חפשו באינדקס קבוצות הוואטסאפ של WhatsAd כדי למצוא את הטובות ביותר.
תוצאה אחת באינדקס הקבוצות של WhatsAd
Timaphunzisa decoration, baking, cooking, carpentry , sausage making and many more zonsezi mukaphunzira mumapasidwa certificate ♥️♥️♥️ zabwino zipose apa............. Sankhani course yakumtima kwanu ndipo muzathandizidwa moyenera ZIKOMO🥰🥰🥰👏👏👏👏👏
*TAKULANDIRANI KU GROUP YATHU DZIWANI KUTI TILINDI MA PDF ILIYONSE NDI 1000 KWACHA MUSAKHA PDF NUMBER YOMWE MUKUYIFUNA* Lipirani ku ma number omwe ali apawa Airtel money 0986795267 Or mpamba 0882400381 Mukalipira inbox with screenshot tizakupasani pdf yanu Ma pdf Ali motere 1 *🍞 Baking & Cooking PDF* Mapulani opitilira 40 monga: • Chocolate, Vanilla, Pineapple & Red Velvet cakes • Pizza, Sausages (home & business), Chicken & Beef recipes • Ice cream, Juice, Maheu, Peanut butter • Jam, Tomato sauce, KFC recipes 2 *🏭 Manufacturing & Household Production* Soap, Dishwash, Perfume, Jelly, Pine gel Wine, Glycerin, Baking powder, Peanut oil Sweets, Biscuits, Soya pieces, Mbeya fertilizer Tissue, Mchere kuchokera ku zomera 3 *🐓 Animal & Poultry Farming PDF* Nkhuku (Mazira, Nyama, Organic), Nkhumba, Akalulu, Chitopa Bee farming, Guinea fowl, Quail, Chicken housing Matenda a nkhuku ndi mankhwala ake 4 *🌱 Crop & Fruit Farming pdf* Onion, Tomato, Maize, Tumeric, Banana, Avocado, Mushroom 5 *Natural Remedies & Agri Guides PDF* 6.Mankhwala achilengedwe kwa anthu 7. Primary and secondary school books komaso ma past papers
קישור הזמנה מאומת, פרטי חברים ואפשרויות פרסום ב-WhatsAd.