ืืคืฉื ืืืื ืืงืก ืงืืืฆืืช ืืืืืืกืืค ืฉื WhatsAd ืืื ืืืฆืื ืืช ืืืืืืช ืืืืชืจ.
ืชืืฆืื ืืืช ืืืื ืืงืก ืืงืืืฆืืช ืฉื WhatsAd
TIPEZE KU INIBOX TIKUPASENIYAKUTIMAKWANU MUVU
ืงืืฉืืจ ืืืื ื ืืืืืช, ืคืจืื ืืืจืื ืืืคืฉืจืืืืช ืคืจืกืื ื-WhatsAd.
MULI OLANDILIDWA NDIPO KHALANI OMASUKA KOMA IFE MA ADMINI TIMAKHALA NDIMA CONDITIONS AMENE MUKUYENELA KUWASATA MONGA NGATI MA MEMBERS A GROUP LINO 1 osapanga send link ina iliyonse pa group kupatula la group lino 2 tikakhala ndizochita pano pa group ngati pic day komaso ndi zina zambili ngati simukutenga nawo gawo asala yake ndi remove 3 osapanga send zithuz zolawula kapena video ๐น yolawula 4 ma recording saloledwa pano 5 voice chat kapena kuti call sizoloredwa 6 osapanga send sticker iliyonse 7 member aliyese akuyenera kukhala ndima message opitilira 10 patsiku 8 anthu omwe simukufuna kukhala pano khomo ndilotsekula mukhoza kutuluka 9 zako ngati akuyambisa mapokoso kapena akukutukwana musabweze chifukwa mukatelo mukhala limodzi pa ulendo 10 khalani anthu okondana ngati ndife amalawi tokhatokha 11 matumizidwe amafilm ngati film yatumizidwa osayibwelezaso 12 ngati muli ndi number yomwe ikufunika kupanga add tumizani ndipo ipangidwa add GROUPULI LIMALAMULIDWA NDI ANTHU AWA OYAMBA DESMOND WACHIWIRI MR PEACE WACHITATU SHONGA WACHINAYI ASIFA WACHI NUMBER 5 LAMIN YAMAL. NGATI PALI VUTO APEZENI ATHU AMENEWO AKUTHANDIZANI NDINE WANUWANU DESMOND DMINI ๐๐๐
TAKULANDILANI KU ZAKWATHU KUMALAWI ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผGROUP mala Mulo athu Ali motele ๐ฉธ๐ฉธ๐ฉธ ๐ฃ๏ธMUKALOWA ponyani chithuzichanu chimodzi ndikunena komwe mumakha komaso dzina lanu ๐ฃ๏ธKUNYOZELANA ZIPEMBEZO AYI opezeka azachosedwa ๐ฃ๏ธKUSAKHANA MITUNDU KAPENA OCHEZANAWO AYI kupezeka out ๐ฃ๏ธVN KAPENA ODIO NDIYO LOLEDWA ngati sutha kulemba osafinyika ndizakwathu izi kumalawi ๐ฃ๏ธOSATENGA MBALI KWA WEEK OUT ALIYESE akuyenela kutenga mbali pa group pano ๐ฃ๏ธKUPEZA BANJA MUNO NKOSALESEDWA bola ngat mwamvana ku in box ๐ฃ๏ธZOLAULA MUNO AYI (BM) KOMASO ASING'ANGA AYI opezeka out ๐ฃ๏ธSUNDAY TIMAKHALA NDI PIC DAY ALIYESE akuyenela kuponya photo yake ndikuzifotokoza komwe amakhala ndi dzila lake kuyenda nkumvina Inu KHALAN OMASUKA NDIINU OLANDILIDWA PA GROUP LAZAKWATHU CHENJEZO Gati sukusatila malamulowa uzachosedawa ukachosedwa osazada muthu komaso macheza ngosalesedwa koma bola machezao akhare osaphela ufulu wa muthu wina kapena chipembeo Kuchokwela kwa addmin onse tingot ZAKWATHU OYEEEE!!!!!!!!!!๐ฉธ๐ฉธ๐ฉธ๐ฉธ๐ฉธ๐ฉธ๐ฉธ๐ฉธ๐ฉธ๐ฉธ๐ฉธ๐ฉธ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ