G1️⃣END TIME MESSENGERS
Marko 1:15 nanena, Nthawi yakwanira, ndipo Ufumu wa Mulungu wayandikira; tembenukani mtima, khulupirirani uthenga wabwino.
Malamulo ali motere
𝐖𝐄𝐋𝐂𝐎𝐌𝐄 🤝ALL MEMBERS
𝒎𝒂𝒍𝒂𝒎𝒖𝒍𝒐 𝒂𝒕𝒉𝒖 𝒂𝒍𝒊
𝒎𝒐𝒕𝒆𝒓𝒆 🙏🙏🙏
👇👇👇👇👇👇👇👇
(1) osaponya zolaura ❌🚮
(2) osatukwana ❌🚮
(3) osaponya zosephana nd group ❌🚮
(4) osaimba group chat call ❌🚮
(5) za asing.anga ❌🚮
(6) ma link a magroup ena muno ayi ❌🚮
(7) ngat mwakumana ndi vuto lilironse apezen admin akuthandizan ✅
(8) ngat mukufuna kufunsa funsan admin✅
(9) aliyense ali ndi.udindo otsatira mau a mulungu ✅
(10) kufalitsa uthenga wa ambuye wathu yesu kristu ndiye cholinga ✅
(11) pa comment ndioloredwa or record palibe vuto pamene group latsekulidwa✅
12 pewen kufunsa mafusa a chodziwadziwa cfk muzaonanga munthu wa mwano posakuyakhan
13 kozan moyo wanu pamene mukupumu , aliyense cfk tikafa tili mu uchimo nd tsoka
Mlaliki 9v4to5
Buku Lopatulika 1992 Mateyu 7:21-24 Si yense wakunena kwa Ine, Ambuye, Ambuye, adzalowa mu Ufumu wa Kumwamba; koma wakucitayo cifuniro ca Atate wanga wa Kumwamba. Ambiri adzati kwa Ine tsiku lomwelo, Ambuye, Ambuye, kodi sitinanenera mau m'dzina lanu, ndi m'dzina lanunso kuturutsa mizimu yoipa, ndi kucita m'dzina lanunso zamphamvu zambiri? Ndipo pamenepo ndidzafukulira iwo, Sindinakudziwani inu nthawi zonse; cokani kwa Ine, inu akucita kusayeruzika. Cifukwa cimeneci yense amene akamva mau anga amenewa, ndi kuwacita, ndidzamfanizira iye ndi munthu wocenjera, amene anamanga nyumba yace pathanthwe;
`
14 mateyu 7v14 aliyense akhale mchimenecho
By admin desk
✅✅✅✅✅✅✅✅✅✅✅✅✅✅✅✅✅✅