Busca en el índice de WhatsAd de grupos de WhatsApp para encontrar los mejores.
1 resultado en el índice de grupos de WhatsAd
Enlace de invitación verificado, detalles de miembros y opciones de publicidad en WhatsAd.
MALAMULO:::::::::::::::::::::::::::::::::: (1) WOSAPONYA LINK YA GROUP LINA (2) ZANDALE KAPENA ZACHIPEMPHEZO NDI KUNYOZANA MUNO AYI ZIMENEZO AWA NDIMACHEZA TIYENI TIKONDANE WINA NDIZAKE (3) WOSATUMIZA CHINTHU CHOKHUZA ZOLAULA MUNO (4) WOSAYIMBA VOICE CALL PA GROUP (5) NGATI MUKUCHEZA NDI ZANU PANKHANI ZA MPIRA CHEZANI BWINOBWINO POSADUMPHA MALILE A ULEMU (6) SUNDAY TIMAKHALA NDI PIC DAY NDICHOLINGA CHOTI TIZIWANE (7) ZIWANI KUTI NDIUDINDO WAWINA ALIYESE KUTUMIZA ZINTHU ZOKHUZA MASEWELO A MPIRA KUTI GROUPLI LIBHEBHE ZIKOMO MAKOMA NONSE MASAPOTA A MA TEAM WOSIYANASIYANA✏️
*MALAMULO ATHU MUNO MU BULLETS MANOMA SILVER 🥈 ZAMASEWERO* ⚽⚽⚽ (1) alendo khalani omasuka potenga nawo mbali mu zochitika za group lino (2) *timakamba nkhani zokhuza mpira 95% zakunja kwa mpira 5%* (3) 99% zilankhulo zovomerezeka chichewa English 1% zilankhulo zina (4) *sitimalola kupanga recode kuponya ma link ama group ena ndi ma sticks ena ali onse muno* (5) matsiku ena timakhala ndi ma program monga Monday timakhala ndi mulendo wathu Friday top 20 munthawiyi sitimalola munthu kuponyapo nkhani zakunja kwa program yo mukagotero remove pompo pompo (6) *kusalana kapena kusankhana pa group chifukwa chosiyana zipembezo kapenanso mitundu nkolesedwa* (7) member yemwe sanalowe nawo mu top 20 kwa 2weeks kapena osakwanisako 30 messages adzachotsedwa (8) *tiyeni tipasane ndi kusungilana ulemu polankhula komanso pano sipopezera mkazi / mamuna chonde guys anthufe ndife akulu akulu komanso ndife pachibale za pa group zizithera pa group pompano* (9) group lino sitimalola kubweresa ma update onama pano ukangopezeka pompo pompo remove (10) *ma dmin athu nawonso ndi anthu ali ndi kufooka kwawo ngati alankhula china chake chosakhala bwino ndi ufulu wa member wina aliyense kuzuzura mwaulemu osati monyoza ayi* (11) ma dmin athu samatulutsa munthu mopanda chifukwa ziwani kuti mukangotulutsidwa simuzapangidwanso add ndiye chonde osamabwera ku in box kwa admin *mukangosunga zomwe mwauzidwa panozi ziwani kuti mukhalitsa muno mpaka kale* mphavu nyerere 🐜🐜🐜🐜🇭🇳🇭🇳🇭🇳🇭🇳 mphavu bullets 🇦🇹🇦🇹🇦🇹🇦🇹 mphave silver 🇦🇷🇦🇷🇦🇷🇦🇷 *umodzi pa machedza* 🤸♂🤸♂🤸♂🤸♂🤸♂