CommunitiesSAPOTA WA MPIRA WENI-WENI

SAPOTA WA MPIRA WENI-WENI

30 membersRecently addedVMW

About this community

*MALAMULO ATHU MUNO MU SAPOTA WA MPIRA WENI-WENI* ⚽⚽⚽ (1) alendo khalani omasuka potenga nawo mbali mu zochitika za group lino (2) *timakamba nkhani zokhuza mpira 95% zakunja kwa mpira 5%* (3) 99% zilankhulo zovomerezeka chichewa English 1% zilankhulo zina (4) *sitimalola kupanga recode kuponya ma link ama group ena angakhale ma link a channel ndi ma stickers ena ali onse muno* (5) matsiku ena timakhala ndi ma program monga Monday timakhala ndi mulendo wathu Friday top 20 munthawiyi sitimalola munthu kuponyapo nkhani zakunja kwa program yo mukagotero remove pompo pompo (6) *kusalana kapena kusankhana pa group chifukwa chosiyana zipembezo kapenanso mitundu nkolesedwa* (7) member yemwe sanalowe nawo mu top 20 kwa 2weeks kapena osakwanisako 30 messages adzachotsedwa (8) *tiyeni tipasane ndi kusungilana ulemu polankhula komanso pano sipopezera mkazi / mamuna chonde guys anthufe ndife akulu akulu komanso ndife pachibale za pa group zizithera pa group pompano* (9) group lino sitimalola kubweresa ma update onama pano ukangopezeka pompo pompo remove (10) *ma dmin athu nawonso ndi anthu ali ndi kufooka kwawo ngati alankhula china chake chosakhala bwino ndi ufulu wa member wina aliyense kuzuzura mwaulemu osati monyoza ayi* (11) ma dmin athu samatulutsa munthu mopanda chifukwa ziwani kuti mukangotulutsidwa simuzapangidwanso add ndiye chonde osamabwera ku in box kwa admin (12) Zolaula muno ai kapena kutukwanizana *mukangosunga zomwe mwauzidwa panozi ziwani kuti mukhalitsa muno mpaka kale* *MPHAMVU KWA MASAPOTA ANZANGA OKONDA MA TEAM A MPIRA KWATHU KUNO KOMANSO KEEP NJA KWA DZIKO LINO*

AIVMW
Unlock / View Community

Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.

Related communities

"⚽️INTERNATIONAL TEAMS⚽️ FANS SUPPORTER WENIWENI WOKONDA TEAM YAKE INU YANU ILI KUTI APA? TIZIWE NAWO

MALAMULO:::::::::::::::::::::::::::::::::: (1) WOSAPONYA LINK YA GROUP LINA (2) ZANDALE KAPENA ZACHIPEMPHEZO NDI KUNYOZANA MUNO AYI ZIMENEZO AWA NDIMACHEZA TIYENI TIKONDANE WINA NDIZAKE (3) WOSATUMIZA CHINTHU CHOKHUZA ZOLAULA MUNO (4) WOSAYIMBA VOICE CALL PA GROUP (5) NGATI MUKUCHEZA NDI ZANU PANKHANI ZA MPIRA CHEZANI BWINOBWINO POSADUMPHA MALILE A ULEMU (6) SUNDAY TIMAKHALA NDI PIC DAY NDICHOLINGA CHOTI TIZIWANE (7) ZIWANI KUTI NDIUDINDO WAWINA ALIYESE KUTUMIZA ZINTHU ZOKHUZA MASEWELO A MPIRA KUTI GROUPLI LIBHEBHE ZIKOMO MAKOMA NONSE MASAPOTA A MA TEAM WOSIYANASIYANA✏️

1K+ membersNYA

🇿🇼🇿🇼Cape town🩵Bellville❤️ Maitland 🖤Kraaifontein💙Langa💜gugus🤍donoon💙Wynberg💛Parow🤎mbekweni ❤️‍🔥etc

‼️‼️Market place 🔨📞🚙💿🖥️📲📱🗜️⌚📸📷‼️‼️ 1️⃣Buying and selling 2️⃣ cape town people chete 3️⃣ No violence 4️⃣ Language shona 5️⃣ Price💰 and location 🏘️ 6️⃣Respect is very important 7️⃣ No links ❌❌❌🚮🚮 💚💚 👏👏 thank you🩵🩷❤️🧡💛💚🇿🇦🇿🇦[link hidden — subscribe to view]?mode=hq2tswa

700+ membersActive this monthYAO

PEZANI WACHIKNDl WENIWENI PANO👫

TAKULANDILAN ALENDO MUNO PEZANI WACHIKNDl WANU Lemekezani malamulo 👇👇 1 Ukalowa ponya PIC ndikomwe umakhala 2 Ukafuna kucheza ndimkazi ku inbox uza ky admin 3 Osaponya ma Link a group yina ❌ 4 Audio or VN Ayi 5 muno ukapezeka ukulemba English ❌ 6 Ndiufulu waliyese kuponya mapono 7 Ngat sukutengapo mbali pa nkhani zose ❌ 8 Ngat ndi Stick yapono utha kuponya 9 Tsiku laTopic ndi limodz lachiwir madzulo kuyamba 7 o'clock 10 Tikhale okondana kuti group la2 lipite patsogolo 11 Oyambitsa voice chat join limove ❌ Lemekezan malamulo kuti masiku amuno achuluke

400+ membersNYA

SAPOTA WENI-WENI 🥅⚽🏃🏾‍♂️

*TAKULANDILANI PA SAPOTA WENI-WENI GROUP* _Please read and follow our rules_ ✍🏾 1: Osatumiza Video or picture ya zolaula ❌ 2: Osatumiza link ya group ina ukapezeka 🤺 3: Ziyankhulo zoloredwa muno ndi *Chichewa 70% & English 30%* 🤝 4: Osatumiza Voice record 🗣️ 5: Tisanyozelane zipembezo Akhristu 💒 ndi Aslam 🕍 ndife amozi. 6: Tisanyozelane ma team zimausa mikangano. Tiyeni tisapote mwa mtendere 🤝 7: Osatumiza za asing'anga supa zanuzo mukapeze group ina 🚮 8: Ngati walakwa lamulo no *1 ndi 2* palibe kumva sorry 🤺 9: Aliyense ali ndi ufulu otumiza nkhani za mpira or News osadikira Admin okha.💯 10: Osatenga mbali muno kwa 2 weeks azitulusidwa.📵 11: Tipatsane ulemu tonse ndi a Malawi 🇲🇼 ```Ngati mwasatila malamulo athu ndiye kuti simuzatulusidwa pano pa group ya``` *SAPOTA WENI-WENI* 🥅⚽🏃🏽‍♂️

400+ membersVMW

INHLUPHO ZANAMHLANJE ESIHLANGANA LAZO EMATHANDWENI

😡 no business aderveties, links , Channel 😡 no porn 😡 this is not date site anyone harrasing you inbox please tell any the admin and we remove this person 😡 no politics, Tribalism, Insults, anger issue etc 😡 no personal debates, arguments ✅ all your confessions send them through your admin ✅ audios allowed not more than 1minute.

300+ membersZUL

MASAPOTA ANYASA BIG BULLETS ✅🤝👍☑️✔️

*JOIN NOW* *💯% secure and genuine* *No scams❌* *100% Real and Legit💯*👇👇👇👇👇👇👇👇👇 *[link hidden — subscribe to view]* *[link hidden — subscribe to view]* *[link hidden — subscribe to view]* 👆👆👆👆 *👉🏾This platform is 100% real and legit with a large number of users earning daily from it. You should be a part of this platform and start earning from it daily...*

200+ membersEnglish

Related searches

AI WhatsApp communitiesBrowse all communities