FRIENDS OF MAKANJIRA
Cholinga Cha group ndikukambirana nkhani zokhuza dela lathu lamakanjiri kundale zadela ,chitukuko komanso mavuto amdela
MALAMULO A GROUP
(1) osatumiza zithunzi kapena ma kanema olawula
(2) osatumiza ma link ama group ena pamudzi pano
(3) osatukwanizana pa group pano
(4) kulemekeza maganizo anzathu ,sitingaganize mofanana
(5) osatenga nkhani zokambidwa pano mwachisawawa chifukwa anthu akhala ndimaufula olankhula zakukhosi kwawo mosaopa
(6) obwela ndichisokonezo sasowa ndipo sitizachedwa kum'panga remove
(7) munthu Ali ndiufulu olemba kapena kugwiritsa ntchito mawu ake pogawana uthenga
(8) osatumiza nkhani zabodza zopanda umboni pa group
Kupezeka ophwanya malamulo adzachotsedwa pa group
(9) Group la friends of makanjira liziyamikira kapena kudzudzula andale ,akapezeka munthu obweletsao chisokonezo pa group posafuna anthu kuti adzudzule kapena kuyamikira andale ,munthuyo adzachotsedwa pa group car h
200+ membersActive this monthNYA