CommunitiesZBS KUTHYAKULA NKHANI

ZBS KUTHYAKULA NKHANI

500+ membersCJK

About this community

1 Osasitha chithunzi kapena mutu wa gulu ❌❌❌❌ 2 Ma videos olaula or pic muno ayiii..🚫🚫🚫🚫❌❌❌❌ 3 Osatumiza link ya group lina muno ❌❌❌❌❌ 4 No voice messages/ stickers.❌❌❌❌ 5 Muno simosewela komo kugawana NKhani ndi Sports.✅ 6 Kumatengapo mbali osamangoti duu muzatulusidwa.✅ 7 Ulemu kwa aliyese ndiofunika✅ 8 Nkhani zaku inbox zithere Komweko Osazibweretsa Pano✅ 9 Ngati member wa group waona polakwika alowe ku inbox kwa admin Kuti Amthandize✅ 10 Kusarana ziyankhulo muno ai or zipembezo tose ndife amodzi amalawi.🚫🚫🚫❌❌❌❌❌❌ 11 Aziwitseni anthu zomwe mwatumiza kupanda kutero mupedzeka panja.✅ 🔚 by Admin

SportsAICJK
Unlock / View Community

Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.

Related communities

ZBS KUTHYAKULA NKHANI

1 Osasitha chithunzi kapena mutu wa gulu ❌❌❌❌ 2 Ma videos olaula or pic muno ayiii..🚫🚫🚫🚫❌❌❌❌ 3 Osatumiza link ya group lina muno ❌❌❌❌❌ 4 No voice messages/ stickers.❌❌❌❌ 5 Muno simosewela komo kugawana NKhani ndi Sports.✅ 6 Kumatengapo mbali osamangoti duu muzatulusidwa.✅ 7 Ulemu kwa aliyese ndiofunika✅ 8 Nkhani zaku inbox zithere Komweko Osazibweretsa Pano✅ 9 Ngati member wa group waona polakwika alowe ku inbox kwa admin Kuti Amthandize✅ 10 Kusarana ziyankhulo muno ai or zipembezo tose ndife amodzi amalawi.🚫🚫🚫❌❌❌❌❌❌ 11 Aziwitseni anthu zomwe mwatumiza kupanda kutero mupedzeka panja.✅ 🔚 by Admin

800+ membersCJK

MA LINK, MA SCANDAL NDI NKHANI

*MWALANDIRIDWA MUNO NONSE.* *MALAMULO AMUNO ALI CHONCHI:* *1. Osanyozana kapena kunyozana mtundu kapena chipembedzo.* *2. Osaponya link imodzi mobwereza, muzidikira ma hours angapo mkuponyanso.* *3. Osatsatsa malondamuno. Ma porno ayi muno.* *4. A Sing’anga muno ayi.* *5. Za ma status zizithera ku ma status komweko.* *6. Ma Gif kapena stickers muno ayi*

700+ membersFUF

ZOCHITIKA MU AFRICA PANO PA CHINYANJA SERVICE NO FAVOUR NO FEAR KOMA KUKUPASILANI NKHANI ZOKHA ZOKHA

1 Osasitha chithunzi kapena mutu wa gulu ❌❌❌❌ 2 Ma videos olaula or pic muno ayiii..🚫🚫🚫🚫❌❌❌❌ 3 Osatumiza link ya group lina muno ❌❌❌❌❌ 4 No voice messages/ stickers.❌❌❌❌ 5 Muno simosewela koma kugawana NKhani ndi Sports.✅ 6 Kumatengapo mbali osamangoti duu muzatulusidwa.✅ 7 Ulemu kwa aliyese ndiofunika✅ 8 Nkhani zaku inbox zithere Komweko Osazibweretsa Pano✅ 9 Ngati member wa group waona polakwika alowe ku inbox kwa admin Kuti Amthandize✅ 10 Kusarana ziyankhulo muno ai or zipembezo tose ndife amodzi amalawi.🚫🚫🚫❌❌❌❌❌❌ 11 Aziwitseni anthu zomwe mwatumiza kupanda kutero mupedzeka panja.✅ 🔚 by Admin

400+ membersNYA

PAKACHERE POTHERA NKHANI

*KUPHUNZITSA ZOPHIKAPHIKA, ZAMA REMEDIES KOMANSO MALANGIZO A M'BANJA*

400+ membersSNA

MA LINK, MA SCANDAL NDI NKHANI ONE

*GROUP YI TANGOYI TSEGULA KUMENE* *MWALANDIRIDWA MUNO NONSE.* *MALAMULO AMUNO ALI CHONCHI:* *1. Osanyozana kapena kunyozana mtundu kapena chipembedzo or remove.* *2. Osaponya link imodzi mobwereza or mutulutsidwa*. *3. Osatsatsa malondamuno. Ma porno ayi muno or mutulutsidwa*. *4. A Sing’anga muno ayi.* *5. Za ma status zizithera ku ma status komweko otherwise remove* *6. Ma Gif kapena stickers muno ayi otherwise remove.*

200+ membersFUF

NKHANI ZAMMADELA

MALAMULO 👇🏼👇🏼 1. Mukalowa tchulani dzina ndi komwe mumakhala kuti anthu akudziweni. 2. Zolaula muno ayi. 3. Nkhani za ku inbox zizithela komweko. 4. Osanyozelana Zipembedzo. 5. Tikuyenela kulemekezana wina ndi mzake. 6. Tiziponya nkhani zoona zokhazokha. 7. Mukafuna kulowa gulu la zachifundo fikilani admin kuti akulongosoleleni bwinobwino. 8. Ngati mwalakwilidwa afikileni adindo kuti akuthandizeni. 9. Aliyense akupemphedwa kutenga gawo muzochitika. 10. Nthawi yophunzitsana chinthu tikupemphedwa kutsatila mwachidwi ndi ndemanga komanso ngati sitikumvetsa tizifunsa pamapeto pa phunziro. 11. Ma stickers komanso ma vn ndi oletsedwa. 12. Za asing'anga komanso ma link ena ndi oletsedwa.

200+ membersVMW

Related searches

Sports WhatsApp communitiesAI WhatsApp communitiesBrowse all communities