Mwalandilidwa guys zikomo khalan omasuka. Pano tima cheza momwe unga chezere bola osanyoza mzako ndiw osaloledw kutelo ๐ทand osa ponya link ๐ muno ukapezeka ndi remove ๐ซต๐ซต๐ซต๐ซต
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
*TAKULANDILANI KUGULUPU LATHU LA KHANI ZAKUCHIPINDA MOTSOGOZEBWA NDINE F KHOZA KAPENA KUTI FRANK KHOZA NYAMATA WAPA MWAZA NDIPO KHALANI OMASUKA CHOLINGA CHA GULUPU LATHU NDIKUFUNA KUPHUZITSANA NDI KUDZIWANA* 1๏ธโฃ *NDIPO MALAMULO ATHU ALI MOTELE NGATI MWALOWA KUMENE MUKUYENELA KUPONYA PIK KOMASO DZINA NDI KOMWE MUKUKHLA* 2๏ธโฃ *KUPONYA MA VIDEO NDIKWAWIMA ALIYESE OSADIKILA ADAMN OKHA* 3๏ธโฃ *KULOWA KU IN BOX KWAMUTHU OPANDA CHILOLEZO* โโโโโโโโ 4๏ธโฃ *KUNYOZANA KAPENA KUTUKWANIZANA SITIMALOLA MUKAPEZEKA PANJA*โโโโโโ 5๏ธโฃ *MA Link AMA GULUPU ENA SITIMALOLA MUKAPEZEKA PANJA* โโโโโโ 6๏ธโฃ *MA VN SITIMALOLA MUKAPEZEKA PANJA* โโโโโโโโ 7๏ธโฃ *MA STICKER SITIMALOLA MUKAPEZEKA* โโโโโโโ 8๏ธโฃ *NGATI SIMUKUTENGA MBALI PAMA PROGRAM ATHU MUDZATULUTSIBW 9๏ธโฃ *KUTUMIZA MA VIDEO NDIKWAWIMA ALIYESE OSADIKILA ADAMN OKHA* ๐ ๐๐๐๐๐ *Dzina la hule muno sitimalola ukapezeka panja*
*WELCOME TO NYIMBO NDI MACHEZA*๐ถ๐ต๐๐ผ๐บ๐ป๐๐ผ๐บ๐ปโค๏ธโค๏ธ *MALAMULOโคต๏ธ* *(1)Mukalowa ponyani chithuzi/photo yanu ndikumene mukukhalira. Komanso kumatengapo mbari muzochitika zathu osangokhara chete๐ง๐ป* *(2)Kunyozerana zipembedzo/kunyozana wina ndi mzake sizoloredwa ukapezeka remove.*โโโ *(3)Sitimalora kulankhula, nkhani, zithuzi or ma videos olawura/porno, ukapezeka remove*โโโ *(4)Kutumiza ma audio/VN, stickers AYI ukapezeka remove.*โโโ *(5)Ndi udindo wa aliyense kutumiza nyimbo, mukamatumiza onetsetsani kuti ndi document. Za ma video kumalemba woyimba ndi tittle kupanda kutero remove๐ถ*โโโ *(6)Sizololedwa kulowerana ku inbox koma ngati mwagwirizana kuti muzicheza ku inbox ndi ufulu wanu komanso ngati mukuwona Kuti mukuvutitsidwa kwambiri muli ndi ufulu kuwuza admin zankhaniyi.* *(7) Ngati munthu wakulowerani ku inbox popanda chilorezo chanu and sizinaku sangalatseni osabweretsa nkhani pa group, mudzatulutsidwa chifukwa zima bweretsa chisokonezo pa group, pitani ku inbox kwa admins adzakuthandizanj.* *(8) Sunday tidzikhara tikuponya chithuzi/pic day kupanda kuponyanawo remove*โโโ *(9)Ndikoletsedwa kuponya ma links amagroups ena komanso a facebook ndi YouTube ukapezeka remove.* *(10) Musana pemphe zondani kaye wanthu pa group pano chikhalidwe or MUSADABWE NYIMBO yanu ikapanda kupatsidwa. Chikhalidwe ndichofunika.* *(11) Zandale muno, mpira kapena kunyoza chipembedzo komanso za malonda kapena a singโanga sizoloredwa or remove*โโ *(12) Nyimbo zonse zizi pemphedwa pano osati ku inbox or mudzatulutsidwa* *(13) Chilankhulo muno ndi Chichewa ndi Chizungu basi.* *(14) Ngati member wa kulowerani ku inbox popanda chilorezo chanu and simuna sangalare nanzo wunzani admin straight osadikira kuti pathe week/ma week chifukwa zimabvuta kupanga sort out nkhaniyo komanso muzibweretsa ndi umboni kwa admins kuti admins athe kuyendetsa nkhani yo bwino.* *(15)Tiyeni titsatire malamuro tonse Kuti nthawi ndimatsiku okhala muno achuluke* *KHALANI OMASUKA KOMANSO KUTENGAPO MBALI MU ZOCHITIKA ZATHU* *By admin* ๐๐ฝ๐บ๐ฝโค๏ธ
๐น๐น๐น WELCOME TO MACHEZA AND LOVE GROUP ๐น๐น๐น ๐๐ CHOLINGA CHA GROUP LA THULI NDI KUPHUZINSANA KOMASO KUTHANDIZANA MAGANIZO PAZOMWE ACHINYAMATA IFE TIKUKUMANA NAZO PAMOYO WATHU WA TSIKU NDI ๐๐๐ (1) MULENDO ALIYENSE AKUYENERA KUPONYA PIC KUTI ATHU AKUZIWENI OSAPONYAYO ๐ฎ๐ฎ๐ฎ๐ฎ ๐ฅฐ ๐ฅฐ๐ฅฐ๐ฅฐ (2) MUTHU ALIYENSE AKUYENERA KULEMEKEZA MAGANIZO AZANU KOMASO MA ADMIN KUKUYENERA KUSATA MA LAMULO OSASATIRA MALAMULO ๐ฎ๐ฎ๐ฎ๐ฎ๐ฎ (3) ALIYENSE AKUYENERA KUTENGAPO GAWO PAZOCHITIKA ZAPA GROUP PANO OSATENGA NAWO GAWO ๐ฎ๐ฎ๐ฎ (4) KUTUMIZA MA VIDEO, MA PHOTO KOMASO MA STICKER OLAULA MUNO AI OPEZEKA ๐ฎ๐ฎ๐ฎ๐ฎ๐ฎ (5) ZONYOZANA MUNO AI OPEZEKA ๐ฎ๐ฎ๐ฎ๐ฎ (6) ๐ฅฐ๐ฅฐ๐ฅฐ๐ฅฐSUNDAY LILILONSE TIMAKHARA NDI PIC DAY ALIYENSE AKUYENERA KUPONYA OSAPONYAYO ๐ฎ๐ฎ๐ฎ๐ฎ (7)๐น๐น๐น๐น๐ฅฐ๐ฅฐ MUTHU AKAKULOWERANI KU INBOX ZIZITHERA KOMWEKO SIMUKUYENERA KUBWERA NAZO PA GROUP PANO KAPENA NGAT MWAPEZA VUTO MUPEZENI ADMIN ALIYENSE AZAKUTHANDIZA ๐๐๐๐ (8) ๐น๐น๐น๐นTIMAKHARA NDI MA PROGRAM PA GROUP PANO ALIYENSE AKUYENERA KUTENGAPO GAWO PAZOCHITIKA ZAPA GROUP PANO OSATENGA NAWO GAWO ๐ฎ๐ฎ๐ฎ๐ฎ NOTICE: ALIYENSE OSASATIRA MALAMULO PA GROUP PANO ADZACHOTSEDWA THAWI YOMWEYO๐คช๐คช๐คช๐คช ๐ฅฐ๐ฅฐ๐ฅฐ๐ฅฐ๐ฅฐ๐น๐น๐น๐น๐นโค๏ธโค๏ธโค๏ธโค๏ธโค๏ธ THANK YOU ๐๐๐๐๐๐น๐น๐น๐น๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ
MWANACHE SUMAILA GROUP group yi ndiya business zili ndinu kukhala kapena kupanga left, mwalandilidwa muno sitiponya ma bm kwamene akufuna inbox km akhale kut ali ndi OTT kapena 1vocha tikutumizilen ku inbox kwanu pogwilitsa ntchito bundle yanuyo zikom kwamene muli ku malaw tumizani ndalam pa number iy 0997756879 NDIPO mupangidwa add ku group ya VIP kut muzilandila mapono aulele komanso group yo SIMATSEKEDWA 24HRS mukadikira zaulele nde muzingoona ma short omweo sinanga zinthuzi timagwirisa ntchito bundle potumiza nde kwamene ali LEDE ATHA kundipeza inbox mukadikira zaulele nde muzingoona ma short omweo sinanga zinthuzi timagwirisa ntchito bundle potumiza nde gulani vocha ndipo mupangidwa add ku group ya VIP kut muzilandila mapono aulele komanso. ndondomeko ili motele ku malaw kukutumiziran ku inbox kwanu ndi K1500 malile data yanu ithe kukupangan add ku VIP ndk2000 ku South African kukutumiziran ku inbox kwanu ndi R10 kukupangan add ku VIP ndi R20 zikom
๐๐๐ค๐ฎ๐ฅ๐๐ง๐๐ข๐ฅ๐๐ง๐ข ๐ง๐จ๐ง๐ฌ๐ ๐๐๐๐๐๐๐ ๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐ ๐๐ ๐ค๐ค๐ค Ngati ndiwe mlendo tumiza picture anthu akuziwe komaso komwe umakhala. ๐ธ๐๐๐ช๐๐ค๐ ๐๐๐ ๐๐๐ ๐ฆ๐๐ฆ๐๐ฆ ๐ ๐๐๐๐๐ ๐๐ฆ๐๐ ๐๐๐ก๐๐๐ ๐๐ฆ๐ก๐๐๐๐ ๐๐๐๐ฅ ๐ค๐๐ฅ๐๐๐๐๐๐๐๐ซ๐ ๐๐ฆ๐๐ฅ๐๐ฆ 1. Voice note โ 2. Sticker's โ 3. Kucheza โ 4. Zaku *INBOX* ๐ฅ *ZIZITHERA KONKO* Ngati zavuta pezani admin akuthandizeni ๐ฎ *Azimai.* ๐๐น.. Ngati mwamuna akukuvutitsani Ku inbox pangani screenshot Ku group anthu timuziwe ayaluke. _Mulibe Mwana muno aliyese chomwe akupanga akuchiziwa_ . 5. Ma Link ๐๏ธ ena Muno ayi ukapezeka remove akusata.๐ฎ 6. *Sunday ndi pic day* = Kuzikhalaso voice Chart = Aliyese akhoza Kuyambisa *NTHAWI*: *_6Am_ to* *_10Pm_* โฝALIYESE OSATENGA MBALI MU GROUP remove amayenda.. mothamangila nthawi๐ ๐๐ ๐๐ค๐ ๐๐๐๐ ๐๐๐ ๐ฆ๐๐๐๐๐ ๐จ๐ ๐ฅ๐๐๐๐๐๐ซ๐ ๐๐ฆ๐ฅ ๐๐ฃ๐ ๐ฆ๐ก ๐๐๐ซ๐๐๐ ๐๐ ๐ก๐ ๐ฅ๐๐๐๐ ๐๐๐๐๐ ๐๐ฅ๐๐๐จ๐ ๐ซ๐ ๐๐ค๐. *NOTE* MALAMULO AGROUP AMASITHIDWA PAKADUTSA NTHAWI FROM: _ADMIN DESK_๐
*SALA YA KUMWOMBA* *MT. YOSEFU MSAADA (SALA KUU KWA* *MTAKATIFU YOSEFU)* Ee Mt. Yosefu mwenye heri, tunakimbilia kwako katika masumbuko yetu, na kisha omba shime ya Mchumba wako Mtakatifu, tunaomba pia kwa matumaini usimamizi wako. Kwa ajili ya mapendo uliyompenda Bikira Mtakatifu Mzazi wa Mungu, na kwa ajili ya kumtunza Mtoto Yesu, twakuomba sana, utuangalie kwa wema sie tuliokuwa fungu lake Yesu Kristu, tukakombolewa kwa damu yake. Tusimamie katika masumbuko yetu kwa enzi na shime yako. Ee Mlinzi amini wa jamaa takatifu, uwakinge watoto wateule wa Yesu Kristu. Ee Baba uliyetupenda mno tuepushe na kilema chochote cha madanganyo na upotevu. Ee kinga yetu mwezaji, utusimamie huko juu mbinguni ulipo, tunaposhindana na wenye nguvu wakaao gizani. Kama vile siku za kale ukamwopoa Mtoto Yesu katika hatari ya kuuawa, na leo hivi likinge Kanisa Takatifu la Mungu katika mitego ya adui, na katika shida yote; mtunze daima kila mmoja wetu, tufwate mfano wako, ili tupate na msaada wako, kukaa na utakatifu maisha, kufa kifo chema, na kupata mbinguni makao ya raha milele. Amina. *LITANIA YA MT. YOSEFU* https://youtu.be/UxdMr9TlUkA?s ๐ช *NYIMBO YA MT. YOSEFU MFANYAKAZI๐น๐น๐น https://youtu.be/kEbaHfBqA-A?si=6d1z6hde7LnzvkRP* ๐ฅ ๐๐ฟโโ๏ธ *KAULI MBIU YETU...โTufanye KAZI za BWANA na zetu ZIBARIKIWEโ*๐๐ฝ โ *Tunamshukuru MWENYEZI MUNGU Kwa kutukutanisha kwenye group letu hili KWA HESHIMA YA MT. YOSEFU, lenye dhima ya SALA NA KAZI. (Uhalisia ni MAISHA YA KIROHO na KIMWILI)*. โ *Sisi kama WAKRISTO tunao wajibu wa kukumbushana juu ya kusali, na tunao wajibu wa kuzifanya KAZI zetu ziwe sehemu ya SALA, na SHUGHULI zote tuzifanyazo ili zimpendeze Mwenyezi Mungu*. โ *Kila mwanagroup anao wajibu sawa kama FAMILIA YA MUNGU NA JUMUIYA YA MT. YOSEFU*. *Kwa NAMNA YA PEKEE TUNAO MAPADRE, MAFRATERI NA WATAWA HUMU KUNDINI*. ๐๐ฝ๐๐ฝ๐๐ฝ *Asanteni Sana* *Wenu:-* *Ndugu;* *ยฉAdam Stanslaus Nandi*.๐ค๐ค๐ค โกโกโกโกโกโกโกโกโกโก ๐๐๐๐๐๐HAIRUHUSIWI:- Kutuma LINK YA GROUP LOLOTE, au MAUDHUI yasiyohusu KANISA KATOLIKI, na yaliyo KINYUME CHA MAADILI.๐๐๐๐๐๐. ยฉ [email protected]