*WELCOME TO NYIMBO NDI MACHEZA ONE (MUSIC AND CHATS)*🎶🎵💃🏼🕺🏻💃🏼🕺🏻❤️❤️ *MALAMULO⤵️* *(1)Mukalowa ponyani chithuzi/photo yanu ndikumene mukukhalira. Komanso kumatengapo mbari muzochitika zathu osangokhara chete🧎🏻* *(2)Kunyozerana zipembedzo/kunyozana wina ndi mzake sizoloredwa ukapezeka remove.*❌❌❌ *(3)Sitimalora kulankhula, nkhani, zithuzi or ma videos olawura/porno, ukapezeka remove*❌❌❌ *(4)Kutumiza ma audio/VN, stickers AYI ukapezeka remove.*❌❌❌ *(5)Ndi udindo wa aliyense kutumiza nyimbo, mukamatumiza onetsetsani kuti ndi document. Za ma video kumalemba woyimba ndi tittle kupanda kutero remove🎶*❌❌❌ *(6)Sizololedwa kulowerana ku inbox koma ngati mwagwirizana kuti muzicheza ku inbox ndi ufulu wanu komanso ngati mukuwona Kuti mukuvutitsidwa kwambiri muli ndi ufulu kuwuza admin zankhaniyi.* *(7) Ngati munthu wakulowerani ku inbox popanda chilorezo chanu and sizinaku sangalatseni osabweretsa nkhani pa group, mudzatulutsidwa chifukwa zima bweretsa chisokonezo pa group, pitani ku inbox kwa admins adzakuthandizanj.* *(8) Sunday tidzikhara tikuponya chithuzi/pic day kupanda kuponyanawo remove*❌❌❌ *(9)Ndikoletsedwa kuponya ma links amagroups ena komanso a facebook ndi YouTube ukapezeka remove.* *(10) Musana pemphe zondani kaye wanthu pa group pano chikhalidwe or MUSADABWE NYIMBO yanu ikapanda kupatsidwa. Chikhalidwe ndichofunika.* *(11) Zandale, mpira kapena kunyoza chipembedzo komanso za malonda kapena a sing’anga sizoloredwa or remove*❌❌ *(12) Nyimbo zonse zizi pemphedwa pano osati ku inbox or mudzatulutsidwa* *(13) Chilankhulo muno ndi Chichewa ndi Chizungu basi.* *(14) Ngati member wa kulowerani ku inbox popanda chilorezo chanu and simuna sangalare nanzo wunzani admin straight osadikira kuti pathe week/ma week chifukwa zimabvuta kupanga sort out nkhaniyo komanso muzibweretsa ndi umboni kwa admins kuti admins athe kuyendetsa nkhani yo bwino.* *(15)Tiyeni titsatire malamuro tonse Kuti nthawi ndimatsiku okhala muno achuluke* *KHALANI OMASUKA KOMANSO KUTENGAPO MBALI MU ZOCHITIKA ZATHU* *By admin* 💃🏽🕺🏽❤️
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
💞🎶🎶🎶 MUSIC IS THE WINE THAT FILLS THE CUP OF SILENCE🎶🎶🎶 💞 💃🕺💫 🌸🌼🌸🌼🌸🌼🌸🌼🌸🌼🌸🌼 ALLOWS✅ 👇 @. Any types of music MP4 & MP3 with caption. RESTRICTS❌👇 @. Unrelated stuffs like, indecent vids & pics, Spam, Scams, Voicemail, Group link etc,,,,,, 👉#* Defaulters will be removed with no further warning.💥
“Music meets the soul” Welcome to Monicah Mbithe Music, the sacred sanctuary where harmonious melodies meet the devotion of all Catholics. 🎶🙏 My mission is to Evangelize Through Music, offering healing to the soul and guiding hearts towards salvation and the glorification of our Lord Jesus Christ. Join me in this divine journey of faith through music. 🙏🎵 https://youtube.com/@MonicaMbitheMusic?si=cfIZAPo1INH1fJgH https://www.facebook.com/profile.php?id=[contact hidden]&mibextid=LQQJ4d https://youtu.be/dA-ubtCFdNs?si=wWMTqLSJGGFt6pHp
𝐄𝐋 𝐐𝐔𝐄 𝐇𝐀𝐂𝐄 𝐒𝐏𝐀𝐌 𝐂𝐎𝐍 SU 𝐌𝐈𝐒𝐌𝐎 𝐋𝐈𝐍𝐊 𝐒𝐄𝐑𝐀́ 𝐄𝐋𝐈𝐌𝐈𝐍𝐀𝐃𝐎 𝐃𝐄𝐋 𝐆𝐑𝐔𝐏𝐎
Solicita unirte y Saluden al ingresar por fa 💘😊 🐱🐱🐱💘😊 🐱🐱🐱🐱🐱🐱🐱🐱💘😊🐱💘 👋 @ `🇼 🇪 🇱 🇨 🇴 🇲 ҽ` ❀ᮬ݃ 🧮⃞݀͘ ㅤ𝆬𝆬 🄵𝗂𝗰𝗵𝖺 𝗗𝗲 ݃ ꒱꒱ ♡᷒ᰰ ꨂꨂ ㅤׄㅤׅㅤ🄿𝗋𝗲𝘀𝗲𝗻𝘁𝗮𝗰𝗶𝗼́𝗻 ㅤ𝆬𝆬 ႂ🎨 ㅤ 𝟶⃞꯭፝𝟷 : ✿ᩧ⃝ㅤֵ 🄽𝗼𝗺𝖻𝗋𝗲 ී ゙ 𝟶⃞꯭፝𝟸 : ✿ᩧ⃝ㅤֵ 🄴𝗱𝖺𝗱 ී ㅤㅤ゙ 𝟶⃞꯭፝𝟹 : ✿ᩧ⃝ㅤֵ 🄿𝗮𝗂́𝘀 ී ゙ 𝟶⃞꯭፝𝟺 : ✿ᩧ⃝ㅤֵ 🅂𝗲𝘅𝘂𝗮𝗹𝗶𝗱𝖺𝗱 𓄹 タ ⋆ 📡 ҂ 𝟶⃞꯭፝𝟻 : 🄶𝗿𝘂𝗽𝗼ꞌꞋꞌ ⏱ ₍ᐢ..ᐢ₎ ˖ ࣪⭑𝗦𝗜 𝗡𝗢 𝗧𝗘 𝗣𝗥𝗘𝗦𝗘𝗡𝗧𝗔𝗦 𝗦𝗘𝗥𝗔́𝗦 𝗘𝗟𝗜𝗠𝗜𝗡𝗔𝗗𝗢 𝗗𝗘𝗟 𝗚𝗥𝗨𝗣𝗢 __________________________________ *💕❤️PUEDEN COMPARTIR LOS QUE DESEEN SIEMPRE Y CUANDO SEA SANO💕😊* ——————————————————— - No pelear, decir groserias, llevemosnos todas bien😉 - No enlaces sin permiso - No acosar a las chicas Conpartir el enlace del grupo que esta disponible en el grupo. s
Please share this link: [link hidden — subscribe to view] Will be posting all the new jewish music here, pretty much on the daily Chat 2: [link hidden — subscribe to view]
"Welcome to MJ Tech Music Promotion, your ultimate partner in music promotion and visual design. We offer a wide range of services, including music uploads, promotion on radio, TV, and social media platforms like Facebook, Twitter, Instagram, and WhatsApp. Our expert graSphic designers create stunning visuals, such as song cover art, album cover art, invitation cards, business flyers, logos, and music lyrics videos. But that's not all! We also host a weekly TOP 10 music challenge competition every Friday, where you can showcase your talent and compete with others. Plus, we offer music Podcast interviews on YouTube, Spotify, and WhatsApp groups and channels. Want to learn more? WhatsApp us at 0982748374 for more information and let's take your music career to the next level!"