Search the WhatsAd Community Intelligence index of WhatsApp groups to find the best ones.
1 result in the WhatsAd group index
*Tumizani ndalama zanu ku chokera ku South African πΏπ¦ kupita ku malawi π²πΌ mwachangu komanso ndimodalilika. Munthu akatipasa ndalama, anthu ali kumudzi amalandila nthawi yomweyo kaya pa manja , Airtel money kapena TNM mpamba komanso ndi Bank iliyonse imene ili Malawi* *Tipezeni lero kuti tipange nanu business Kaya inu ndi super agent kapena agent wamba kapena siinu agent tipezeni lero kuti tipange business.* *MUKAFUNA KUDZIWA ZAMBIRI NDILANKHULENI KU IN BOX*
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
*β οΈπ¨π»βπ»CHONDE MA CUSTOMER π¨π»βπ»β οΈ* *OUR FORUM_* MALONDA ACHILICHONSE π―βοΈ TITSATILE MALAMULO ππ»ππ»π¨π»βπ»π¨π»βπ»β οΈ *1οΈβ£_MKATUMIZA MALONDA LEMBANISO MTENGO / PRICE π―βοΈπ―βοΈ* *2οΈβ£_MKATELO MUCHITA BWINO CUSTOMER AKAKONDA MALONDA ANU .. ππ»INBOX π―* βοΈ *3οΈβ£KULUWA YAYI KULEMBAP0 ππ»Mtengo/ Priceπ―βοΈ* 4οΈβ£ *PALA MUNTHU WAIKAPO MALONDA YAKE KUMUJUMA YY* π―βοΈ 5οΈβ£ *ALIYENSE AGULISE MALONDA ACE MWAFULUπ―βοΈ* *CHONDE WAPAPI TILONDOLE MALANGO AYO βπ»* β οΈπ¨π»βπ»π¨π»βπ» ```6οΈβ£CHIKONDI NDICHOFUNIKA!!!! OSASANKHANA MUTUNDU MUNO AYIβ οΈ PLEASE NDISE WAMOZA PELA π―``` βοΈ ~Zikomo Mabwana By~ Admin Mr *Magwaza* Mvaro & ~C.chima~ π¨π»βπ» ππ»π¨π»βπ»
πΏπ¦π²πΌπΏπ¦π²πΌπΏπ¦π²πΌπΏπ¦π²πΌπΏπ¦π²πΌπΏπ¦
0
Twaibu
Tumizani ndalama kumudzi mwachangu komanso modalilika pa rate yabwino.
Gululi ndilaulele. Nde pasapezeke utumiza zinthu zosagwikizana ndi gululi Nthawi yomweyo azachosedwa. Ndipo pakanyasa kwambiri timapempha seka. Only admin ndiamene akumakwanisa kutumizapo uthenga. Nde tikaliseka pasamapezeke wina okalupa as if ndilolipila. Zichepe zimenezo.