Welcome pa mrakatuli wapamphata;;;; chonde satilani izi kuti mukhalitse👇👇. 1, ngati mwalowa kumene khalani odekha chifukwa mutha kutulusidwa popopo, 2, mono zoponya zolaula ayi ukapezeka ulongeza kusadache, 3,cholinga cha group lino ndikupasana ndakatulo,komanso macheza,, 4,sitilola munthu kulo ku inbox Kwa mnzake opanda kupempha ukapezeka out. 5,ngati mwapeza vuto mu group ili aziwiseni addim ndipo akuthandizani. 6,anthu timapanga add loweluka lokha basi komanso ili nditsiku limenenso timabweresa chikolopa chosetsa onse ongofuna kuzadzitsa pa group pano 7,ngati mwakonda munthu mupempheni popa before kumulowera Ku inbox .. 8 loweluka lililonse tizikhala ndi pic day pachifukwa ichi aliyense akupemphedwa kutenga nawo gawo osateroyo out
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
*PLEASE ATTETION* 🙏🙏 *Muli bwanj kose Muli mwalandridwa group lino nkhan Nd kugawana malink bas nyimbo,nkhan,chilichose Muno Nd choloredwa kupatula kutukwana Nd zo laula bas* *Nd ma recorder* *Machezaso Muno Nd ororedwa km Chichewa Nd chingerez KT tizane bas* *TIVELANE KM CHINTHU ICH PLZ OSAPONYA KAMBILIMBLI LINK IMOZMOZ KUPONYA KAMOZ ANTHU NGAT AIKONDA ALOWA BAS UKAPEZEKA ROMOVE ZBWANA TIMAKANA MUMUNO*💪 *Mmalo mwa madmn ose Nd ngot MWAKOMA nose*🙏🙏🙏🙏🙏👇👇👇👇🤸🤸
Tigawane ma link""";;; udindo otumiza link muno ndi wa wina aliyense, pemphani ndipo muzapasidwa, ndipo nkhani yathu muno ndi ma link bas zinazo osaponya muno usanafunse uzachitidwa remove, macheza abwino zikomo.
*TAKULANDILANI* *KUNO SITIPONYAKO MA FLIM MWAKATHITHI* *KUNO NIMANGOKUDZIWITSANI ZA MA FLIM OMWE ATULUKA KAPENA OMWE ATULUKE* *NGATI MUKUFUNA MUZIPEZA MA FLIM OSE MWADONGOSOLO MUKUYENELA KULIPILA KUTI NIKUPANGENI ADD PA GROUP MBAMBANDE YACHANGU NI YODALILIKA* 0994167642 or 088427789 kmso 0995580610
WELCOME TO KUCHIMAKE KWA NYIMBO MALAMULO ALI MOTERE 1💤NDI UDINDO WA ALIYESE KUTUMIZA NYIMBO OSAMANGODIKILA ADMIN OKHA 2 💤SUNDAYBLILILONSE PALIBE KUGAWANA NYIMBO ILI NDI NSIKU LA PIC DAY NDIMACHEZA 3💤VN MUNO AYI 4 💤ZAUSINGANGA MUNO AYI UKAPEZEKA REMOVE 5 💤MALINK MUNO SAKULOLEDWA KUPATULA LINK LA GROUP LANTHU 6 💤 OSATUMIZA ZOLAULA MUNO UKAPEZEKA REMOVE 7 💤CHIKOLOPA CHIZIYENDA KAMOZI PA MWEZI 8 💤OSANYOZERANA CHIPEMBEZO KAPENA KOCHOKERA 9 💤 ALIYESE AMENE AKUFUNA NYIMBO CHONDE LEMBANI TITLE KOMASO OYIMBAYO 10 💤 GROUP LINO LIZISEKEDWA NTHAWI YA 10:00PM NDIPO LIZISEGULIDWA NTHAWI 6:00AM ZIKOMOOOOO
MUKANGOPANGA JOIN ISANATHE 10 MINUTES PELEKANI MONI KUPANDA KUTERO MUDZATCHOTSEDWA NDIPO SIMUDZAPANGIDWASO ADD. @CHICHEWA MOVIES@ *CHOLINGA CHA GROUP LINO NDIKUGAWANA MA FILIM A CHICHEWA* a English mutha kuponya ngati muli nawo. Zoyenera kutsatira 👉 *👉 Osatumiza link ya group ina* 👉 _Osatumiza zolaula_ _👉 Osatumiza stickers_ _👉 Osatumiza vn voice recorder_ _👉 Osalowa ku inbox popanda chifukwa chomveka_ *_👉 Machedza ndiololedwa
Osatenga Gawo Remove Wotumiza link ya group lina remove Zolaula ayi ukapezeka remove VN ayi ukapezeka remove No pic day Muno ma film ndi aulele Zikomo🤝🤝🤝🔥🔥👌👌