Search the WhatsAd Community Intelligence index of WhatsApp groups to find the best ones.
1 result in the WhatsAd group index
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
Welcom all members Group rules Pangani zogwilizana ndi group zokhuza makhwala zokha No vn No videos No kuyankhula zosephana ndi cholinga cha group Muno chilichose timaphunzisa komaso kupereka komwe muli or kubwera kunoko kumitambo. Nkharani omasuka , funsani zomwe mukufuna kut tikuthandizeni. Participating is the must ngat munthu Akhara 1 week osafunsako or kuyankhulako kalikose timachosa . Muno si zoti munthu azitenga ma information amuno ndikukatuma kwina nooo if so tizapanga remove Ndipo muno chilichose nchaulele.π©π©π©π²π³ππ²
*IFE NDA GREEN WORLD TIKUPEZEKA KU KARONGA, MZUZU, LILONGWE, BLANTYRE,ZOMBA, CHIKWAWA NSANJE ,MWANZA KOMASO LIWONDE*. *TIMATHANA NDI MATENDA OSIYANA SIYANA* *YIMBANI PHONE PA 0887922919 KUTI MUYANKHULANE NDI MR MADALITSO KAJAMU*. *DZIWANI KUTI IFE NDA CHIPATALA OSATI ZITSAMBAπ€*
Cholinga Cha group ndikukambirana nkhani zokhuza dela lathu lamakanjiri kundale zadela ,chitukuko komanso mavuto amdela MALAMULO A GROUP (1) osatumiza zithunzi kapena ma kanema olawula (2) osatumiza ma link ama group ena pamudzi pano (3) osatukwanizana pa group pano (4) kulemekeza maganizo anzathu ,sitingaganize mofanana (5) osatenga nkhani zokambidwa pano mwachisawawa chifukwa anthu akhala ndimaufula olankhula zakukhosi kwawo mosaopa (6) obwela ndichisokonezo sasowa ndipo sitizachedwa kum'panga remove (7) munthu Ali ndiufulu olemba kapena kugwiritsa ntchito mawu ake pogawana uthenga (8) osatumiza nkhani zabodza zopanda umboni pa group Kupezeka ophwanya malamulo adzachotsedwa pa group (9) Group la friends of makanjira liziyamikira kapena kudzudzula andale ,akapezeka munthu obweletsao chisokonezo pa group posafuna anthu kuti adzudzule kapena kuyamikira andale ,munthuyo adzachotsedwa pa group car h
Kodi muli ndimavuto ngatai awa nde mukufuna mayankho. -period yosalekeza,yodontheza,yonunkha,kuwawa kwa msana. -ma ulcers. -sugar/diabetis. -zotupa zachiberekero. -Asthma. -kuwawa ndi kuthimbilira kwa Mano.ndipeze pa #0993818181#