Busca en el รญndice de WhatsAd de grupos de WhatsApp para encontrar los mejores.
1 resultado en el รญndice de grupos de WhatsAd
Enlace de invitaciรณn verificado, detalles de miembros y opciones de publicidad en WhatsAd.
*BAKILI MULUZI TV 2 ๐บ๐ก* GROUP ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ MALAMULO ALI MOTELE *(1) OSAPONYA LINKโโโโ YA GROUP INA MUNO UKAPEZEKA UTULUSIDWA TIFUTASO LINK WAPONYAYO POMWEPO* ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ *BAKILI MULUZI TV* *(2) OSANYOZANA MUNO MITUNDU KOMASO ZIPEMBEZO* ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ *BAKILI MULUZI TV* *(3) OSAPONYA ZOLAULAโโโโโโโ MUNO* ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ *BAKILI MULUZI TV* *(4) MUNO KHAN TIKUFUNA ZOKOZA MALAWI OSATI KUMAYAMIKILA BOMA POMWE LIKUPANGA ZOSAUKISA MALAWI IFE A BAKILI MULUZI TV SITIKHALA CHETE MPAKA MALAWI AZAPEZE UFULO ZIKO LATHU LINO* ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ *BAKILI MULUZI TV* *(5) NDI UDINDO WA ALIYESE KUPONYA KHAN MUNO POSADIKI MA DIMIN* ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ *BAKILI MULUZI TV* *(6) TIKHAKE AMALAWI OKONDANA NDI OLEMEKEZANA WINA NDIMZAKE KUTI ZIKO LATHU LIKHALE LOSOGOLA CHIFUKWA CHIKONDI NDICHOMano liga me aqui Andrรฉ CHUMA*. ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ BAKILI MULUZI TVCHIYAMBI KOMASO MATHERO A ULAMULIRO WA CHISLAM ( Islamic State) part 2 Kumwalira kwa Umar kudali mathero a ulamuliro wake mu 644CE Council kapena kuti akuluakulu adakhalirana pansi ndikusankha dzina la Uthman Ibn Affaan kukhala mulowa M'malo mwa Umar mu Chaka Cha 644CE Ngakhale kuti Uthman adakhala mtsogoleri wa wa asilaam , anthu ena chapasipasi sizidawasangalase kuti Uthman akhale mtsogoleri wa asilaam , koma Iwo amafuna Ali ibn Abu Talib . Uthman adakhala pa udindo kuyambira mchaka Cha 644 mpaka mu 656 , mwachidule adakhala mtsogoleri Kwa zaka 12 Uthman Ali pa utsogoleri adapanga zitunukuko izi ; Adasonkhanisa Quran kukhala Buku limodzi , poyamba Quran asilaam amayisunga Mutu ( amayiloweza ) ndiye Uthman pokhala mtsogoleri wa asilaam zidayamba kumupasa mantha kuti tsiku lina anthu amene adaloweza Quran azatha ndikufa ndiye Quran izasowa , kenako adabwera ndi maganizo osonkhanisa Quran yonse mu buku kuti isungike mpaka kalekale kumibado . Uthman ndi amene adakulisa dziko la chislam ( Islamic State) kukafika mpaka ku mpoto Kwa Africa ( north Africa) komaso chagawo chotchedwa Armenia Uthman adakhazikisa ch GROUP๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐ก๐ก๐ก๐ก๐ก๐ก๐ก๐ก๐ก๐ก๐ก๐ก๐ก๐ก๐ก๐ก๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ