Busca en el índice de WhatsAd de grupos de WhatsApp para encontrar los mejores.
1 resultado en el índice de grupos de WhatsAd
Group ino ndi ya unthenga wabwino wa Yehova Mulungu mu nthawi ino yotsilidza amene angadane nazo atulukepo pano sipotumizira zithu zolakwika monga kutukwana ma videos olakwika olaula kapena zithunzi ukapezeka remove iyendapo
[link hidden — subscribe to view]?mode=ac_t *NKHANGA ZAONA PA LIMPOPO FM NDI COMRADE NTANYIWA* *MALAMURO PA GROUP PANO*. 👇👇👇📝📝📝 *OSATUMIZA VOICE CHAT* *OSATUMIZA ZITHU ZOLAULA* *OSATUMIZA LINK LA GROUP LINA* *OSATUKWANIZANA NDI MUTHU PA GROUP PANO* *OSAMANGOTUMIZA ZILIZOSE PA GROUP PANO* *NDI ADMIN OKHA AMENE ANGATUMIZE NKHANI PANO* *NGATI MULI NDI NKHANI MUKHOZA KUTUMIZA* *PLEASE SATIRANI MALAMURO A PA GROUP PANO* *NKHANGA ZAONA*✌️✌️🤞🤞🤞 🇲🇼🇿🇲🇿🇦 🔥🔥🔥🔥 *LIMPOPO FM*
MALAMULO:::::::::::::::::::::::::::::::::: (1) WOSAPONYA LINK YA GROUP LINA (2) ZANDALE KAPENA ZACHIPEMPHEZO NDI KUNYOZANA MUNO AYI ZIMENEZO AWA NDIMACHEZA TIYENI TIKONDANE WINA NDIZAKE (3) WOSATUMIZA CHINTHU CHOKHUZA ZOLAULA MUNO (4) WOSAYIMBA VOICE CALL PA GROUP (5) NGATI MUKUCHEZA NDI ZANU PANKHANI ZA MPIRA CHEZANI BWINOBWINO POSADUMPHA MALILE A ULEMU (6) SUNDAY TIMAKHALA NDI PIC DAY NDICHOLINGA CHOTI TIZIWANE (7) ZIWANI KUTI NDIUDINDO WAWINA ALIYESE KUTUMIZA ZINTHU ZOKHUZA MASEWELO A MPIRA KUTI GROUPLI LIBHEBHE ZIKOMO MAKOMA NONSE MASAPOTA A MA TEAM WOSIYANASIYANA✏️
Enlace de invitación verificado, detalles de miembros y opciones de publicidad en WhatsAd.