Search the WhatsAd Community Intelligence index of WhatsApp groups to find the best ones.
1 result in the WhatsAd group index
*Asalam walykum walahamat llah wabalakatuh* Takurandiran pano pa tiphuzire chisilamu, cholinga cha group rathu kuphuzisana za chisilamu ( 1 )Malamulo ali motere? Munthu akalakwisa kuwerenga Quran osaseka, (2) Group rathu limasegulidwa ma siku four 4 pa week (3) osaponya sticker yosephana ndi chisiramu (4) osaponya group link ina kupatula ma group athu (5) ma ccter sakuyenera kuponya voice azingonvera
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
Salamu alahkum walahamaturah wabrakatu Takulandilan Malamulo athu ali chochi:: 1 Osatukwana nzako 2 Osatenga mbali remove 3 Mastick muno ai 4 aliyese ali ndi ufulu ofunsa mafunso komanso, uliki, hadith, ndizina 5 sizoloredwa kunseka nzako 6 siziloledwa kusasa malonda kapena using'anga kapena nkhani zilizonse zosakhala mau amulungu. 7 sitilo voice yomvera kamodzi 8 moni oti hell, hi, wawa, bhobho siovomelezeka koma salamu alahkum. 9 Osatulusa mutu wa nkhani ina, lna isanathe 10 voice call ndiyololedwa 11 ziyankhulo zonse ndizololedwa, chiyao, chichewa, English ndizina 12 Nthaw iliyonse ya swalat group imatsekedwa 10mns 13 osatumiza malink a group lina muno ukapezeka remove. muno simopempha chithandizo, kulengedzetsa uthenga wamaliro, ngozi, malonda, ZACHIPAN and nyimbo siziloledwa