CommunitiesSPORTS UPDATES โšฝ๐Ÿ†โšฝ IN MALAWI โšฝ๐Ÿ†โšฝ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ

SPORTS UPDATES โšฝ๐Ÿ†โšฝ IN MALAWI โšฝ๐Ÿ†โšฝ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ

400+ membersBAN

About this community

*WELCOME TO SPORTSโšฝ๐Ÿ†โšฝ UPDATES IN MALAWI ๐Ÿ†๐Ÿ†โšฝโšพ๐Ÿโšฝ๐Ÿˆ๐Ÿ€ * *_AWA NDI MALAMULO OMWE TIKHALE TIKUYENDERA PA MUDZI PANO_* 1. ZIYANKHULO ZOVOMEREZEKA : Chiyankhulo chinachilichose chomwe timavana ndikuyankhulana kuno kumalawi monga chichewa 2. NO LINK YA GROUP LIRISOSE LAKUNJA:๐Ÿ‘‰opezeka kuti waponya link yakunja kwa group lino uzichotsedwa pompo -pompo. 3. KUTENGAPO GAWO:๐Ÿ‘‰aliyese akuyenera Kumakhala active pazochitika za pa group pano MONGA kubweretsa nkhani za mpira โšฝ , kukomenta ,kufunsa ndi Zina zambiri koma osati zoononga group . 4.KULEMEKEZANA:๐Ÿ‘‰kulemekezana ndikofunika Osatukwanana, Osanyozana, kapena kusemphana zochita chifukwa chosiyana zipembedzo, zipani, ziyankhulo ndi mitundu .'. Chifukwa tonse ndife amodzi tiyeni tipange za mpira๐Ÿ€โšฝโšพโšพ. 5. ZOLAWULA:๐Ÿ‘‰ pa group pano Pali anthu olemekezeka ochokera mmaulemu osiyana-siyana ndiye Zolawula pa MUDZI PANO ayi tiye tizitumiza khani za mpira basiโšฝ๐Ÿ€. 6. MA AUDIOS : ๐Ÿ‘‰ngat mukutumiza audio izikhala sport osati kumayakhula ma Audio pa group sitikumvomeleza poka poka ngat ma admin Ali ndi zolengeza. 7. INBOX:๐Ÿ‘‰Za ku inbox zizithera ku inbox komweko osati zizibwera pa group pano ayi, mkapezeka muzichosedwa. 8. MALONDA:๐Ÿ‘‰kutsatsa MALONDA pa group lino sakuloledwa ayi ukapezeka uzichosedwa. 9. MEMBER:๐Ÿ‘‰ wina aliyese akuyenera kumalemekeza ma lamuro agroup lino komaso kulemekeza amaudindo ose kupatikizapo ma admin athu.โšฝ 10. MA ADMIN NDI COMMITTEE YOSE:๐Ÿ‘‰ azikhala akuyendera group lino week ina liyose nde yemwe sakhukhala active asazadabwe akachosedwa. 11.PORN: ๐Ÿ‘‰mu group lino osayelekeza kutumizamo ma video kapena zithuzi komaso ma audio a zolaura ukapezeka uzichosedwa nthawi yomweyo *_ALINSE OPEZEKA KUTI WAPHWANYA LIMODZI MWA MALAMULOWA AKUYENERA KUCHOTSEDWAโšฝ๐Ÿ€๐Ÿˆโšพ_* SATURDAY AND SUNDAY: week inailiyonse Saturday komaso sundy komaso masiku omwe kuli ma game tizikhala tikupeleka ma update okuzana ndi ma game amuma league osiyanasiyana omwe azikhalapo komaso kupeleka satanesatane wama game ampiraโšฝ๐Ÿ€๐Ÿˆ

NewsSportsBAN
Unlock / View Community

Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.

Related communities

ED Israel Updates 1

ื‘ืจื•ื›ื™ื ื”ื‘ืื™ื ืœืงื‘ื•ืฆืช ื”ืขื“ื›ื•ื ื™ื ื”ืืจืฆื™ืช ืฉืœ ืืงืกื˜ื˜ื™ืง ื“ืื ืก ื™ืฉืจืืœ!! ืงื™ืฉื•ืจ ืœืงื‘ื•ืฆื”: [link hidden โ€” subscribe to view] ืœืขื“ื›ื•ื ื™ื ื ื•ืกืคื™ื, ื”ืฉืจืื” ื•ื”ืจืฉืžื” - ืขืงื‘ื• ืื—ืจื™ื ื• ื‘ืขืจื•ืฆื™ื ื”ืฉื•ื ื™ื: ืคื™ื™ืกื‘ื•ืง - https://www.facebook.com/Ecstatic.dance.il ืื™ื ืกื˜ื’ืจื- https://instagram.com/ecstaticdanceisrael?igshid=MmJiY2I4N

1.4K+ membersActive this monthHebrew

Medical Updates & Doctor Jobs

Medical Events, Conference, Workshop, General Physicians, Dentists, Radiologists, Nurses, Physiotherapists, Gynaecologists , Sonologists Pharmacists Jobs Opportunities, & Home Sessions, Across Pakistan. [link hidden โ€” subscribe to view] [link hidden โ€” subscribe to view] Share With Colleagues & Friends

1K+ membersEnglish

2:KUCCPS, HELB,KMTC, HEF,TVET UPDATES 2

Helping you get quality education ๐Ÿ“ข KUCCPS | TVET | HELB UPDATES GROUP ๐Ÿ“ข Welcome to the official information group . This group provides verified updates on: โœ… KUCCPS Applications, Placement & Transfers โœ… TVET Program Admissions & Guidelines โœ… HELB Loans โ€“ Application & Disbursement โœ… Key Dates & Student Support Alerts ๐Ÿ“š Stay informed. Stay ahead.

1K+ membersEnglish

๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผMALONDA ACHILICHONSE KUMALAWI GROUP ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ

*โš ๏ธ๐Ÿ‘จ๐Ÿปโ€๐Ÿ’ปCHONDE MA CUSTOMER ๐Ÿ‘จ๐Ÿปโ€๐Ÿ’ปโš ๏ธ* *OUR FORUM_* MALONDA ACHILICHONSE ๐Ÿ’ฏโ˜‘๏ธ TITSATILE MALAMULO ๐Ÿ‘‡๐Ÿป๐Ÿ‘‡๐Ÿป๐Ÿ‘จ๐Ÿปโ€๐Ÿ’ป๐Ÿ‘จ๐Ÿปโ€๐Ÿ’ปโš ๏ธ *1๏ธโƒฃ_MKATUMIZA MALONDA LEMBANISO MTENGO / PRICE ๐Ÿ’ฏโ˜‘๏ธ๐Ÿ’ฏโ˜‘๏ธ* *2๏ธโƒฃ_MKATELO MUCHITA BWINO CUSTOMER AKAKONDA MALONDA ANU .. ๐Ÿ‘‰๐ŸปINBOX ๐Ÿ’ฏ* โ˜‘๏ธ *3๏ธโƒฃKULUWA YAYI KULEMBAP0 ๐Ÿ‘‰๐ŸปMtengo/ Price๐Ÿ’ฏโ˜‘๏ธ* 4๏ธโƒฃ *PALA MUNTHU WAIKAPO MALONDA YAKE KUMUJUMA YY* ๐Ÿ’ฏโ˜‘๏ธ 5๏ธโƒฃ *ALIYENSE AGULISE MALONDA ACE MWAFULU๐Ÿ’ฏโ˜‘๏ธ* *CHONDE WAPAPI TILONDOLE MALANGO AYO โ˜๐Ÿป* โš ๏ธ๐Ÿ‘จ๐Ÿปโ€๐Ÿ’ป๐Ÿ‘จ๐Ÿปโ€๐Ÿ’ป ```6๏ธโƒฃCHIKONDI NDICHOFUNIKA!!!! OSASANKHANA MUTUNDU MUNO AYIโš ๏ธ PLEASE NDISE WAMOZA PELA ๐Ÿ’ฏ``` โ˜‘๏ธ ~Zikomo Mabwana By~ Admin Mr *Magwaza* Mvaro & ~C.chima~ ๐Ÿ‘จ๐Ÿปโ€๐Ÿ’ป ๐Ÿ™๐Ÿป๐Ÿ‘จ๐Ÿปโ€๐Ÿ’ป

1K+ membersTOI

MOVIE UPDATES ๐Ÿฟ๐ŸŽฌ

Follow the MOVIE UPDATES channel on WhatsApp: [link hidden โ€” subscribe to view]

1K+ membersGerman

๐Ÿ”ฅโšฝ FOREIGNER SPORTS HOME โšฝ ๐Ÿ”ฅ

*_WELCOME TO ๐Ÿ”ฅโšฝ FOREIGNER SPORTS HOMEโšฝ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ’ฏ_* *Football related only โœ“* *English &Twi onlyโœ“* *We need your participation โœ“* *No linksโŒ* *No insults โŒ* *No audio recordingsโŒ* *No advertisment โŒ* โšฝ๐Ÿ‡ฌ๐Ÿ‡ญโšฝ๐Ÿ‡ฌ๐Ÿ‡ญโšฝ๐Ÿ‡ฌ๐Ÿ‡ญโšฝ๐Ÿ‡ฌ๐Ÿ‡ญโšฝ๐Ÿ‡ฌ๐Ÿ‡ญ *โœ…Live football match links of all clubs* *โœ… Transfer news and rumors* *โœ… Football news* *โœ…Match fixtures* *โœ…Match results & match HIGHLIGHTS๐ŸŽฅ๐Ÿ–ฅ๏ธ* *โœ… Football Trolls & memes๐Ÿคฃ* *โœ… Football funny videos* *โœ… Football skills and dribbles videos* [link hidden โ€” subscribe to view] ```You are welcome again```๐Ÿฉท๐Ÿ’ž๐Ÿ’ฏ *_SIGNED ADMINS_*โœ๏ธ๐Ÿ‡ฌ๐Ÿ‡ญ

1K+ membersEnglish

Related searches

News WhatsApp communitiesSports WhatsApp communitiesBrowse all communities