Busca en el รญndice de WhatsAd de grupos de WhatsApp para encontrar los mejores.
1 resultado en el รญndice de grupos de WhatsAd
MALAMULO ๐๐ผ๐๐ผ 1. Mukalowa tchulani dzina ndi komwe mumakhala kuti anthu akudziweni. 2. Zolaula muno ayi. 3. Nkhani za ku inbox zizithela komweko. 4. Osanyozelana Zipembedzo. 5. Tikuyenela kulemekezana wina ndi mzake. 6. Tiziponya nkhani zoona zokhazokha. 7. Mukafuna kulowa gulu la zachifundo fikilani admin kuti akulongosoleleni bwinobwino. 8. Ngati mwalakwilidwa afikileni adindo kuti akuthandizeni. 9. Aliyense akupemphedwa kutenga gawo muzochitika. 10. Nthawi yophunzitsana chinthu tikupemphedwa kutsatila mwachidwi ndi ndemanga komanso ngati sitikumvetsa tizifunsa pamapeto pa phunziro. 11. Ma stickers komanso ma vn ndi oletsedwa. 12. Za asing'anga komanso ma link ena ndi oletsedwa.
Enlace de invitaciรณn verificado, detalles de miembros y opciones de publicidad en WhatsAd.
1 Osasitha chithunzi kapena mutu wa gulu โโโโ 2 Ma videos olaula or pic muno ayiii..๐ซ๐ซ๐ซ๐ซโโโโ 3 Osatumiza link ya group lina muno โโโโโ 4 No voice messages/ stickers.โโโโ 5 Muno simosewela komo kugawana NKhani ndi Sports.โ 6 Kumatengapo mbali osamangoti duu muzatulusidwa.โ 7 Ulemu kwa aliyese ndiofunikaโ 8 Nkhani zaku inbox zithere Komweko Osazibweretsa Panoโ 9 Ngati member wa group waona polakwika alowe ku inbox kwa admin Kuti Amthandizeโ 10 Kusarana ziyankhulo muno ai or zipembezo tose ndife amodzi amalawi.๐ซ๐ซ๐ซโโโโโโ 11 Aziwitseni anthu zomwe mwatumiza kupanda kutero mupedzeka panja.โ ๐ by Admin