ืืคืฉื ืืืื ืืงืก ืงืืืฆืืช ืืืืืืกืืค ืฉื WhatsAd ืืื ืืืฆืื ืืช ืืืืืืช ืืืืชืจ.
ืชืืฆืื ืืืช ืืืื ืืงืก ืืงืืืฆืืช ืฉื WhatsAd
TAKULANDILANI PANO PA KUPEZA WACHIKONDI MOSAVUTA AND MOSALIPILITSA Malamulo ali motere 1๏ธโฃ kupeza wachikondi ndi ulere 2๏ธโฃ ngt mukufuna mkazi /mamuna pezani admin aliyese ndipo muzifotokoze like 1 zaka 2 ana ngt mulinao 3 mukukhala kt nanga wachikondiyo akhale wakt 4 akhale wazaka zingt mkazi/mamuna mukumufunayo mukatelo muzidikila admin mwamutumizila zithuyo kubwereselani wachikoniyo 3๏ธโฃ ngt mkazi or mamuna mwapatsidwao sadakusangalaseni muliso ndi mwai obwera kwa admin ndikuwauza kt akupaseniso wina 4๏ธโฃ sitimalora zinthu izi 1 kuzipanga post wekha 2 ndi admin ekhayo amapanga post muthu ngt mwini wakewe ukuvomera kt akupange post pa grp 5๏ธโฃ ngt mwalowa ku inbox kwa mkazi ky mamuna without admin zomwe mukazione uko ife sizimatikhudza 6๏ธโฃ timakhala ndi call pa grp pano aliyese ndioloredwe kukapanga join 7๏ธโฃ pano sitimalora zinthu izi 1 Zolaula 2 ma sticker 3 kunyozana 4 link ya grp ina muno ai 5 za ku inbox ky maudani akomwetimakhalako asabwere pano Ngt zina zakusowetsa mtendereukufuna ma ganizo anthu pezani admin tizapnga topic ndipo muzapeza choonadi kuchokera ku maganizo anthu omwe amapeleka pa toic Akapezeka onyozela malamulowa timapanga remove posatengera mtundu By admin
ืงืืฉืืจ ืืืื ื ืืืืืช, ืคืจืื ืืืจืื ืืืคืฉืจืืืืช ืคืจืกืื ื-WhatsAd.
*TAKULANDIRANI KU TIPEZE WACHIKONDI ๐๐* *MALAMURO NDI AWA* ๐ *1๏ธโฃALIYENSE AKUYENERA KUTENGA NAWO MBALI KUTI MACHEZA AKOME KOMASO KUTI TIPEZE WACHIKONDI MOSAVUTA๐ฉโโค๏ธโ๐โ๐จ๐จโโค๏ธโ๐จ* *2๏ธโฃMULENDO UKAFIKA AKUYENERA KUPONYA PIC NDI KUNENA KOMWE UMAKHALA๐๐บ* ๐คณ *3๏ธโฃMA LINK AMA GROUP ENA MUNO AI ๐บ๐บ* 4๏ธโฃ *MA PROGRAM ATHU ALI MOTERE:* *MONDAY, WEDNESDAY NDI FRIDAY TIMAKHALA NDI* *TOPIC. NDIPO SUNDAY NDI PIC DAY* ๐๐บ๐คณ *5๏ธโฃNKHANI ZA KU INBOX ZIZITHERO KUMWEKO* ๐ซ๐ซ๐ซ๐ซ๐ซ *6๏ธโฃKUCHEZERANA KUZIWANA KUMAONONGA GROUP KUMACHEZA NDI ALIYENSE* ๐คบ *7๏ธโฃVOICE NOTE MUNO AI & WEEK ILIYONSE TIMACHOSA ANTHU OSATENGA NAWO MBALI* ๐คบ๐น *๐น๐น๐นTIPEZE WACHIKONDI*
Timapereka ngongole za business komanso Ulimi