KUSADZIWA NDIKO KUFA KWENIKWENI
1. TAKULANDIRANI ABALE NDI ALONGO AMENE MUKUPEZEKA PA GULU LINO LA 'KUSADZIWA NDI KUFA KWENIKWENI" CHOLINGA CHA GULU LINO NDIKO KUPHUNZITSANA WINA NDI MZAKE, KOMA NDI MAUMBONI OGWIRIKA, IFE AMENE TIMATSATIRA 'MASHIACH'(MESIYA) TAFUFUDZA MU SAIZI YATHU NDIPO TAPEZA KUTI MABAIBULO ONSE AMENE ALIPO LERO KU CHIKHRISTU ACHITA KUSANDULITSIDWA' UMBONI WOGWIRIKA ULI NDI MKONZI NDI MLEMBI WA "HEBRAIC ROOTS BIBLE" Sinior Elder wa Mpingo wa ku YHWHSHALYM(JERUSALEM) B'Shem Yahshua, komanso a Societi ya Malawi, kudzera Mu Mpingo wa KATOLIKA, komanso Mpingo uja wa MBONI ZA YEHOVA,,
2. NDIYE CHOONDE AMENE MUNALOZEREDWA KUTSUTSA OPANDA UMBONI, WOTSUSIRA SITIKUKUTSOWANI PAGULU LINO, NDIPO NDINU OLOLEDWA KUPITA KU ZIWE LINA LA ZITHABWI, MALEMBO AMENE AKUTITSOGOKERA NDI MISHLE (MIY) 1:5 Munthu wanzeru amvetsera bwino, kuti awonjezere kuzindikira zimene samazidziwa, ndi munthu womvetsa zinthu bwino ndi yekhayo amene amapedza nzeru yoyendetsera moyo wake.