Search the WhatsAd index of WhatsApp groups to find the best ones.
1 result in the WhatsAd group index
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
Malamulo a Muno ------------------------------ (1)Kupempha ndikutumiza nyimbo. (2)Nyimbo zake ziyambire 2010 kumatsika kumusi. (3)Osatukwanana wina ndimzake timalimbikitsa ubale muno. (4) Osatumiza link or ma Photo olaura kapenanso zosemphana ndi group lino muzachotsedwa. (5)Osanyozerana mtundu kapena chipembedzo tonse ndi amodzi. Komaso osaponya ma sticker muno ayi (6)Ndi udindo wa aliyense kutumiza ndikupempha nyimbo zakale koma ngati mwafuna zatsopano pemphani ku inbox ena azakupatsani komweko. (7) Ma voice note siololedwa muno koma zikavutitsitsa kuti mufuna nyimbo nde mutu wake simukuudziwa funsani admin aliyense kuti mumumvetseletse Voice note ndipo akusakireni . (8)Osatukwana muno tili ndi anthu akulu akulu azaka zapakanthawi omwe amafunika kuwalemekeza. Tiyeni titsate malamuro kuti tipitilize kusangalara ndinyimbo komanso zochitika zotikumbutsa kale lathu .
Only links No links ekurombesana Kufara chte 1 links p day pliz anopfurikidza 3 riri1 unobutswa Musawanza nalinks emabhero nema Ecocash plizz