*TAKULANDIRANI KU TIPEZE WACHIKONDI 💓💓* *MALAMURO NDI AWA* 👇 *1️⃣ALIYENSE AKUYENERA KUTENGA NAWO MBALI KUTI MACHEZA AKOME KOMASO KUTI TIPEZE WACHIKONDI MOSAVUTA👩❤️💋👨👨❤️👨* *2️⃣MULENDO UKAFIKA AKUYENERA KUPONYA PIC NDI KUNENA KOMWE UMAKHALA💃🕺* 🤳 *3️⃣MA LINK AMA GROUP ENA MUNO AI 👺👺* 4️⃣ *MA PROGRAM ATHU ALI MOTERE:* *MONDAY, WEDNESDAY NDI FRIDAY TIMAKHALA NDI* *TOPIC. NDIPO SUNDAY NDI PIC DAY* 💃🕺🤳 *5️⃣NKHANI ZA KU INBOX ZIZITHERO KUMWEKO* 🫐🫐🫐🫐🫐 *6️⃣KUCHEZERANA KUZIWANA KUMAONONGA GROUP KUMACHEZA NDI ALIYENSE* 🤺 *7️⃣VOICE NOTE MUNO AI & WEEK ILIYONSE TIMACHOSA ANTHU OSATENGA NAWO MBALI* 🤺🏹 *🌹🌹🌹TIPEZE WACHIKONDI*
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
𝕋𝕀ℙ𝔼ℤ𝔼 𝕄𝔸𝕃𝕀ℕ𝕂 𝕄𝕌ℕ𝕆 Welcome alendo nonse takulandilani khalani omasuka 🤸♀️🤸♀️🤸♀️🤸♀️🤸♀️🤸♀️🤸♀️🤸♀️🤸♀️muno timalola kuponya malink ndi macheza basi🤺🤺🤺🤺🤺🤺🤺🤺🤺🤺Zosaloledwa muno ndi izi👇🏻👇🏻 𝗭𝗮𝘀𝗶𝗻𝗴'𝗮𝗻𝗴𝗮 𝗭𝗮𝗺𝗮𝗹𝗼𝗻𝗱𝗮 𝗞𝘂𝗽𝗼𝗻𝘆𝗮 𝗹𝗶𝗻𝗸 𝘆𝗼𝗺𝘄𝗲 𝘆𝗼𝗺𝘄𝗲𝘆𝗼 𝗸𝗼𝗺𝗮 𝗺𝗼𝗯𝘄𝗲𝗿𝗲𝘇𝗮 𝗯𝘄𝗲𝗿𝗲𝘇𝗮 ✖️✖️✖️✖️✖️Anzathu onyozera ma 𝗿𝗲𝗺𝗼𝘃𝗲 🙏🏻🙏🏻🙏🏻🙏🏻🙏🏻
MALAMULO AGROUP INO NDI AWA✍️✍️👇👇👇 TIPEZE MALINK PANO 💯% 1 osatumiza ma video olaula kapena photo zolaura ukapezeka remove❌ 2 osatumiza zotsatsa malonda ukapezeka remove❌ 3 osatumiza ma stick ukapezeka remove❌ 4 Osatumiza zachipani ukapezeka remove❌ 5 Osatumiza ma vn kapena record ukapezeka remove❌ 6 tisasakhane mitundu ukapezeka remove❌ Kuponya malink ndi udindo wawina aliyese tiyeni tigawane ma link amene zathu wapepha zikomo Komaso kucheza ndikofunika Tiyeni ticheze Ma member nonse mukhare omasuka pamene mwalowa muno maramulo ndi amenewo tiyeni titsate malamuro kuti masiku okhara muno achuluke mwakoma nose munali ndine m'bale wanu mr Joseph admin anu baye ❤️🇲🇼🇲🇼
Mwalandilidwa. mabwana nose muno sitimaponya mafilimu. Mwaka thithi ndimaponya. Ma post amafilimu omwe atuluka or omwe atatuluse. Pali group limene ndimaponya mafilim. koma ndimayika. Okhao alipila timalipisa pa week kapena pa mwedzi mutha kutumiza ka dora ku number iyi 0998778946 Tilankhulen mukafuna kafuna kuziwa zambili tilakhule pa 📲 0983372539 osawopa
1 Nose ndnu olandilidwa muno. 2 kwambr pano nd macheza ngati pali zofunika kudzwitsa tidzwitsane bola zikhle zowona. 3 Ma link ena siwololedwa pano ukapezeka ukapezeka remove. 4 Utukwanana kpena unyozana pano szikuloledwa tiyen tipatsane ulemu. Zikomo nose tiyen tichezen bas.
📌We sell hotplates ( Good mama, Jx model and diamond) 📌In terms of price, we are very flexible, its almost a give away price
TIPEZE WA CHIKONDI WENIWENI ❤️❤️❤️😍 MALAMURO ALI MOTERE 1 osatumidza link ya group lina ukapedzeka remove 2 osatumidza zolaula ukapezeka removed 3 ngat mwalowa kumene muyenela mponye PC yopanda HD kut tikuziwen mwalamulo 4 Osanyozana ziyankhulo or zipembezo ukapezeka removed 5 Sunday ndi PC day 6 ukapezeka ndivuto rankhula kut tisove vutolo 7 member aliyese ndi oroledwa kuyambisa nkhan zabwino 8ukarowa ku Inbox kwa member aliyese yankhula chomwe ukufuna zikakanika osatukwana 9 chilangulo chilichose chororedwa 10 respect other tonse ndi amodz 11 osapanga business ya iliyose muno ukapedzeka removed 13 ngat wina avutika data timuthandize cholinga cha group ndikupeza mabanja ndikumphuzisana zabanja NDIKHULUPILILA. AVEKA. MALAMULOWA ❤️❤️❤️😍