPAMBANA KWABASI* 1️⃣3️⃣🍿🇦🇹 *GULU LIZINKHALA LOSEKA KUYAMBIRA 10:30pm FOR SECURITY REASONS MALINGA NDI ANZATHU OFUNA KUTUMIZA ZOSAYENERA* *📰📝By your Administration* *Ngati mwalikonda group ili, tsatilan malamulo onsewa kuti tikhale limodzi bye bye for now* Don't forget (We are here for the football) *FOREVER MAULE 🇦🇹🇦🇹🍿🍿🇦🇹🇦🇹🔥🔥*
Malamulo aa group ali mothelo 1 Vn yoletsedwa ❌❌ 2 macheza katiti ✅✅ 3 Voice chat yoletsedwa ❌❌ 4 kutukwanana muno ay ❌❌ 5 Nkhani za mpira ✅✅✅ 6 ma stick No ❌❌ 7 mautenga okuza team ina ay ❌❌ 8 ma link aa group lina ay ❌ ❌ 9 Lamulo lomaliza chonde mokumbepa all members monga masapoter aa team yathu ya NBB NYASA BIG BULLETS chonde osanyosa ma admin tikale okondana kulakwisa admin timausana kut tikotse mvuto limenelo zikomo maule notse 🙏🙏🙏🙏🙏