CommunitiesPHWETE🤣LOSATHA🤣PANO 1🤣

PHWETE🤣LOSATHA🤣PANO 1🤣

46 membersNDO

About this community

*WELCOME TO PHWETE LOSATHA GROUP* 💎💎💎💎💎💎💎💎💎💎💎 *_MALAMULO ALI MOTELE MUNO_* (1️⃣) *Aliyese mulendo akalowa muno akuyenela kuponya picture yake komaso dzina ndikumudzi kwanu* (2️⃣) *Sitilola kuponya links ya group ina muno ukapezeka remove🚮❌* (3️⃣) *Sitilola zinthuzi zolawuula kapena ma video olawula ukapezeka remove❌🚮* (4️⃣) *Sitilola kuponya sticker muno ukapezeka remove ❌🚮* (5️⃣) *Ma voice muno sitilola komas muno simopangila business ukapezeka remove*❌🚮 (6️⃣) *Aliyese osatengapo mbali muno after week mudzienda chikolopa kuyambila (25 message in 22 message out)* (7️⃣) *Osalowa ku inbox popanda chilolezo cha mwini wakeyo, akakupatsa chilolezocho za kuinbox zinthele konko zisafike pa group* (8️⃣) *Kupeza wachikondi nkololedwa ngati mwakondana pitilizani pokwanilitsa maloto Anu* (9️⃣) *Ngati muli ndi wachikondi wanu pa group chezani ndi wina aliyense koma mosapyola malire kupewa phokoso ndi okondedwa anuwo* (🔟) *ngt ndiwe wa nsanje modzi pa uwu wiri wanu akuyanera kutuluka or ayi nonse limodzi* *_Chenjezo_*: _ngati Zachikondi zanu zikubweletsa chisokonezo pa group pano nonse mudzachotsedwa posayang'anira kuti ndindani eve admin_ *Ma program anthu ali motele muno* 👇👇👇👇👇👇👇👇👇👇👇👇👇👇👇👇👇 (1️⃣) *Monday timakhala ndi topic 8:00pm* (2️⃣) *Tuesday timakhala ndi topic 8:00pm* (3️⃣) *Wednesday program ya Miyambi yomwe aliyense amayenera kutenga po gawo 8:00pm* (4️⃣) *Thursday timakhala ndi topic 8:00pm* (5️⃣) *Friday timakhala ndi topic 8:00pm* (6️⃣) *Saturday program ya tikudziweni yomwe tidzikhala tikucheza ndi mulendo 8:00pm* (7️⃣) *Sunday lililonse program ya tidziwane amai ndi abambo yomwe idzikhala pic day (ndiwe okwatila kapena uli single) kwa tsiku lonse* *_tiyeni tilemekezane wina ndi zake tisanyozane🙏🙏🙏_* *Tisanyozelane zipembezo muno* *_Tiyeni malamulo tiwagwilitse tchito kuti Masiku onkhala nafe muno achuluke zikomo_* *Ndiudindo waliyese kutenga nao gawo muno* *_Done_by_administration_panel.com_*......📝📝🤳

BusinessNDO
Unlock / View Community

Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.

Related communities

FOTOS DE PANOCHAS 😋😈🥵🔥

Bienvenid@s al grupo. Abre este enlace para unirte a mi grupo de WhatsApp: [link hidden — subscribe to view] Fotos de panochas ♨️🔥🥵😈♨️ Permitido ✅ Musica ✅ Películas ✅ Relatos eroticos ✅ Videos xxx ✅ Fotos solo de panochas ✅ Parejas Swingers ✅ Voyeurismo ❌ Prohibido ❌ Menores de edad ❌ CP ❌ Zoofilia ❌ Gore ❌ Molestar por pv ❌ Pedir administración ❌Mirones Bam ❌ Insultos ❌Activas chat audio Bam ❌ Enlaces Disfruta la instancia Solo números +52 🇲🇽 🇲🇽 🇲🇽 ♨️🥵🔥😈♨️🥵🔥😈♨️

1K+ membersSpanish

LINK GROUP 24/7 PANDA UCHIFARA APANA KUTUKANA PANO KUFARA NEKUWADZANA CHETE ...ONE LINK PER DAY ✅

Well come to Link grp happy and happy munhu wese..🤳🤳🤳🫂🫂🫂✅✅ 1) munhu unotenderwa kusenda one link pazuva ukasenda anopfura hwani tokubudisa pn😳🫢 2) this group is for links nekutaurawo nyaya dzakasiyana siyana ✅✅✅🤸‍♂️👉 3)no video or voice note to this group 🚫✅ 4) atibvumi kutukana pano or kutaura politics..🤝🤝🤝🐃 5) mafaro chete 😜 chete 😜 munhu wese

1K+ membersSNA

ZAKUCHIPINDA ZILIPANO

[link hidden — subscribe to view]

900+ membersSNA

ZIKACHITIKA MUMVERA PANO

MWALANDILIDWA PANO PA: 🎬📺📖🖊️💫👇👇✍️🇲🇼 🇲🇼 ZIKACHITIKA MUMVERA PANO (ZmpNews). Gulupu lino sila ndale, cholinga cha gulupu lino ndikuziwisana zomwe zikuchitika maiko otsiyatsiyana. Lino ndi gulu lomwe lili ndi ukadawulo polemba nkhani palokha ndikudziwitsa nkhani zongochitika kumene. Ndipo cholinga cha gulupu lino ndi kutsangalatsa, kudziwitsana, ndi kuphunzitsana. Chomwe gulupuli silinyengelera ndi munthu yemwe; amatukwana, kunyoza, kutumiza ma Links, zolaula, kutumiza nkhani zaboza, kukoledzera kugawikana, ndi zina. Osatenga mbali timachotsa ndipo tikachotsa sitibwenzeretsaso. Mwalandilidwa khalani omasuka. #ZmpNewsMalawi🧑‍💻🖊️🎻🎧⚽⚽🇲🇼🎬📺💫🧑‍💻✍️🇲🇼

800+ membersSNA

🔞BATA PANONAKA KUTII DZVIII🔞🍑🍌🍆

No links ❌No kutukana❌kufara chte nemabbe pungwee nobori🍑🍌🍆🔞

600+ membersSNA

Recetas Hispanoamericana

🌟🔥 ¡ *BIENVENID@* al *GRUPO DE RECETAS*, *MÚSICA* Y *REMEDIOS CASEROS*! 🍲🎶🌿 ¡Un lugar donde la *buena vibra*, el *conocimiento* y la *creatividad* se encuentran! 🎯 Aquí compartimos: 🍳 *Recetas caseras* y *saludables* 🎧 *Música* de todos los géneros 🌱 *Remedios naturales*, *consejos* y *trucos del hogar* 💬 *Ideas*, *historias*, *experiencias* y *buen rollo* 🚨 *NORMAS CLARAS Y ESTRICTAS* 🚨 ❌ *PROHIBIDO ABSOLUTAMENTE*: 🚫 *Enlaces* que no sean timatica del grupo 🚫 *Publicidad*, *promociones* o *SPAM* 🚫 *Pedir ser administrador* 🚫 *Irse a privado sin consentimiento* 🚫 *Faltas de respeto*, *insultos* o *actitudes tóxicas* ✅ *REGLAS DE CONVIVENCIA Y PARTICIPACIÓN*: 💬 *Participación activa* 🤝 *Respeto mutuo* y *buena educación* 🔄 *Aportar contenido* que sume y sea relevante 📚 *Leer bien los mensajes* antes de opinar 📸 *Solo se permiten fotos* relacionadas con los temas del grupo 💥 *ESTE GRUPO ES UNA COMUNIDAD ACTIVA*, *ALEGRE* Y *CON PROPÓSITO*. ¡Participa, comparte y sé parte del cambio con *buena onda* y *respeto*! 🙌 ¡*GRACIAS POR TU ENERGÍA* y por respetar las reglas! Todos los lunes habrá eliminación los que no hablen serán eliminados

500+ membersSpanish

Related searches

Business WhatsApp communitiesBrowse all communities