ืืคืฉื ืืืื ืืงืก ืงืืืฆืืช ืืืืืืกืืค ืฉื WhatsAd ืืื ืืืฆืื ืืช ืืืืืืช ืืืืชืจ.
ืชืืฆืื ืืืช ืืืื ืืงืก ืืงืืืฆืืช ืฉื WhatsAd
WELLCOME TO KUPHWETSA MKUTO PA PHWETTE LA MACHEZA GROUPโโ๐๐ฃ๐ค๐ช* *~_NGATI ULI SING'ANGA ZIPASILETU ULEMU SOCIAL MEDIA SIMAOPA MAULA_~* *๐Cholinga cha group lino ndikundikulimbikitsa ubale komaso macheza pajaamati kuyendamkumvina๐ค๐ค๐ช* *MALAMULO ATHU ALIMOTELE๐๐๐๐๐* *1๐Osatumiza link ya group ina muno opezeka remv๐ซ* *2๐Mulendo akalowa ayenera kuponya pic komaso kunena komwe amakhala โ * *3๐ma VN ( RECORD โบ๏ธ) muno ayi* *4๐Tiyenela kulemekezana wina ndizake osati kusalana* *5๐sunday llililose tixikhala ndi pic day โ * *6๐Ngat mwalowelana ku inbox zizithera komweko zisafike kuno* *7๐osaponya zithuz zolaula komaso ma vidios olaula* *8๐Ma mumbers nose ndinu ololedwa kubwela ndi topic ngat admin sana bweletse* *9๐onse omangokhala ndwiiiii muno osama commenta zanzake zakolopedwa* *10๐Muno zandale sitilola komaso kutumiza khani za sing'anga muno ayi๐ซ๐ซ๐ซ* *๐ฃ๐ฃndakusokosela mkulinga utamva tsatiran mallamulo kuti tiyendele limozi* *`๐ค๐ค MUMODZI MULI PHAMVU BY PANGOLINI` ๐ฆ๐ฆ๐ฆ๐ฅ๐ฅ๐ฅ*
ืงืืฉืืจ ืืืื ื ืืืืืช, ืคืจืื ืืืจืื ืืืคืฉืจืืืืช ืคืจืกืื ื-WhatsAd.
TAKULNDILANU MUNON NDIPO KHALANI OMASUKA๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ๐ฝ๐ฝ
Takulandilani alendo anthu ku group lamacheza Atsikana ndi Anyamata Malamulo ali motele angati walowa kumene akuyenela kutumiza picture ndi kudzfotokozelaso muli 2 muno link ya group lina sitimalola kupatula lanthuli 3 osasankhana osankhana machezedwe muno nkazi kapena mamuna ali ndi ufulu kucheza amene akufuna muno 4 muno ma video olaula sakuloฤบdwa ukatumiza remove 5 osamulowela munthu inbox yake asadavomele kuti mupite ukapezeka ndi remove 6 Sunday ndi pic day aliyese amaponya pic osatumizayo tsiku limenelo amatulutsidwa 7 muno kungonkhala osamayankhula kapena osakometa remove 8 nkhani ya topic aliyese atha kulemba topic koma osalemba topic wina ataponya kale chonde ๐๏ธ๐๏ธ๐๏ธ๐๏ธ 9 chonde ngati mwawona kuti wina sadakuchezeleni bwino pezani admin akuthandizeni 10 muno nkhani zaku inbox zisafike pano pa group zithele konko 11 osatumiza ma sticker please ma sticker ena amankhala wonyoza nde osaponya please 12 mayina awa muno osatchula munthu ngati hule, fiti,kapolo ndi ena 13 osanyoza chipembedzo chazako muno ukapezeka remove Zikomo kwambili achibale nose muno ngati likumveka group chifukwa cha inuyo tiyeni tidzicheza Kutsatira Malamulo kut masiku ako opedzeka pano achuluke๐ฅฐ๐โฃ๏ธ๐๐๐